A MICHAEL USI KUYANKHULA PAMASO PA PRESIDENT -27 March 2024

2024 ж. 26 Нау.
139 617 Рет қаралды

Пікірлер
  • SKC my vote

    @user-qp8kh2hj9o@user-qp8kh2hj9o29 күн бұрын
  • Keep the fire burning Mr Usi❤

    @user-id1oo9hl5x@user-id1oo9hl5x18 күн бұрын
  • Mr president,,,,you're responsible to bring the solutions,,,,not asking us the way forward,,,,just command what suppose to be done,,,,adzikupisani mr ussi,,,fundo

    @frasermoyo8999@frasermoyo8999Ай бұрын
  • My vote is for apm

    @patricgama4788@patricgama4788Ай бұрын
    • Mmene wathera muja? Ndiye kuweramira chitandatu

      @djmakedzana9917@djmakedzana991728 күн бұрын
    • 😂😂😂😂mpaka chitanda

      @gesinasutherland9241@gesinasutherland924126 күн бұрын
  • Ise tikufuna anyamata president ngati Senegal chilima bomaa

    @user-le9su3mt7r@user-le9su3mt7rАй бұрын
  • Amalawi munansanga wolakwika mbambadi course wochakwela wolibe mfundo nthawi zonse amakalila mawu amodzi please next time we need be very careful pangani yonsanga upule chifukwa ntchito iyi sintchito yamasewela ayi yy😢😢😢😢😢😢😢😢

    @issahkagansamussah@issahkagansamussahАй бұрын
  • Powerful message

    @AlexisKantondo@AlexisKantondoАй бұрын
    • Which message?

      @user-jn9tz3li3v@user-jn9tz3li3vАй бұрын
    • Which message?

      @user-jn9tz3li3v@user-jn9tz3li3vАй бұрын
  • Fundo zapa maliro 2% zandare 89%

    @user-jn2oc3cn3q@user-jn2oc3cn3qАй бұрын
  • Apm my vote

    @SamuelMakalani@SamuelMakalaniАй бұрын
  • Powerful massage

    @user-ip4kz3jo8y@user-ip4kz3jo8y19 күн бұрын
  • Great speaker

    @TimothyKwangu@TimothyKwangu22 күн бұрын
  • Chakwera my vote. Osati opanda Mano mkamwa uja ngati wadya chimanga chotentha

    @christophergibson72@christophergibson72Ай бұрын
    • Mbolo yako

      @FrankPhiri-iw9xm@FrankPhiri-iw9xmАй бұрын
  • Malawi dziko lomvesa chisoni always doing politics very shameful

    @user-eh1gn1nj9d@user-eh1gn1nj9dАй бұрын
  • Usi zinazo wangoyankhulira ntchito koma mwainu mulibe sogolo labwino kuposa kuba kupha ndikuononga

    @user-vl5on2lj8b@user-vl5on2lj8bАй бұрын
    • Pp

      @LukaSavala@LukaSavalaАй бұрын
    • Ku opposition kumeneko ?

      @ancientnkhata1137@ancientnkhata113726 күн бұрын
  • Mr Michael usi amatha heavy

    @LenardWillard-nu6fr@LenardWillard-nu6fr29 күн бұрын
  • Andale inu muziyamika chifukwa kuno ndi ku malawi, koma kunakakhala kuti ndi ziko la mkhongo ine ndinakakhala mmgulu lopanga upo okuphani for sure inu nonse ndi mbeu yoipa kwambili.

    @user-jk8sh7fh2d@user-jk8sh7fh2dАй бұрын
    • Zoona same like me

      @user-ks3uw3pq7d@user-ks3uw3pq7dАй бұрын
  • @JamesAjibu-ff6rf@JamesAjibu-ff6rfАй бұрын
  • Za ziiiii

    @josephkalulu4320@josephkalulu432021 күн бұрын
  • 😂😂😂 utm is not a small. Party it has brilliant brains 😊

    @emmanuelchavula7144@emmanuelchavula7144Ай бұрын
  • APM my vote

    @owenmoses9434@owenmoses9434Ай бұрын
  • Wise saying Dr Utsi we really need to pray for our leaders as good citizens and that has promises attached before God.

    @isaacchagwa2917@isaacchagwa2917Ай бұрын
  • Chilungamo, kuvotela (Ras Chikomeni Chirwa) munthu wapadela, amene ali ndi mfundo zothandiza dziko la Malawi, Dpp, Utm,Mcp Udf, no more we need new leadership.

    @user-fv3mb2qm7n@user-fv3mb2qm7nАй бұрын
  • Mr president how many advisor do you have? Is it a speech to tell malawians? That is speechless, am not against with you but as president mumayenera kukhala ndi fundo zogwilika, zopasa chiyembekezo koma mmmmmmm tidabesa amalawi koma Mulungu atichitira chifundo

    @ChikumbutsoJohn-rs4tt@ChikumbutsoJohn-rs4ttАй бұрын
  • Very few of us know who Eliya is

    @jackwilfrednyangazi2756@jackwilfrednyangazi275626 күн бұрын
  • Thus very true

    @DavieZimba-hr4vs@DavieZimba-hr4vs21 күн бұрын
  • Kwatsara pan'gono kucha

    @AustinPanja@AustinPanja28 күн бұрын
  • Apm team we are

    @user-qx3dd7xt9c@user-qx3dd7xt9cАй бұрын
  • Bwanji Vice president bcz phindu asamayendenawo sindikuona

    @KnowxySainet@KnowxySainetАй бұрын
  • Mmmmm koma pa chakwela nde tidabetsa basi kuchitakusowa ndi mfundozomwe iiiiii amalawi basi tilibe chiyembekezo? Chakwela ndi panja pa munthu😢😢😢😢😢💔💔💔💔💔

    @DitebogoMarutle-wy8qo@DitebogoMarutle-wy8qoАй бұрын
    • Inu munthalika mumavapo fundo zanji? Bodzalokhalokha basi

      @OwenNyangu-nv1yt@OwenNyangu-nv1ytАй бұрын
  • Usi zining'a mumachulutsa sometimes kungoyankhula straight forward ndibwino, Ena akuwomba mmanja koma sanamve zomwe mwatanthauza pazomwe mwayankhula, #eliya wabwela

    @chisomotolani1186@chisomotolani1186Ай бұрын
    • True

      @excellthom8245@excellthom8245Ай бұрын
    • 😂😂😂😂😂

      @user-uc1pd1tc2x@user-uc1pd1tc2xАй бұрын
    • Ndipo live

      @JonesChingaya-yf4gg@JonesChingaya-yf4ggАй бұрын
  • Anthu aku Mulanje angopitilako kut akakuziweni palibe vote ya Chakwera pa anthu onsewo😂😂😂

    @charitylyson7350@charitylyson7350Ай бұрын
  • Chakwela mbava

    @user-le9su3mt7r@user-le9su3mt7rАй бұрын
  • Palibe chomwe tapidula ife ndi chakwera bola Apm

    @MathewsMANDUTU-lh6oo@MathewsMANDUTU-lh6ooАй бұрын
  • Ndalezo zikufunako chani kumaliroko

    @user-hx9mg6ei1t@user-hx9mg6ei1tАй бұрын
    • Onse ali ku nsanja uko ndi a ndale amadyera momo

      @africanmusichits265@africanmusichits26526 күн бұрын
  • Oooooooh my bando yawonongeka pazadzi koma galuyu

    @princedetbozsmallboy1749@princedetbozsmallboy1749Ай бұрын
  • Zachamba eti Kodi odzutsa president samakhala vice mesa

    @user-lz5tl7gn4v@user-lz5tl7gn4vАй бұрын
  • Ukupanga zosankhana mitundu ndi iweyo Chakwela ma udindobonse azibalewawo ndi ana ako

    @user-oc9vl9xz8e@user-oc9vl9xz8eАй бұрын
  • Mbomba lija anakonzekela mademo akalindo

    @homeremedys3748@homeremedys3748Ай бұрын
  • Bwana chilima mukukalambatu

    @AustinChiyembekezo-cx4mz@AustinChiyembekezo-cx4mzАй бұрын
  • I can't waste my time honestly,I have important burning issues to pray for, don't provoke me please 😠😠

    @alexsumani6823@alexsumani6823Ай бұрын
  • See you next year September guys, you really fooling down any time

    @samuelbrian3409@samuelbrian3409Ай бұрын
  • Mbuzi za anthu

    @mphatsojuliostandy4918@mphatsojuliostandy4918Ай бұрын
    • Kkkkkkk

      @MadalitsoMaungu@MadalitsoMaunguАй бұрын
  • Mbambande Mr usi

    @WadalitsoChinguwo@WadalitsoChinguwoАй бұрын
  • Izi nde za ziiii

    @user-xv5pr3ji6w@user-xv5pr3ji6wАй бұрын
  • Komatu anthu Inu panachitikila Freddy paja mukabwere lero,manyazi mulibe

    @user-go1eh4fq3i@user-go1eh4fq3i28 күн бұрын
  • Anthu tizikupemphelelan kt mupange cha, takupemphelelan 4years tapindula chan kwainu

    @user-ue8eb9hj6s@user-ue8eb9hj6sАй бұрын
  • Joseph mkasa

    @Robertmalunga-bi8sj@Robertmalunga-bi8sj4 күн бұрын
  • Ndale ndi kumaliro komwe kma chakwela ndi otsekesa kwambili

    @jabulilemngomezulu3243@jabulilemngomezulu3243Ай бұрын
  • 2 let for mama.2025,kuba mukubaku uku,mudzabvala,ma silipasi okutha.amalawi,alipopaja.

    @HarrisonMwanga-xy4sc@HarrisonMwanga-xy4scАй бұрын
  • Abanja limodzi kodi ena mkudya ena akugona njala‼️‼️ ife ndima opharn bax 😳😳

    @noahtsamdoka1172@noahtsamdoka1172Ай бұрын
  • Usi ndimwana wanzeru

    @MwawiMinga@MwawiMinga5 күн бұрын
  • 😂😂😂 Komatu akulu awa amayankhula mwachidule😂

    @JohnKanjete@JohnKanjete28 күн бұрын
  • Wakumva wamva osamva sanamve zomwe wanena Manganya

    @lukempata3086@lukempata308621 күн бұрын
  • Uyu sichilima iyi ndindondocha yachilima chifukwa chilima amene timamudziwa Kuti amalankhula ichi ndichikwangwani nchifukwa sichikulankhula chilichonse

    @user-bi6pb5gc8t@user-bi6pb5gc8tАй бұрын
    • Komadi ndi ndondocha

      @user-si7po9sd5i@user-si7po9sd5iАй бұрын
    • 😂😂

      @user-nx7yz4qo8f@user-nx7yz4qo8fАй бұрын
  • Tilibe nthawi yowapemphelera achilima ndi chakwera masataniki nkhati amenewo

    @user-vl5on2lj8b@user-vl5on2lj8bАй бұрын
  • Kkkkkk inu kodi ndindani mukamakhala mumati ndini ndani Eliya wabwera Abushiri alipano mukawauze Ambuyanu kuti Eliya wabwera mukamalira Achilima ali apo Achakwera ali apo dziwani kuti aEliya wabwera amanena ndani Bushiri kapena ndani mManganya sazatheka

    @user-cv3zw9ic6d@user-cv3zw9ic6dАй бұрын
  • Kkkkk koma ussi kubalalitsa chakwera kumeneku?

    @MadalitsoWaya-uo7mi@MadalitsoWaya-uo7mi29 күн бұрын
  • Kkkkkk a usi tidaikatu chikhulupilirotu mwainu koma aaaasa madzi a mphutsi

    @user-un6qv6sj3h@user-un6qv6sj3hАй бұрын
  • Tidziyankhula zinthu ndikuzichitq

    @MaganizoSalima@MaganizoSalima24 күн бұрын
  • Akupasa chani

    @HopeNandola-ew8td@HopeNandola-ew8tdАй бұрын
  • A usi koma muli ndi ku mudzi inu,? Ngat mulinako mmapita koma? Mwayankhula ngat mukukhala kunja kwa dziko linotu, kuyankhula kot akuchemeleleni mabwana anuwo zomwe zili zaziiiiiiii ndizotipsetsa ife mitima

    @Jermah51kennias@Jermah51kenniasАй бұрын
  • Watipha Lazaro,wawononga dziko

    @user-cd4df3vg4y@user-cd4df3vg4yАй бұрын
  • Funso labwino kwambiri, Chakwera Ndi ndani?yankho, Chakwera Ndi mbava 💯 10:42

    @dondamissonchdziwe3958@dondamissonchdziwe3958Ай бұрын
  • Aaaa ofoira uyu

    @user-bz4fs6gv8v@user-bz4fs6gv8v29 күн бұрын
  • Pemphelo, loti lipite kuti kwayani lipite kwasatana lazalas ndi nkazake chilima

    @user-pw1kl3vo5d@user-pw1kl3vo5dАй бұрын
  • Michael Usi ndi katundu samaopa 😅

    @africanmusichits265@africanmusichits26526 күн бұрын
  • 😮😮

    @user-nr7st1ox7y@user-nr7st1ox7yАй бұрын
  • Iweyo ndipambali penipen

    @user-rr8kq2dc9j@user-rr8kq2dc9j15 күн бұрын
  • Usi zining'a zakozo uzatipweteketsa nazo....nfundo zabwino koma kuzikoletsakoletsa...ma drama paliponse kodi....kumakhala serious koma

    @user-mw6zl2dt5t@user-mw6zl2dt5t6 күн бұрын
  • Unification gathering

    @GervaseGamadzi@GervaseGamadzi28 күн бұрын
  • OK chabwino akambilanaa

    @MadalitsoMaungu@MadalitsoMaunguАй бұрын
  • Ine mau ambiri ndilibe always mau ambiri ndilibe kkkk

    @user-vo7cb4cv5d@user-vo7cb4cv5d29 күн бұрын
  • 😂❤

    @DaveMafuken@DaveMafuken29 күн бұрын
  • Kkkkkkk koma dziko ndi anthu akhe

    @jameskachulu8141@jameskachulu8141Ай бұрын
  • Azapenphelela ndani awusi zaziiii

    @Abdul-xk8dq@Abdul-xk8dqАй бұрын
  • Kkkkk watera ndege pompano kkkkk ndie kt chan?

    @WonderfulSalifu@WonderfulSalifu24 күн бұрын
  • 😂😂😂 Koma malawi ife tizipephelera achuma mmalo motipephera anthu osaukafe

    @MaliGomani@MaliGomaniАй бұрын
  • 13:49 kuyankhula KWA nzelu michale usi

    @Daneck-rm1gg@Daneck-rm1ggАй бұрын
  • Very nice, cook talking President.You are my vote.God continue bless you good president.

    @FOSTERLUPIYA-zc1xv@FOSTERLUPIYA-zc1xvАй бұрын
  • Mapephelo ndiwofunika koma ukusokoneza zithu ndi iweyo kusakhana mitundu ndiweyo mwangozazana palipose achigawo cha phakati nokha nokha uziwona thawi ikubwela

    @user-ud9wl8yg1t@user-ud9wl8yg1tАй бұрын
  • Chakwela amaganizanso ngati Mbuzi kwabasi

    @user-yu9pn8ux1k@user-yu9pn8ux1kАй бұрын
  • okay 😱

    @user-gk6bf7xe9g@user-gk6bf7xe9gАй бұрын
  • Eliya wabwera 😂😂😂

    @glynbulambo@glynbulamboАй бұрын
  • Michel usi umatha mwachinsisi kkkk zimenezo ndiye ndale

    @user-oc9vl9xz8e@user-oc9vl9xz8eАй бұрын
  • Apa sindinanvepo fundo yeni yeni, chakwera alibe nfundo, ndipo sakukwana pa u President ayi. Za ziiiiiiiii! Bola michael Usi.

    @user-pv9uk6sc3w@user-pv9uk6sc3wАй бұрын
    • Osakonda mtendere akunenedwayo ndi Inuyo.Adzwinansotu a Chakwera.

      @FOSTERLUPIYA-zc1xv@FOSTERLUPIYA-zc1xvАй бұрын
  • Choka iwe galu

    @Mbwanaayami-hp3xk@Mbwanaayami-hp3xkАй бұрын
  • Mr president 😂😂 tandipasani dzina la amene wakulembeni speech😢

    @SungeniNgombero@SungeniNgomberoАй бұрын
  • Eliya wako wabwera ndi njala choka iwe

    @MathewsMANDUTU-lh6oo@MathewsMANDUTU-lh6ooАй бұрын
  • Kumaliro mpaka uniform yachipani

    @user-rp2bc1ro3r@user-rp2bc1ro3r23 күн бұрын
  • Muzizipemphelela nokha ndani amene angamataye nthawi yake ya padela ndikumapanga za inuo ngakhale iweo usi fodya bas uzipemphelele wekha wamva iwe za ugalu basi

    @user-jl6sq3ph1b@user-jl6sq3ph1bАй бұрын
  • chakwera ine sindingamupepherere😢

    @AlbertDuke-of9nn@AlbertDuke-of9nnАй бұрын
  • For what Mbuzi ngati zimenezi

    @user-vx5vk5ss6k@user-vx5vk5ss6k29 күн бұрын
  • Iwe Siwa yamba NDI iwe zosakhanazo buzi

    @KassimmwSteven-og8ny@KassimmwSteven-og8nyАй бұрын
  • Anthu oipa awa kobasi amatitenga ngati chitosi

    @AlexZambia-hq2jk@AlexZambia-hq2jk29 күн бұрын
  • Bambo Asikono ....Anakonza😂😢😅

    @user-vq9if2ep5q@user-vq9if2ep5qАй бұрын
  • Chakwera ndi chilima ndi amfiti onsewa

    @user-si7po9sd5i@user-si7po9sd5iАй бұрын
  • namadrama mapazi ako aliyetse amazipempherera yekha

    @user-qj3db4lu7c@user-qj3db4lu7cАй бұрын
  • Ndipo m’mutu mwachakwera mulidi mphuzi anabwerellanji 😢

    @princedetbozsmallboy1749@princedetbozsmallboy1749Ай бұрын
  • Chakwela galu wa pusident chisilu

    @RobertLuka-wy9cl@RobertLuka-wy9clАй бұрын
  • Kupempheler mbabva

    @user-ik7fq4ok2r@user-ik7fq4ok2rАй бұрын
KZhead