ZOMWE APANGA A NANKHUMWA-ZA MKATI MWACHIPANI CHOMWE AYAMBITSA

2024 ж. 25 Сәу.
19 774 Рет қаралды

Пікірлер
  • Basitu Navitcha uja wamasuka. Moreeeee fireeeeee! APM voting yaaaaaaanga😋😋😋👍

    @Harlod5566@Harlod556611 күн бұрын
  • Osokoneza uyu,ali ngati chilima,anthu woononga dziko.mozambique.

    @user-yh3dw6qu7z@user-yh3dw6qu7z11 күн бұрын
  • Ngati umalephela kutsutsu ku parliament ungakhale otsogoleli otani iwe muthu opanda chilungamo ngati iweyo panopa tikufuna m, tsogoleli oopa mulungu osati asatana ngati inuyo iyaa mwatitola eti

    @user-eh1mg3ww6d@user-eh1mg3ww6d11 күн бұрын
  • DPP pachiongolero basi wina afune asafune basi❤❤❤❤❤

    @user-uc1pd1tc2x@user-uc1pd1tc2x11 күн бұрын
  • APM my vote❤❤❤❤❤❤❤❤

    @user-uc1pd1tc2x@user-uc1pd1tc2x11 күн бұрын
  • APM my vote

    @user-bf9mj9yb1v@user-bf9mj9yb1v11 күн бұрын
  • A broz anga a Cemeon Phiri ulemu wanu..More fire A Nankhumwa..

    @gesinasutherland9241@gesinasutherland92419 күн бұрын
  • Another Chichewa name for the eagle is mvundula madzi Ngati simukudziwa

    @user-is5dl7np9g@user-is5dl7np9g11 күн бұрын
    • 😂 palibe zomuvotela mwana wachepa

      @user-kd8ce8iw1k@user-kd8ce8iw1k11 күн бұрын
  • Nakhumwa ndiosokoneza kwambili ndipo cholinga chawo ndichokapanga alliance ndi MCP kmbe sangazamphule kanthu,DPP more fire 🔥

    @PeterJanuary-lu3hc@PeterJanuary-lu3hc11 күн бұрын
    • Mmm

      @FatimaKazembe-ot1os@FatimaKazembe-ot1os10 күн бұрын
  • Nankhumwa,chilima, Chakwera,mapwala anu.DPP APM my vote

    @user-ez1kc7zp9m@user-ez1kc7zp9m11 күн бұрын
  • Papah!! mwapoilatu apa😂😂😂

    @AustinChiyembekezo-cx4mz@AustinChiyembekezo-cx4mz11 күн бұрын
  • Nankhumwa mutu wake suukugwira wa balalika 😂😂

    @user-cy7gd1go6y@user-cy7gd1go6y11 күн бұрын
    • 😂😂😂

      @JafferTiles-hp4mu@JafferTiles-hp4mu11 күн бұрын
  • Apm My Vote ❤

    @InnoChabwerah@InnoChabwerah11 күн бұрын
  • Marawi waphweka. 😢😢😢😢

    @LuteSynos@LuteSynos9 күн бұрын
  • Nankhumwa angamuvotere ndani? Kavuwe_vuwe

    @isaaczidana2914@isaaczidana291411 күн бұрын
  • Gulukunyinda uyu galu wangwanayo

    @user-vh9uk1jy7w@user-vh9uk1jy7w11 күн бұрын
  • Zose izi ndikusowa zeru

    @user-rn7wv8ze3v@user-rn7wv8ze3v10 күн бұрын
  • adakali ndi mkhwizi ndi DPP. why choose a name similar to DPP and the colour too. akufuna kusokoneza DPP

    @PatrickNamakhoma-zm6kq@PatrickNamakhoma-zm6kq11 күн бұрын
  • Dpp❤❤❤❤❤

    @user-oq5rg5mz7q@user-oq5rg5mz7q11 күн бұрын
  • Atupele,nankhumwa,joice Banda,ndi peter onsewo azikagawana ma vote kumwera chakwera basi kuyenda mwantendere mpaka 2030 wooo

    @user-gj4li2gc8o@user-gj4li2gc8o9 күн бұрын
  • Wacita bwino kuyambisa cipani thawi yofinyana ncipani inatha Cilima akamudelela koma atayamba anagwedeza dziko

    @NoelMajawa-wi3vv@NoelMajawa-wi3vv11 күн бұрын
  • Logo ngati security company 😂😂😂😂😂

    @ahmedmsume1489@ahmedmsume148911 күн бұрын
  • Kutha kwa a Nankhumwa😂😂😂😂

    @JafferTiles-hp4mu@JafferTiles-hp4mu11 күн бұрын
  • Kungokula muthu opanda zeru mbuzi ya muthu

    @user-yf5vq3dl5u@user-yf5vq3dl5u10 күн бұрын
  • Kkkkkkk nakhumwa kumvesa chisaoni

    @user-rc3ze2oi7u@user-rc3ze2oi7u11 күн бұрын
  • Vote yanga kwa ADAD DPP more fire❤

    @PeterFly-mv2nq@PeterFly-mv2nq11 күн бұрын
  • Apa ndiye waziulula yekha kuti ndi chiomba nkhanga, chimunthu choipa mtima, chodanisa, choombanisa anthu, chamoyo oipa

    @josephchitsulo5882@josephchitsulo588211 күн бұрын
  • Akafunse NDA ya brown mpinganjira big muyende bho Inu ndi chiwomba nkhangadi

    @jamesgama5489@jamesgama548911 күн бұрын
  • Mumachedwa kuti kadeti wa mcp tiyeni tiwonane pa ground

    @user-ud9wl8yg1t@user-ud9wl8yg1t11 күн бұрын
  • hahahahahahaha...koma dzikoli.....kaaya!

    @gabrielben-vj2eb@gabrielben-vj2eb11 күн бұрын
  • Nankhumwa my vote

    @user-gj4li2gc8o@user-gj4li2gc8o9 күн бұрын
  • Anapiye angapulumuke koma 😂😂😂😂😂.Rip nankhumwa

    @user-vl8uw8mc3u@user-vl8uw8mc3u11 күн бұрын
    • 😂😂😂😂 komadi sadya ose

      @user-cp8rz3qs8l@user-cp8rz3qs8l11 күн бұрын
  • Aaaa mutayeni uyoo

    @hanifahmponda8711@hanifahmponda871111 күн бұрын
  • Amp my vote

    @user-xu2ui5em3i@user-xu2ui5em3i7 күн бұрын
  • Aaaa zopusa eti ngati ulendo simukatsegula Manda ku mudzi ndi mwayi

    @user-lz5tl7gn4v@user-lz5tl7gn4v8 күн бұрын
  • Anakhumwa galu kwabas

    @user-pl2lj6mh1z@user-pl2lj6mh1z11 күн бұрын
  • Ine gulu uyu amandibowa bwanji

    @user-pl2lj6mh1z@user-pl2lj6mh1z11 күн бұрын
  • wachamba uyu anguvotere ndani?

    @Johnybegood260@Johnybegood26011 күн бұрын
  • Dpp❤❤

    @ManzuzoMbawa@ManzuzoMbawa10 күн бұрын
  • DPP bomaaaaaa iloooooooo❤❤❤❤❤

    @user-uc1pd1tc2x@user-uc1pd1tc2x11 күн бұрын
  • Basi nankhumwa watha palibe achita nsanje Basi mboleche sangawine malo moti akanagwirizane niazake

    @user-st6bt5vv9c@user-st6bt5vv9c11 күн бұрын
  • Mukumana ndi Chala inu

    @AbuOsman-ts6ef@AbuOsman-ts6ef11 күн бұрын
  • Nankhumwa sangatsogolere dziko la Malawi akudzinyenga chabe

    @user-is5dl7np9g@user-is5dl7np9g11 күн бұрын
  • Nankhumwa zomwe wapanga apazi ñdichimodzimodzi kukasekula babashopu yometa mavuzu ankhumba

    @user-bi6pb5gc8t@user-bi6pb5gc8t11 күн бұрын
  • Iwe ife ndiye tinapita kale kwa Peter ukunama

    @user-oj2jr6kf9c@user-oj2jr6kf9c11 күн бұрын
  • Ziliko ku Malawi eee 😅😅😅

    @trynessmsowoya4187@trynessmsowoya418711 күн бұрын
  • Wachita bwino poti watiuza kale kuti ndi eagle chiomba 😂😂😂😂😂 anankhumwa mukuchepa 😂😂😂😂😂

    @RobertLuka-wy9cl@RobertLuka-wy9cl11 күн бұрын
  • Eggle chimbalame yowopya anthu tose tizadibwa

    @MosesNyasulu-lq9sf@MosesNyasulu-lq9sf11 күн бұрын
  • Kungofuna kuononga nthawi awa Sangakhare president wa Dziko wachulutsa bodza ndikudzikonda yekha

    @user-jn2oc3cn3q@user-jn2oc3cn3q11 күн бұрын
  • Nankhumwa manyaka😅😅😅😅

    @ThoccoBondo-mx7vt@ThoccoBondo-mx7vt11 күн бұрын
  • Wachita bwino kuyambitsa chipani chake nankhumwa limenelo ndiye tsogolo

    @user-qb1ef1xw5d@user-qb1ef1xw5d11 күн бұрын
  • Nankhumwa ayende bwino, kanauluka kanatera.. Anatopetsa kwambiri...

    @eliffagondewe8214@eliffagondewe821411 күн бұрын
  • Nankhumwa akutsatira mapazi a Brown mpinganjira

    @JafferTiles-hp4mu@JafferTiles-hp4mu11 күн бұрын
  • Chitselekwete ichi chomvetsa chison APM woyeeeeeee 1:23

    @NijoWanjah@NijoWanjah11 күн бұрын
  • Chakuba ichi chinakumwa amakhala ngati wa DPP koma ali wa mcp ali ngati chiompha nkhanga chomwecho chimangonyosola nyama kumangotaya osanya kungophera njilu wachabe 😢😢😢😢

    @mussamapira801@mussamapira80111 күн бұрын
  • 😅 President wanji opanda ma looks

    @wangachindeya8577@wangachindeya857711 күн бұрын
  • Chiomba nkhanga too much eating beware Malawi kkkj

    @zondanitzulumusicfly.5202@zondanitzulumusicfly.520210 күн бұрын
  • Hot 265 we love you

    @samsonmtumbati4855@samsonmtumbati485511 күн бұрын
    • Zikomo Kwambiri bwana🙏🙏

      @hot265.@hot265.11 күн бұрын
  • Ndizo mphavu aliyense alindifulu kuyambitss chipani Ngati akukhala mopatikizika

    @JuliusSikanawawe@JuliusSikanawawe11 күн бұрын
  • Angozitu mcp undercover zimatheka bwanji anthu anzeru zawo kugulitsa ufulu wao chifukwa cha ndalama a Yudasi we see u throw

    @FosterChilumba@FosterChilumba10 күн бұрын
  • Koma kummwera anthu akuvutikaa kukakomzesa ma ID and akubwezedwaa so malamulo alibe ntcito

    @ElliotOrban-th3qn@ElliotOrban-th3qn11 күн бұрын
  • Chiselekwete chamunthu ichi compensation chison DPP ,APM woyeeeeeeeeeeeeeee

    @NijoWanjah@NijoWanjah11 күн бұрын
  • Galu iwe ukapange ndi akubanja ako dza choomba nkhanga zakozo mbudzi

    @hopembendela@hopembendela11 күн бұрын
  • mmm koma agalu awa amatiyesa agalu

    @KELVINIDENESS@KELVINIDENESS11 күн бұрын
  • Apa ndiye mwatiojeza mpaka kungwetsa passport ayi zikomo achakwera

    @SullyBartsony@SullyBartsony11 күн бұрын
  • Apm my vote

    @JustfiedProperties@JustfiedProperties11 күн бұрын
  • Wayambisa chipani koma palibe chomwe akuziwa mbuzi ya muthu imeneyi

    @user-yf5vq3dl5u@user-yf5vq3dl5u10 күн бұрын
  • zitsiru za anthu nakhumwa nkhope mutu ngati phwala

    @JafaliAkimu-ll1bf@JafaliAkimu-ll1bf10 күн бұрын
  • MUKAMATI msogoleli WA CHIPANI chotsutsa Boma.chipani chake chiti

    @PrinceThom-pe6ie@PrinceThom-pe6ie11 күн бұрын
  • tikakumana kuseu komweo

    @mathewssiliya574@mathewssiliya5748 күн бұрын
  • DPP my vote Nankhumwa kagwere

    @DONNEXKhama-bk1gy@DONNEXKhama-bk1gy11 күн бұрын
  • Kuyambisa chipani chako wachita bwino koma zomwe mwaonesa akulu kosusa tilibe chikhulupiliro painu munkangopanga zamimba yanu osati zaanthu ife president wathu ndi bon kalindo waanthu amphawi.

    @user-vl5on2lj8b@user-vl5on2lj8b11 күн бұрын
  • Kusowa zochita osamakangotsegula Ku Manda bwanji

    @user-qj3db4lu7c@user-qj3db4lu7c11 күн бұрын
  • Pano timveno akhothi ati chani uyu ndiye wayamba chipani chake ,tikungokuonanitu

    @alexsumani6823@alexsumani682311 күн бұрын
  • a mec inu ndiinunso zitsiru

    @JafaliAkimu-ll1bf@JafaliAkimu-ll1bf10 күн бұрын
  • Sangawine😅

    @user-hu6fd8yi7x@user-hu6fd8yi7x10 күн бұрын
  • Munthu walephela kusutsa monga iye wa opposition leader mcp kudusa moyela sangakwanise kulamula boma

    @AndrewBwanali@AndrewBwanali11 күн бұрын
  • Kaya zanu izo zivotani muzivutika Nokha ine kuno ku joni niripheee nikudya chicken deyire

    @user-gs7wc3nx3q@user-gs7wc3nx3q9 күн бұрын
  • Hot 265 umakwana

    @ManzuzoMbawa@ManzuzoMbawa10 күн бұрын
  • Mumthu osokoneza ngati iyeyu mkumayambitsa chipani kuti zimveke bwanji ? Adad sanalakwitse kumutulutsa ku DPP

    @FatimaUlanda@FatimaUlanda6 күн бұрын
  • Chilima president and nankhumwa vice president.

    @Emmanuelngona8751@Emmanuelngona875111 күн бұрын
  • Forming personal parties is not a solution to our development please avoid forming family parties

    @BenBotolo@BenBotolo9 күн бұрын
  • DPP Boma 2025😂😂😂 nakhumwa ndi gawo

    @FatimaKazembe-ot1os@FatimaKazembe-ot1os10 күн бұрын
  • 😂😂😂 50+1 ukuwona ngt masewera kkkk😅

    @user-pj7hn2ky5j@user-pj7hn2ky5j11 күн бұрын
  • Or atakhala ndi chizindikiro chofanana ngati dpd sangasokoneze a Malawi, anthu adzaona pomwe pali chimanga osati mbalame wagwa naye ameneyo! APM motoooooo Navicha more fire in Parliament

    @user-uf4db7im7d@user-uf4db7im7d11 күн бұрын
  • Izi ndi zipan zakuba sorry Malawi samalan ndithu

    @user-xm3zl5cg6x@user-xm3zl5cg6x11 күн бұрын
  • Anakhumwawotu Kaya awonesa zichani zake zimenezo iyeo sangakhaleso president ngakhale patavuta motani ndi mp akuluzaso ameneo 😂

    @user-jl6sq3ph1b@user-jl6sq3ph1b11 күн бұрын
  • PDP security forces

    @LandiranJubeck@LandiranJubeck11 күн бұрын
  • Zopanda mchere nakhumwa angakhale president 😂

    @user-be3is8rc4r@user-be3is8rc4r11 күн бұрын
    • Eti-eti-eti???

      @gabrielben-vj2eb@gabrielben-vj2eb11 күн бұрын
    • Nakhumwa yemweyo 2025 more fire

      @CyprianoSandalamu@CyprianoSandalamu11 күн бұрын
  • Nankhumwa yomweyo kuli wawawa zili bwino zipani zose anachita kuyambisa adpp analibe ndi mp yemwe inu pitilini ndi ufulu wanu

    @user-pt8wb4vw6r@user-pt8wb4vw6r11 күн бұрын
  • Watha uyu basi

    @alexsumani6823@alexsumani682311 күн бұрын
  • Zogwilizanatu izi ndi a mcp akufuna aisokoneze dpp akufuna anthu adzabalalike povota cholinga asadzaipeze 50 1 pasana pawo sizintheka zimenezo

    @EstherPeter-cf1vf@EstherPeter-cf1vf10 күн бұрын
  • He is not 2 late , but he is weak , even he was a leader of opposition he done nothing Zipani zonse ndizadyela , inshort

    @rashidadan2533@rashidadan253311 күн бұрын
  • More fire Dr Namnkhumwa dziko likufuna atsogoleri achinyamata opanda matha kunena za kumtima kwawo this is our next president mufune musafune Dr chilima Dr Namnkhumwa Enock chihana,Atupele muluzi dziko lokomera tonse more 🔥

    @EmercianahKasiku-en6hl@EmercianahKasiku-en6hl11 күн бұрын
  • Zamchere nde zija akumakodzedwa asakudziwa adad ali pa msonkhano zija 85 yrs old Gogo kumamulimbikira kit alamulebe Anthu aulesi inu imilani inuyo lija Gogo lakula mwauponda mumafuna muzizasolora muti adadiwo akugona nfi ukalamba 😅😅😅😅 Eagle waona kale sigwira dpp kutha ngati makatani 😢

    @EmercianahKasiku-en6hl@EmercianahKasiku-en6hl11 күн бұрын
  • koma Malawi muntu wa 80 years akapanga chiyani

    @lazaruschitsamba8394@lazaruschitsamba839411 күн бұрын
    • Ndie omwe sanafike Kuma 80 wa akuchita chani after kulumikizana zipani 9 komabe zakanika kufikira zomwe wa 80 yo anazifikira 😂. Mulungu akutiphunzitsa kulemekeza achikulire ,adadziwa kuti wachikulire amakhala ndimaganizo okhwima ndichifukwanso afikira zaka 80

      @duncainjimmy@duncainjimmy11 күн бұрын
  • Mbuzi ya mano pansi Nan'khumwa..Zaka 4 ukungololera kuti boma lizizunza a Malawi bola iwe ukumatsidwa zammanja , Ndiyeno do you think kuti ndindani yemwe angakhulupilire iwe.. Musapusitse an'thu apa , Amalawi akutulukirani mapulani anu wonse ,Iwe Galu Nankhumwa pamodzi Gwape Frank Tumpale Mwenefumbo", Nonsenu ndinu a MCP up to now, Achayini akenu mukuti kuchalira kuyisokonedza Dpp mu 2025 election .. Mmm mwawuponda .Amalawi 2025 akukasamutsa Mbava zonse zomwe zili ku State House , Ndipo tikukayikako APM ..Even muzabele nkulengezanso kuti Chakwera wawina" Koma Amalawi sadzalora inu kuti muwazunzenso ×2 .Apono ndiye tidzagendanano zogendana basi

    @mkhulukinyata5198@mkhulukinyata51989 күн бұрын
  • Nankhumwa chifukwa amayenda ndi mcp zeru walibe chifukwa dpd ndi dpp mukuona pali kusiyana then blue kala chimozimozi ndi dpp.chipanicho abwereso kukapanga bwino bwanji nankhumwa akulimbana ndi dpp

    @thulanimpphiri6873@thulanimpphiri687311 күн бұрын
  • APM my vote

    @IdrisssJabu@IdrisssJabu10 күн бұрын
  • APM my vote

    @ChrisEnos-to5uv@ChrisEnos-to5uv11 күн бұрын
KZhead