Anthu omwe ali ndi kuthekera kozawina u President Chaka cha mawa

2024 ж. 30 Нау.
42 627 Рет қаралды

#malawi #trending #politics

Пікірлер
  • Kungowina chakwera I'm going to extend my stay in South Africa because there's nothing I see in chakwera's leadership

    @mayesojameskatete@mayesojameskateteАй бұрын
  • Bushiri amathandiza ndizolinga za kumidima. Chifukwa Bushiri zake zonse zimene akuchita ku Malawi ndi zakumidima ndichifukwa chake anathawa ku South Africa ndi mbava ogwilira

    @user-yx6oo2pc3r@user-yx6oo2pc3rАй бұрын
  • Komaso akulu inu munasowa zolankhula et?

    @JamesLinno-ec1zq@JamesLinno-ec1zqАй бұрын
  • Sukuziwa chomwe ukuyankhula iwe mbuz.

    @YunusVima-ce8yk@YunusVima-ce8ykАй бұрын
  • Or atapanga kampeni munthu amenewamvakuwawa zakatadusazi sangavotele chakwera

    @user-ln3zx6wo4w@user-ln3zx6wo4wАй бұрын
  • Chakwera kuwina ndekut wabela mavoti

    @ronaldflitwick3383@ronaldflitwick3383Ай бұрын
  • Iweyo mavita ulindi khunyu ukudwala

    @ronaldflitwick3383@ronaldflitwick3383Ай бұрын
  • Mwasowa chokamba inu aaa komatu musamale ndindalama mukulandilazo plz amalawi siopusa

    @paulmanyamba5437@paulmanyamba5437Ай бұрын
  • Gwape wachabe chabe ndimangot uyankhula zamzeru watumidwa eti

    @Evancemdoka@EvancemdokaАй бұрын
  • Mboliyako kape u don't know what u say

    @juniortsegula3847@juniortsegula3847Ай бұрын
  • Akulu inu kuganiza kwakuvutani mwanyika koopsa Anga umadya chachikulu kumaona Momwe dziko anthu zokhumba zawo

    @user-xn9ov2fn4i@user-xn9ov2fn4iАй бұрын
  • Are u in malawi or not

    @DanielXzelera-op6tx@DanielXzelera-op6txАй бұрын
  • Am sure unafulumira kubwera poyera usanagakhonzeke ukayambirenso sizikumveka bushiri si wandale chikoneni ñdi osaziwika ukumudziwa ndi iweyo ndiponso iweyo ukungochula onse andale kusonyeza siukudziwa chimene ukukamba mwina unapengapo some time back wangonditayisa nthawi kumangobwaza basi😅😅😅😅😅

    @user-rl5zq1qr4d@user-rl5zq1qr4dАй бұрын
  • Ma program ako amandinyasa ase

    @user-nm7pv4bs2y@user-nm7pv4bs2yАй бұрын
  • Ameneyu mutuwake sugwila

    @LenardKayisi@LenardKayisiАй бұрын
  • Amalankhula zaziiii ameneyu

    @user-hr2cg3ku1l@user-hr2cg3ku1lАй бұрын
  • Ndawi zina umayakhura bwino koma iweyoso ndichisiru

    @user-pf6qw3pv9s@user-pf6qw3pv9sАй бұрын
  • Man mukasowa zochita muzipita ku chimbuzi kokanya kusiyana ndizoopusazi mukunenadzi mwanvaa

    @user-yt8qn1uv3d@user-yt8qn1uv3dАй бұрын
  • Pachakwela yekha ndiye wapala ayise komaso nakhumwa wapala uchosepo awiliwo ndipo uyikepo atupele muluzi

    @GEORGE-yr7nx@GEORGE-yr7nxАй бұрын
  • Koma iwe ukuyakhula we ndkape kwambili mbuz yamunthu wangobwelesa no sense

    @user-dk6yc8pl2m@user-dk6yc8pl2mАй бұрын
  • Musamukakamize bushiri musiyeni achite ntchito ya mulungu osati ndale musapusitse amalawi kawiri palibe kukhulupilila chilimanso atinamiza kwambiri

    @user-ee6be5kl5o@user-ee6be5kl5oАй бұрын
  • Iweyo nde waboza basi

    @JerryChain-cz8ru@JerryChain-cz8ruАй бұрын
  • Manyi ako mbolo yosadulayo

    @RobertLuka-wy9cl@RobertLuka-wy9clАй бұрын
  • Chamba eti akutuma eti

    @mclorydamiano@mclorydamianoАй бұрын
  • Ndiwe nkhumba

    @user-pl8kw3dc9d@user-pl8kw3dc9dАй бұрын
  • Tanenani zaurosi mbuzi iwe

    @user-pl8kw3dc9d@user-pl8kw3dc9dАй бұрын
  • Takukhululukirani akulu

    @user-cs4ud8wd5f@user-cs4ud8wd5fАй бұрын
  • Zamanyi

    @user-nj3gn5xq2s@user-nj3gn5xq2sАй бұрын
  • Mbuzi yamunthu

    @user-ky4we4nu2v@user-ky4we4nu2vАй бұрын
  • Wanyopola ndlama iwe galu iwe sumatha kulankhula nyapapi iwe

    @user-yd3zw7ye5u@user-yd3zw7ye5uАй бұрын
  • Aliyense angayimire alindi mwayi owina. They risk of being chosen...and the probability effects. Thats how they work. So their is no analysis here...

    @mzeewandembonyirongo2972@mzeewandembonyirongo2972Ай бұрын
  • Iwe ndi galu kwabasi

    @user-in8of6mu1f@user-in8of6mu1fАй бұрын
  • Chikhomeni ali nfundo ndimayesa nkhani ya chamba imene avomeleza aphungu week yathayi anabweletsa ndi Las Chikhomeni masiku ambuyomo. Which means this guy he is a clever guy and i support him Chikhomeni

    @user-yx6oo2pc3r@user-yx6oo2pc3rАй бұрын
  • Zopanda umboni izoo

    @aaronbagatelle4529@aaronbagatelle4529Ай бұрын
  • Wadya chamba chowawa kwambiri uzawuza makolo ako

    @user-ud9wl8yg1t@user-ud9wl8yg1tАй бұрын
  • Wakhuta nyawu iwe

    @lymonmanda-cd8ol@lymonmanda-cd8olАй бұрын
  • Ndiwe mbuzi ya munthu

    @user-wr4rb1pt4c@user-wr4rb1pt4cАй бұрын
  • Ndaona ulindimisala

    @FrancisStima-sc7zs@FrancisStima-sc7zsАй бұрын
  • Bushiri akulephera kuyima coz ali mbali imodzi ndi Chakwera so come 2025 if akufuna kulowa ndale he will be a running mate of Dr Lazarus Chakwera

    @honourablemcgregorysc97tv@honourablemcgregorysc97tvАй бұрын
  • Aaaaa iwe ndi galu eti

    @daltonkapalamula7931@daltonkapalamula7931Ай бұрын
  • Abambo inu ndiopoira bwanji mmmmmmmm😂😂😂

    @user-uc1pd1tc2x@user-uc1pd1tc2xАй бұрын
  • Panyapako

    @JosephNkhoma-bo9ce@JosephNkhoma-bo9ceАй бұрын
  • Kumpheto Kwa akazako iwe

    @kennethkaunda3636@kennethkaunda3636Ай бұрын
  • What does you smoke mate????

    @user-uc1pd1tc2x@user-uc1pd1tc2xАй бұрын
  • Kkk koma ngati wadya chamba ngati supenga ndi mwayi ndithu

    @thomluciouss7360@thomluciouss7360Ай бұрын
  • Malume zisiyeni basi palibe zikuveka

    @carenchikwe268@carenchikwe268Ай бұрын
  • Ndewamaliza onse mesa nde opanda kuthekela ndiyati popeza makandidet onse chitsilu iwe

    @KasuMustafa@KasuMustafaАй бұрын
  • Ngati kuli channel yachimidzi ndiye ndi iyiyi guys let's un follow this galu

    @giftchale672@giftchale672Ай бұрын
  • Peter is our grand father so how

    @ChikondiChauluka@ChikondiChaulukaАй бұрын
  • Bwana Sam Nankhomwa yekhayo mchotsenipo, Malawi adapenya lelo and Nankhomwa wathandizila mavutu ndziko muno. Timakunyadilani

    @user-bu7ut2gb7o@user-bu7ut2gb7oАй бұрын
  • Ànalysis yanu ndiyabodza, chisankho sawina anthu Ambiri, amawina ndi modzi, ndiye mutitchulire Munthu mmodziyo ngati mukumudziwa.

    @user-nc2yo7rt7z@user-nc2yo7rt7zАй бұрын
  • Zaziii ndiwe wa MCP number 1 ndi Peter basi enawa ndi manyaka

    @LovelyBlini-cu3iu@LovelyBlini-cu3iuАй бұрын
  • Iwe choka mbuzi iwe palibe chomwe ukunena chomveka

    @user-hy6gc6ld9w@user-hy6gc6ld9wАй бұрын
  • Chakwera Ngati angazawine ndiye Kuti wa Bela Koma kwa chilungamo sangawine

    @ElizaMalaya-nv6gl@ElizaMalaya-nv6glАй бұрын
  • Las Chikomeni yemweyooooo! Nfundo zake ndizolondola, chamba ndi gold. Yili mu manfeto yake.

    @user-pv9uk6sc3w@user-pv9uk6sc3wАй бұрын
  • Boza

    @osmanwanja3733@osmanwanja3733Ай бұрын
  • I don't think Chakwera is capable to win in 2025

    @frankielikangala1569@frankielikangala15698 күн бұрын
  • Bushiri ,mr brown mpingamjira mayi joyce banda ndi omwe angathe kulamula dxikoli

    @CharlesMulikhiwa@CharlesMulikhiwa6 күн бұрын
  • Kodi anthuwo sakuziwa kuti bushiri akuziwana ndi chakwela ndiye pamene akuthandiza anthu akuthandizira chakwelayo.ndiyeno muziziyamba dala

    @user-rv8gi4ro6r@user-rv8gi4ro6rАй бұрын
  • Muziyamba mwamina Kaye forsake iwe galu machende ako

    @MuhammadSamson-yz1kl@MuhammadSamson-yz1klАй бұрын
  • Chikomeni n Nankhumwa n Joice Banda mmmm no way

    @Alomwe@AlomweАй бұрын
  • Kd inu mumadya chamba yeti pano musamabweresi nkhani zopusa pano

    @usumanidaudi@usumanidaudiАй бұрын
  • 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 mpaka ndani ????????

    @mollymasangano473@mollymasangano4739 күн бұрын
  • Wachamba angàlamulire dziko monga ukunenelamo osamaseweretsa upulezidenti

    @user-ee6be5kl5o@user-ee6be5kl5oАй бұрын
  • Iweyo ndichipwisi chamunthu ndithu or kaye kunya mau

    @user-rk5ye2tv9z@user-rk5ye2tv9zАй бұрын
  • Kkkkkk iwe akupasa chani mbava yakoyo ichotsepo imozdiyo

    @user-dp6tz3pn1b@user-dp6tz3pn1bАй бұрын
  • Wandithela bundle yanga Kaya watumidwa

    @user-gw4dt9hq9l@user-gw4dt9hq9lАй бұрын
  • DPP under Peter Mutharika ndamene angawine osati manyaka awawa

    @mannietwea@mannietwea26 күн бұрын
  • Zobowa zikuyakhulidwa apa 😮

    @user-oq5rg5mz7q@user-oq5rg5mz7qАй бұрын
  • Ndaononga data yanganso apa eisheee, maphwala ako galu iwe

    @user-on5qq9tg1y@user-on5qq9tg1yАй бұрын
  • Chilima sakulolendwa kuyimanso pa chisakho, Watikwana Chilima akapume wakhalapo matemu awiri it's enough now Kuphatikizapo Chakwera sakufunikanso pamalawi adzikapanga zawubusa zake adzipita

    @user-jd9yz5hp7y@user-jd9yz5hp7yАй бұрын
  • Chilima sangaime muzifunse Justin Malewezi... Nthawi yake yatha

    @user-jb5yb9wq3y@user-jb5yb9wq3yАй бұрын
  • Chakwera ine voti yanga sangaipeze

    @HopesonMkomaula@HopesonMkomaulaАй бұрын
  • Peter muthalika emwey

    @KhumboSimukonda-li6pe@KhumboSimukonda-li6peАй бұрын
  • Galuuu wanchira iwe

    @NeversonThefuture@NeversonThefutureАй бұрын
  • Maviti anji aliyese ali ndi mwayi wowina za ziiiii

    @edenbelievemseteka5197@edenbelievemseteka5197Ай бұрын
  • Aise pantumbo Pako wamva

    @user-ez1kc7zp9m@user-ez1kc7zp9mАй бұрын
  • Nde aliyese ali ndi mwayi kuthandauza kuti chan? Chamba eti

    @edenbelievemseteka5197@edenbelievemseteka5197Ай бұрын
  • Kodi ukamayankhula umakhala wadya nandolo nde umakhala ukulota?? Zaziii kagwere

    @user-qp8kh2hj9o@user-qp8kh2hj9oАй бұрын
  • Awa zokamba zawo sizimaveka ndikuona ngati mutu wake sukoka

    @adamusaidih8570@adamusaidih8570Ай бұрын
  • Kodi amene amakupatsa ndalamayo amati uzitani pomalankhula zopanda mutuzi ndakulankhulanso kokuvuta unayamba yolakwika simbaliyako yolankhulalankhula odontha iwe ukawauze akazi Ako azilankhula angalankhule zanzelu p Palibe owina pamenepo wandithela bandoll😔😔😔

    @chisomochavula@chisomochavulaАй бұрын
  • Akulu inu nkhani zanu zimakhala zofoyiraso bwanji

    @user-rv7tk8cv2q@user-rv7tk8cv2qАй бұрын
  • Mu nkhani zanuzi mulibe za nzeru. Onsewa anayi oyambawa sizingatheke. Bola mwanena za Peter . Enawa ayi

    @user-zs7pn3tv1j@user-zs7pn3tv1jАй бұрын
  • Kodi galu ameneyu akuganiza bwanji tamangopitani ku dimba mudzikalima zoputsa eti

    @md.ruhul-aminmd.ruhul-amin298@md.ruhul-aminmd.ruhul-amin298Ай бұрын
  • This is not prophecy but analysis

    @peterkinsLekera@peterkinsLekera13 күн бұрын
  • Suziwa ndare iwe

    @VincentSibu@VincentSibuАй бұрын
  • Pa chilimapo mwatinamiza man Chilimo tikalowa mmalamulo adzikolino sali ololedwaso kuima us president or vice coz ma term ake 2terms anakwana

    @IsaacChimbalanga@IsaacChimbalangaАй бұрын
  • Utiuzenso olephela chifukwa wanena ozawina chisankho cha 2025😂😂😂😂😂😂😂

    @SandramuMakina@SandramuMakinaАй бұрын
  • Ukumpemph ndan garu

    @user-wb3us4pg4b@user-wb3us4pg4bАй бұрын
  • Uzikhala ndi manyazi popanga zinthu anthutu ndiokwiya

    @user-wh2my2ey3l@user-wh2my2ey3lАй бұрын
  • Iwe kuteleko amakutuma achakwela et Kani ndimakusata ulimbuzi yamuthu

    @FrancisStima-sc7zs@FrancisStima-sc7zsАй бұрын
  • Iwe chimfini usatithere nthawi .Kodi mulibe zochita musadzadzitse mabodza mukusokoneza media anthu akudziwaokha zochita osatikwapusisa zaziii

    @johnman4619@johnman4619Ай бұрын
  • Iwe mbolo yako

    @princenyumwa2550@princenyumwa2550Ай бұрын
  • Iwe galu kwabasi

    @ChimwemweMagombobanda@ChimwemweMagombobandaАй бұрын
  • Nyamako

    @user-ex3tk2wx9p@user-ex3tk2wx9pАй бұрын
  • Awanso ndachitsilu bwanji

    @user-ru8xm6sk2n@user-ru8xm6sk2nАй бұрын
  • Iwe ndi chisilu di eeee

    @SulaimanaIssah@SulaimanaIssahАй бұрын
  • Nfiwe chitsiru kwambiri ok?

    @user-dk4he8zr7m@user-dk4he8zr7mАй бұрын
  • Ngati analuza Kamuzu ndi JB, nde Chakwera nkandani?

    @user-jb5yb9wq3y@user-jb5yb9wq3yАй бұрын
  • Omwe sunawachulewo ndi omwe angawine

    @MasterJailos-kv5sd@MasterJailos-kv5sdАй бұрын
KZhead