Mtambo ndi m'bulundi...and i never expected any good could come from this man...malawians be watchful of such wolves in sheep skins....
@PrinceKachimanga10 күн бұрын
AMalawi ,KUMENYERA ufulu zinathera pa THOM CHAKUFWA CHIHANA, these. Days ndidyera simungamenyere ufulu , freedom fighter asamakhale munthu wadyera ,you can't be freedom fighter. Be wise Malawians ,I hope Mr DC is trying on his side
@user-im7sc2my4w15 күн бұрын
Ngakhale atapepesa is too late nthawi yonsei anali kuti this man betrayed Malawians big time
@user-zg7iw8kq4r15 күн бұрын
I agree with you my brother
@patrickmacheso506215 күн бұрын
APM ndi dilu ❤
@user-zk5nu5fh6l15 күн бұрын
mtambo...dragged MALAWIANS in 2019 from light into darkness.Mtambo is wicked...
@PrinceKachimanga10 күн бұрын
Apepese chani, zoti 2019 ma vote anabera a dpp aaaa chamba eti
@user-nw6ie3xx8b15 күн бұрын
kupepesa kwa Mtambo payambile pobwezela a Peter Munthalika pampando wa u president popeza mtima wa unkhwizi unayambila pammenepa
@dorcasmwale632815 күн бұрын
Anthu adyera awa apa ndiye zaonekera mtambo ndi mbudzi ya munthu.
@chitanibenito110914 күн бұрын
Palibe kupepesa chifukwa cholinga chake ndi choti azitisiya mavuto nde mwamuwona zomwe akupanga wayamba kupangila campaign ena cholinga ayendenso pa nseu Pano a Malawi anachenjera akuwona ngati awapusitsanso akafuna kuyenda kunsewu akatenge ana ake ndi akazi ake
@user-je8jm5uy1q10 күн бұрын
I like this guys
@user-xx3mg2gz5z14 күн бұрын
Sanadye nawo
@LytonMickson15 күн бұрын
Checking and balancing adzifufuza chani? mbulundi ameneyi, nthawi yathakale iyi ngati wasowa chochita kayambe using'anga kwanu.
@jamesgama548915 күн бұрын
Chisilu cha munthu mtambo ndipo ndizoonadi umasuta chamba eti komanso iwe ndi mmalawi kapena waku Drc .....chisilu cha munthu iwe kwambili
@isaaczuze8 күн бұрын
Mtambo olo atadzigwetsa pa mwala pali amwene angamunvele
Mtambo alibe tiyiming ndi fana wadyera akanadekha dziko la Malawi akanalamulirako cz panopa mene zafikira iyeyo akanakhara ali still kumbali ya malawi bwenzi panopa anakangoti inewo ndiyima u president palibe amene anakapikisana naye bwenzi ali president koma panopa a Malawi ambiri tinatuluka Kamba ka kupusa kwake
@PhillipAcquaron14 күн бұрын
Kodi m'malawi ozindikira sangakhulupilire zomwe garu mtambo wayankhula zija
mtambo...mmalo mwa ma demo...tizakupanga ma demo iweyo.Tizakudina😂😂😂😂😂
Mtambo asatinvese mutu ,wathu tilinaye Bon kalindo anachoka kubomako ataona manyi, opanda kuchosedwa
Mtambo ndi m'bulundi...and i never expected any good could come from this man...malawians be watchful of such wolves in sheep skins....
AMalawi ,KUMENYERA ufulu zinathera pa THOM CHAKUFWA CHIHANA, these. Days ndidyera simungamenyere ufulu , freedom fighter asamakhale munthu wadyera ,you can't be freedom fighter. Be wise Malawians ,I hope Mr DC is trying on his side
Ngakhale atapepesa is too late nthawi yonsei anali kuti this man betrayed Malawians big time
I agree with you my brother
APM ndi dilu ❤
mtambo...dragged MALAWIANS in 2019 from light into darkness.Mtambo is wicked...
Apepese chani, zoti 2019 ma vote anabera a dpp aaaa chamba eti
kupepesa kwa Mtambo payambile pobwezela a Peter Munthalika pampando wa u president popeza mtima wa unkhwizi unayambila pammenepa
Anthu adyera awa apa ndiye zaonekera mtambo ndi mbudzi ya munthu.
Palibe kupepesa chifukwa cholinga chake ndi choti azitisiya mavuto nde mwamuwona zomwe akupanga wayamba kupangila campaign ena cholinga ayendenso pa nseu Pano a Malawi anachenjera akuwona ngati awapusitsanso akafuna kuyenda kunsewu akatenge ana ake ndi akazi ake
I like this guys
Sanadye nawo
Checking and balancing adzifufuza chani? mbulundi ameneyi, nthawi yathakale iyi ngati wasowa chochita kayambe using'anga kwanu.
Chisilu cha munthu mtambo ndipo ndizoonadi umasuta chamba eti komanso iwe ndi mmalawi kapena waku Drc .....chisilu cha munthu iwe kwambili
Mtambo olo atadzigwetsa pa mwala pali amwene angamunvele
munthu osokoneza ntambo
Amtumbo ife sitiwalandila olo atapepesa
Apepetse ndipo akati asapepetse aphedwe coz anatiikitsa mumavuto zedi
Mtambo alibe tiyiming ndi fana wadyera akanadekha dziko la Malawi akanalamulirako cz panopa mene zafikira iyeyo akanakhara ali still kumbali ya malawi bwenzi panopa anakangoti inewo ndiyima u president palibe amene anakapikisana naye bwenzi ali president koma panopa a Malawi ambiri tinatuluka Kamba ka kupusa kwake
Kodi m'malawi ozindikira sangakhulupilire zomwe garu mtambo wayankhula zija
Athufe sidzitsilu mtambo tinathana nawe tikuyang'ana kutsogolo
Mtambo machende Ake panopa amalawi akulira ndikukwera kwazinthu chifukwa chambava zimenezi we don't like him anymore no matter angapepese
Eee Malawi wafika kumapeto koma tiyeni tisataye tima panja ana aizarayere anaoloka panyanja adani awo anamira tiyeni tisithe chipani mwadzeru izi zakanika tiyeni tigwirane manja
Inu animes mwana I ineyo kuyambitsa mademo anu
Malawi amuntenga ngati munda wa ambuye ao
Mtambo ndiwabodza
Ntambo ndiwakuruwanda uyu
kuzolowera nkhondo kwawo ku burundi...😂😂😂panya pake
Ntambo game yamuvuta basi amuchosa pa bread 😂😂😂 samuwawa akufuna timuthandizeso mademo ena 😂😂
wamisa mtambo akagone
Mtambo is better than Facebook activists if you think he is wrong get up and act don't just write on social media.
Akufuna chan kape ameneyi...wachedwa kwambir
Tonse alliance.... 🙉🙉 CHIRIMA, GOSPEL KAZAKO, NTAMBO NDI NZAKE, CHAKWELA, MANGANYA, NDI ENAO,,, ndikuyamba kukusalilani kudya kuyambira lelo ndikufuna onsewa awa!!! Mulungu awalange ndithu!!! Ndipo ifeo amalawi tione kuti mulungu wakulangani ndithu
Game yamuvuta wamenya 90 minutes kenakooo aonjezera 5 adziti game simnaione bhooo
Mtambo ngati wasowa zochita dont take malawian ngat zitsiru kwako kunatha kazidya machenji ako basi
Mutavala ma shirts ngati uniform 😂😂
A times nanunso chamaba
Mtambo azikatola masuku kuchitipa kwawo asatisokose
A Malawi akuvutika chifukwa cha mtambo, Timothy mulungu akulange opusa wadyera iwe
Mtambo uzikhala ndi manyazi
NTAMBO NDI CHIGAWENGA CHACHIKULU KU MALAWI KO
Asatinyase ameneyi ndi munthu wamdyela akanati asachosedwe unduna sakanabwela kumayankhula mbwelera zakezo
Apepese ndithu.
kubadwira malawi zovesa chisoni
Mumuone KASAKULA pano, anasinthatu tune, Zoti kuli mavuto anyooo! Ndi Boma ili oposera nthawi ya DPP achita khungu sakuona. Adyeretu 2025,Paulendo.
Mtambo ngakhare atapepesa palibe anga mukhulukukire wakhetsa ndi kuononga miyoyo ya anthu ambiri
Iweeee nkhopeyo uzichotsapo
Amaona ngati a Malawi ndi zitsilu Malawi now is matured political
Timothy wachedwa atalawira 😂😅
Koma Malawi sizatheka guys Kaya tichoka mumavuto Awa Kaya 🤷🤷 tiziwona 2025
The guy in between is smoking too much just like train
Ntambo ndigalu kwambiri panopa wadziwa kuti able akewo zwavuta
Galu wamunthu ameneyu abwelele ku Burund chitsilu
Mtambo wakhala 4 year akabwere pano ayi wachedwa khala pasi pliz mulungu asanakukathe
Ndkape
Frankly speaking Mtambo he's not an activist, all knows ndikudanitsa anthu komanso kuika aMalawi paukapolo.
Mtambo a Malawi si zitsilu kut azingokumvera mbwelera zakozo
Akakolope nyanja shu
Iwe ntambo kangwele uko angakuvele ndindani kape iwe, munthu osokoneza
Malawi dziko langa 😮lipatsa bwanji ufulu foreigner mpaka kumpatsa unduna kuphweketsa dziko
Ndipo mbava imeneyi si yakumalawi kuno
Alibe ntchito ameneyo azingodya bomamo mmesa ankapanga mademo kufuna kudyetsa mimba mwake nde apa asatinamize
Ntambo manyazi alibe ndithu
Apepese ndukubwela ndi thima ose
Amalawi nthawi yoti mtambo atipusitse kawiri tisalolenso atizunzisa ife kwambiri ndi atonse alliance, pomwe nthawi ya muthalika zinthu zinali kuyenda bwino koma mtambo anatilakwitsà kutulitsa Dpp mboma Pano amalawi akufa ndi njala zinthu zaduliratu moti amalawi akumukumbukila peter muthalika 2025 tivotere peter muthalika yomweyo basi kuti atipulumutse mmanja kwa asatanawa
Osangomulola bwanji kuphela komweko nkhumba yachabe chabe
Munthu osokonedza kwambili omwewa ndiyamene ankayenda pansewu kuti dpp sikulamilira bwino tikufuna tisithe boma lero boma linasithidwa ukubwelanso ndi mbwelera zakozo chomwe ukufuna chani ntambo pezani zochita zina musatikwanepo apa malo momwebweraa kuzapesa pazomwe unachita,shame to you Ntambo
Sitikavita
tingodikila kampeni ya Adad
Ngati mmene anachitila born kalindo
Wapanga bwino kutulukila kunja kunu timamulephela chifukwa amayenda mpheto mwanjovu nkwiyo wathu kwameneyi ife siunatithele APA ndipamene atibwezele mashopu athu Aja sopano komanso anaphesa anthu abaleawo sikuti ayiwala tamulandila basi panjapano tiocha kanyenya ameneyu
Enough is enough azikalima galu ameneyo
Omwa tea adzamwanso ntambo zivute zisavute mulungu adzatsegura Pena palibe okhoza pandale olankhula sapeleka Mwai ai Koma mwini kumwamba
True and well said
Ntambo mbolo yake akumgofuna ndalama.
This guy asatiese its too late
Mtambo sangatinamizeso akagwere uko
Anacotsedwa pakulepera kukwaniritsa nchito yake.
Ntambo asatizolowere tinakutuluka kalekale
Uyu ndi chupiti fotseki fotseki
Mumalawi amene ali nzeru panopa waziwa munthu amene angakhale mutsogoleri wathu.kuyambila mtambo chakwela chilima onsewa ndi mbuzi za wanthu muno mumalawi
Ndiposo azimupepesa ndani ife boni kalindo amatikwanila bas
Kalindo anaonesa kukhwima nzelu kuposa amabungwe enawa
Silly guy
Mtambo fotsek zake
Nonsense,,,,, we will never trust you again
I think his out of his mind really the way he was speaking now he come up with nonsense
Bagamoyo avuta
This guyz I don't like him
Chichewa zikanamvekatu
Nes😂
Mtambo Moto... Fire 🔥🔥🔥🔥🔥 mtambo
Amalalawi wopanda nzeru still backing galu president Peter muthalika, racist president Peter muthalika nanga mtambo walakwa chani?
I hate him
Akuona ngati amalawi angamukhulupile never