Hilco and Ching'axy - Provoke Provoke ( Plan B Season 1 Episode 2 )
2024 ж. 7 Нау.
388 018 Рет қаралды
Get Wakuba Audio 👇
open.spotify.com/album/6Nopi5...
Get Wakuba From A store Of your choice 👇
fanlink.tv/vz6z
Watch Pemphero ft Sangie 👇
• Hilco feat Sangie - Pe...
Get My E.P Maluwa 👇 open.spotify.com/album/7Dpfql...
---------------------------------
Follow Hilco
TikTok : / hildaulolo
Instagram : / hilcomw
Facebook : / hilcomw
#hilco #ching'axy #wakuba #ponit #malawi #trending #maluwa #hilco #ching'axy #planB #malawi #comedy #trending
😂😂😂😂 Fanz yaching'axy ibwele pano tipatse moto🔥🔥🔥👍
provoca basi
😢❤😮😮😮@@vincentngulube2300
Nice 👍👍 well done 👍👍✅
Wow that's awesome 👍
Fans ya Hillco bwelan pano tiipatse moto pa modzi ❤🎉
Ife ai😂😂
Tilipo tiyipasa moto
mkazi winayo ..amanga hilco kumutu she is too emotional ...akufunika traning yabwino ...
The prove mode.😅😅🔥 Was everything
Hahahahahahaha kofunsira banja kuja akufunsirakonso ntchito ,mpaka kulira.
Ndpo kufusila kuja osazapwekesa ndi ntchito yapadera.
Ine ngat ndingalembedwe ntchito tuu kumeneko ndiyonkhala ndi Hilco yooo 😂😂😂😂😂 ching'axy fire 🔥🔥🔥🔥
🙌🙌😂
😂😂😂😂😂
Ati " look at Mr spider 🕸 " koma @ching'aning'an you are the best Comedian in Malawi 🇲🇼.
Eeeh komano ching'axy amatha ma guy eeeh 😂😂 🔥 🔥 Next plz
Ndipo ndi dolo kwambili
This guy is something else
Ching'axy ma award onse mpaseni 😂😂😂
Ndi a usiku omwe😂😂😂
Kufunsira kuja ndikovutaa😂😂😂😂Ine umbon ndili nawoooo😂😂😂
😂😂😂😂😂😂
😂😂😂😂😂
Mwachita bwino pomuthandiza ndinnaKakhara ineyo munakatani kkk ❤ you
Amayi anga❤
Koma Ng'axy😂😂😂😂😂😂😂 Hilco keep the fire burning, I have laughed today lol😅😅😅😅😅😅😅😅
Ati look at Mr Spider 🤣🤣🤣
😂😂😂
😂
I love this...mayi ching'axy
I love seriousness in all the actors 😂 Mabwera ngati coming
If you see this comment in 2063 know that I was watching this in 2024 while smiling 😀
Am gonkoko😂
2063 youtube kuzakhala kulibe aise
kkkkkkk guys
😂😂@@mlimolubanda6348
Thanks for the feedback
Zabhob
Hello
Kkkk for those watching in 2080 remember that I shall be in the grave then
Wow this is so great guys😂 Km Ching'axy😂😂😂
Umakwana ching'axy ati muzipempha appointment 😂😂😂
Kkkkkkk Mmmm chinga`aning`ani unapitililila pokwana I can't wait for episode 3 Guys chonde pasamatenge nyengo yaitsli musanatuluse kena mix mukutisiyila nmalere anyway more fire
@@AungunKadzinja-wv2uc kod part 3 sibwela
Ili fire mwala mwala ching'axy ndi gate man 😂😂
Kuyipasa moto chinga'axy😂😂😂😂
I can't wait, next 🤣😂🤣
Provoke provoke 🤣🤣🤣🤣🤣 kma yeah 🙌
God be with you Hiloc be with me 😂😂😂🔥🔥🔥😊
Wow! I've enjoyed it. Can't wait for the next episode. 🥳😋 Ndi Ambuye indeed 🔥 from the song in the background.
Wow that's great 🎉
Ati awumale mi😂😂
😂😂😂😂 Ching'axy ati munthu osekesa ngat iwe sindinamuwone chonsecho osekesa ali iyeyo 😂🙌🙌🙌
Paliponse pakungosekesa ndiye nkuyambila pati kusekako 😂😂😂 ching'axy anaza 😂😂😂😂
Uyu kukhomelela 😂😂😂😂more 🔥🔥💯♥️♥️
Adha awowo operekeza ching'axy, a very good actor
More fire 🔥 keep it up guys 🥇
Ndaseka paka misozi
Ndungoseka ine kuno iiih. Ching'aning'ani ndi dolo eeeesh 😂😂😂🙌🙌🙌🙌
God be with you & Hilco be with me... koma ching'axy 😀😀😀
😂😂😂Ayi ndithu. Zoti kufunsila kumavuta Ndaonela pa ching'axy😂🤣 Ayi ndithu. May God be with you and Gate be with me😂😅🤣
Ching'asy aise 🔥
Kali bho😂😂😂 can't wait next ep
This is great
Wangoyamba kulira chingaxy po mmene ndasekera ine😂😂😂😂komatu mwaikometsa musachedwe ina changu❤❤
Fire 🔥 🔥 🔥 mabomba ching'axy n Hilco
God be with you, hilco be with me 🤣🤣🤣🤣
Ching'axy anagkonza
Hilco be with me 😂😂😂😂😂 chi vibe ching'axy
Provoke, provoke😂😂
Kkkk zina umangoona waziyamba❤❤😅😅
bwana ching''axy kkkkkk nice one
😂😂😂 can't wait another part
Video ya clean ❤
Umafunika kukakamila inde ching'aning'ani
At ali n mayake ovutika 😂😂❤❤
😂😂😂😂ching'aning'ani more 🔥🔥!!
😂😂😂😂😂😂kkkk ipatseni 🔥😍😍😍😍 guys 🎉🎉🎉🎉❤❤❤
Ching'axy anabwela kudzakhala😂😂😂😂
Kuphandako nde amalila kkkkk😂
💥💥💥💥💥 Umakwana m'dara wazimagwelu 😂😂👏😂😂
Akuti kusakhulupilira ngati Thomas didimu kuti misomali inayenda bwanji 😂😂😂😂
ching_axy his always make crazy....... big up to hilco and them
Kikkkk,, ati mukhala pa pay slit 😂😂😂 Ching'axy 🔥🔥🔥🔥
Ching'axey tsopano
Koma yah
Koma akazi okongolanu mutipepeletsa bwanji 😂
Fanzi ya hilco bwelani tiyibongese🔥🔥🔥🔥😄🤣😂
😂😂kofusila mpaka kufuna tchito 😏
🤣🤣🤣🤣 aaa nde amabwera kuzagwila ndi wina iwe ukulepheera choncho
Kkkk kuyambira lero alimi ndasiya kucheza nawo 🤣🤣🤣🤣
Ching'azy tsopano wabwera ndi fire 🔥🔥🔥💚 ipitilize mission ilibwino hvy
😂😂😂 u made my day guys😂
umakwana ching'axy
😅😅😅😅 bwana ching'axy ati mkazi uja ndagwira.... My me
Adona atsegula gate wa nde mmmmm Ali serious 😅😅😅ngat afuna iwowo bwa
Kkkkkk aaaa zee mfundo zeee nothing Koma ching'axy 🤣🤣🤣🤣🤣 ayi senks 🔥 🔥
😂😂😂😂😂 Koma mfundo kubakalika hahaha
Kufunsira mkovuta😂😂😂
Way to go uli bho keep pushing
Kofusira mpaka kulira 😂😂😂😂
This is beautiful
Kikikikiki za power another episode please 😂😂😂😂😂😂
Bro 🎉 keep fire burning
Komatu umatha hilco
Mmmmm ndimachedwa yatuluka❤❤❤❤ imandiwaza azibwelabe
😂😂😂😂😂Atii muzibukatu ma pointment 😂😂😂 ndie dzakeyo atii ndikukupatsatu 10 minutes ndikuonera😂😂😂😂😂
Koma ching'axy eti😂😂💔
Kkkkkkk satanayo ndi balé wa hilco hahaha , ndimakufilani ku kumozambiki
😂😂😂😂😂😂 Ching'axy ndi one
kkkkkkkkkkk koma yeeeeeeeh apa wabwera hilco ndi nzako ching'axy
Satana amatha kukhara Nanu pafupi Koma inu simudziwa😂😂😂
I can't stop laughing 😅😅😅!! keep it up guys zangondikumbutsa tizibwezi taku primary school 🤣🤣🤣🤣🤣
Kofusira hilco chibwez wakafusira tchito 😂😂😂😂Kom ching'ax
🥰🥰🥰🥰. Guys keep it up
Ching'axy unaza ndiwe G.O.AT🤣🤣🤣🤣🤣
Tipasa moto bas 😂😂😂😂
Mbambande
Ati God be with you hilco be with me kkkkkkkkk
Kulutsan episode 2 changuchangu Kali bhoo 🎉🎉
Kofusira banja mpaka kulira mwati muloredwa inu😂😂😂😂🙌
Kkkkk ching'axy @ wasiya kucheza ndi alimi
Nyc nyc nyc ili mwala hvy