IZI NDIZIMENE AYAKHA KUCHOKERA KWA ATOLANKHANI

2024 ж. 26 Сәу.
55 066 Рет қаралды

Пікірлер
  • Anthu anakudalilani koma pano tili ndi boni kalindo amatimenyera nkhondo kuposaso iweyo galu iwe shame

    @user-tn2qg1vs9j@user-tn2qg1vs9j18 күн бұрын
    • Zoonad aaaa awa anali kale😅

      @maxwellluciano4943@maxwellluciano494318 күн бұрын
    • Pamenepo 😂

      @GodfreyFavorEliot@GodfreyFavorEliot17 күн бұрын
    • Bon Kalindo said amalawi siowafera

      @ancientnkhata1137@ancientnkhata113715 күн бұрын
    • Mbava siku bweraa zaona chizango

      @user-le9su3mt7r@user-le9su3mt7r14 күн бұрын
  • TIMOTHY MTAMBO PLS STOP TO TAKE THE MALAWIAN'S AS YOU'R COWARDS/DZITSILU ZAKO ...WE ALL KNOWS THAT " AN'THU YINUYO PACHINA CHILICHONSE CHOMWE M'MAPANGA", YOU DO IT FOR YOUR STOMACHS BUT NOT THE CITIZEN'S AT ALL ..Pano ndiye tikukudziwanino agalu yinu bwino lomwe mwinanso kuposa momwe mukuzidziwira achayini akenu . Posafuna kutaya n'thawi mwina ndingonena kuri ; Ma Citizen's m'ngokwiya nanu kwambiri , Ndipo chikhulupiliro chathu mwayinoyo chinafa kuthetatu, Lerolino kukukhulupulirani inuyo bolanso kuwukhulupilira Mkango , Chenjezo ",", Musamale chifukwa ndimomwe yilili mikwiyo ya an'thu pano", Ndiye kuti mukhonza kutheta mmanja mwa anthu

    @mkhulukinyata5198@mkhulukinyata519818 күн бұрын
  • Malawians are wise enough to be fooled by you.😅😅😅

    @tisuhmakhwah7085@tisuhmakhwah708518 күн бұрын
  • Aise ntambo osatenga ngat dzikoli ndilako ayi, amalawi adutsa mavuto azaoneni chifukwa chaiweyo, zimenezo izikauza akubanja kwako

    @user-iw6cz5ft2l@user-iw6cz5ft2l17 күн бұрын
    • that's true bra

      @ThaboKhanye-wp9pm@ThaboKhanye-wp9pm17 күн бұрын
    • Iwe wabodza

      @ancientnkhata1137@ancientnkhata113715 күн бұрын
    • Boza lachani pathako pako serious

      @benjulius6070@benjulius607014 күн бұрын
  • Otumidwa ndi MCP awa kuti alumile kumbuyo pochepesa mavoti a DPP awa. Anthutu akuyiopa DPP osati masewera.Tizipani/ma pressure group onsewa akupanga za Adad basi. MUSAUVER🔥🔥🔥DPP ndi 🔥🔥

    @enockmlanga@enockmlanga18 күн бұрын
    • 0

      @user-mq1jl2rr5j@user-mq1jl2rr5j17 күн бұрын
    • Mcp send you to get more vote😂😂😂😂😂

      @JohnConar-kq4hi@JohnConar-kq4hi17 күн бұрын
    • Ase this time around DPP singawinenso siyani kulota

      @yamikanijames6915@yamikanijames691514 күн бұрын
  • Aaaaaa, chomwe ndatola apa, ndimafunso atolankhani basi. Koma ofunsidwawo palibechomwe ayankha chanzeru. Olomutanfusa .mwana wapabere akuuzani kuti palibechomwe chanveka. Mudaziwotchera cv nokha

    @sayidimisessa@sayidimisessa17 күн бұрын
  • Mtambo machende ako

    @SamukLungu-zg7fl@SamukLungu-zg7fl18 күн бұрын
    • I support your comment with one packet of sugar

      @HAMISI265@HAMISI26517 күн бұрын
    • Zoona big ndi munthu opusa Mtambo

      @sydneyjamu8877@sydneyjamu887717 күн бұрын
    • You have my vote mister

      @festoneGanizani@festoneGanizani17 күн бұрын
  • Mukuona ngati ndife zitsiru..Malawi mwaipangira chani? muzitinyasa..Mwatilira

    @stanleymollen7273@stanleymollen727318 күн бұрын
  • Anakakhala unduna sanawachotse sakanabwera kuzalankhura awa

    @cassimyusuf6683@cassimyusuf668317 күн бұрын
  • And we are not sure if there will be any wise person person who will follow you again during your next film shoot Mr. Drama man😂😂😂😂😂

    @mcsydenynsinga7610@mcsydenynsinga761015 күн бұрын
    • Drama man indeed

      @thoccomapunda@thoccomapunda12 күн бұрын
  • Ife wachilungamo tikudziwa Bon kalindo

    @MaxwellChiwaya-tv7kn@MaxwellChiwaya-tv7kn17 күн бұрын
    • Ndipamene anatuluka chaka choyamba ndi kuyamba kuyakhula

      @raffickchicco2724@raffickchicco27243 күн бұрын
  • NKHUMBA YA MUNTHU IYI HE USED AS A TOILET PAPER 😂🎉😅

    @user-nl5nk2wx1q@user-nl5nk2wx1q17 күн бұрын
  • Munatibweletsera mavuto inu

    @user-gs7qk6lk7z@user-gs7qk6lk7z17 күн бұрын
  • Munali m'bomamo munali ziiii ,pano akuchosan muli nyoo nyoo nyoo mxm

    @HAMISI265@HAMISI26517 күн бұрын
    • GALU kwabas ameneyu mxiuh

      @user-ky4ce9gb6j@user-ky4ce9gb6j15 күн бұрын
    • People u are talking on my behalf kkkk

      @thoccomapunda@thoccomapunda12 күн бұрын
  • Mr m'tambo sitikuksowani or pang'ono kamenyereni ufuru banya ranu osati a marawi apo ayi uzingopemphera kuti mulungu azikukhurulukira chifukwatu ndiye ukuzuzisa athu

    @afrozwayson7482@afrozwayson748217 күн бұрын
  • Peace and unity,,,,,,zauchitsilu! Boni kalindo wakhala akumangidwa pa nkhani za ndale chifukwa chakuti akumenyela ufulu wa anthu osauka iweyo nthawi imeneyo udatani kulimbana ndi boma kut Peace and unity ioneke pomutulutsitsa kalindo yo? Mbava iyi!

    @user-qv4ko6ps4j@user-qv4ko6ps4j17 күн бұрын
  • Udalikut potuluka relo bogolo , you take Malawian for grant 🥸

    @sthoramexjrsa902@sthoramexjrsa90218 күн бұрын
  • Another prophet from down north, much respect comrade

    @TedMlauzi@TedMlauzi11 күн бұрын
  • Comred unatha nsuzi iwe, ife tinakutuluka kale kale pita ukamu joine nankhumwa mukaendese chipani.

    @user-gq1lj6nc8h@user-gq1lj6nc8h17 күн бұрын
  • Mtambo came at a critical point when Malawians have lost interest in him

    @user-mb8ye1ve5w@user-mb8ye1ve5w14 күн бұрын
  • Ameneyu ndi galu kwa bas fit yen yen

    @user-rs5qn4pr7e@user-rs5qn4pr7e17 күн бұрын
  • Uyu pansana pake ndithu

    @user-jf3kv3jl2h@user-jf3kv3jl2h18 күн бұрын
  • From all media stations guys you now how to ask good questions... Congratulations

    @TedMlauzi@TedMlauzi11 күн бұрын
  • Mr mtambo mukuonetsa kuti ndinu mmodzi mwa anthu adyela Kodi mukuyembeza kuti enaso akupatseni ndalama pa msana pa Osaka? Nanga mukuyembeza udindo wotani kwa amene mukwalankhulira lero lino

    @ShakiraRashid-yy2nz@ShakiraRashid-yy2nz17 күн бұрын
  • Ine ndili pano ngati MEC volunteer just check comments & see how much votes do you have ‼️‼️ majority we say No No

    @noahtsamdoka1172@noahtsamdoka117214 күн бұрын
  • Great Kalindo

    @PreciousChilombo-ps2yu@PreciousChilombo-ps2yu17 күн бұрын
  • Akuziona ngati Mlungu ndi mubale wake. Awoo atumidwa asatitayise nthawi. Ntchito yao anagwila kale panopa akudyelela. Bwana kumwamba kuli Mlungu

    @douglaskamanga7679@douglaskamanga767918 күн бұрын
  • Mtambo ndi nyan

    @YusufuUsumani@YusufuUsumani18 күн бұрын
  • Komano muyankha bwanji funso lakumapeto kusiya oyambirila ndiye mukamawelenga mapepalaanuo mukuyambila ku manzele kumapita kumanja ngati ndiwe wachisilamu ndipo palibe chanzeru wayankhula garu iwe

    @user-qi8xe7qh1e@user-qi8xe7qh1e18 күн бұрын
  • Big up!!

    @kubengovender6996@kubengovender699617 күн бұрын
  • Adzakhumudwa 2025 apa nipang,ono adziwe zimenezo amtamboo adafulumira kulowa ndale chakwera ali pa top 1

    @user-px6kt8rx2p@user-px6kt8rx2p12 күн бұрын
  • Mtambo ndiwee galu kwabasii

    @user-vu9rt8gj3o@user-vu9rt8gj3o17 күн бұрын
  • he has senses actually

    @user-km2js5nq9k@user-km2js5nq9k17 күн бұрын
  • Wamupasa chibanzi nadi AAA ukawankhu nyengo yose iyi

    @user-mu5cs9qf7z@user-mu5cs9qf7z17 күн бұрын
  • Kupoto kulibe muthu opanda dzelu ngati Tambo uyu ndikazizi wakumbulundi mafuso achichewa choveka bwino timayakhaso chinyanja chomwecho bwilimakhwe

    @user-xt2gu9yt9q@user-xt2gu9yt9q11 күн бұрын
  • Very pathetic to see somebody who ever lied to us coming again with lies as well inorder to correct our taxes again,may God help him to realize.

    @blessedmichael5124@blessedmichael512411 күн бұрын
  • Credible comrade

    @SamsonMWNgwenya@SamsonMWNgwenya17 күн бұрын
  • Kodi galu mtambo ulipo, ndalama zangokuthera basi usatinyase. Galu iwe unatiyika mavuto bwanji😢

    @jamesgama5489@jamesgama548918 күн бұрын
  • Munthu aliese amakhala ndi nthawi ya uyu ndiimeneija idatha chakwera siyemwe akubweletsa miliri ndi kusintha kwa nyengo mwina adayamba kuledzera a mtambo asatinamizeso

    @user-px6kt8rx2p@user-px6kt8rx2p12 күн бұрын
  • Now i can assume that may be he used to bring forth with some good ideologies for the betterment of malawians but he couldn't penetrate thru.... My thoughts

    @TedMlauzi@TedMlauzi11 күн бұрын
  • Kuyankhula zimenezo chfukwa choti anakuchosa pa udindo mn mzayenda nokha mmusewu

    @GodfreycultureBanda@GodfreycultureBanda14 күн бұрын
  • Ine umandiwaza adha ...umayankhura zanzeru though enake akuzitenga negatively

    @RABSONSIKELO@RABSONSIKELO17 күн бұрын
  • Mwafusidwa chichewa choveka bwino ndiye mukuzayakha English yanu yothoka thoka ndiziti munalowa kalasi kuzikonda bwanji iyaaa

    @cassimsiginala5432@cassimsiginala543217 күн бұрын
  • Palibe chanzelu unganene kwa amalawi ganyu wakanika apapa unagwilisa amalawi fuwa lamoto

    @patrickscott9086@patrickscott908614 күн бұрын
  • Only the dull will follow you. There is nothing you can say to the wise.

    @omarajibu860@omarajibu86017 күн бұрын
  • Timothy unadya Ntambo pano ndiye ukuti chani? Wadyanso sikono apa koma ukubweranso kuzapusisa a Malawi zoba"

    @MadalitsoGama@MadalitsoGama17 күн бұрын
  • Magazi onse a anthu akufa pano chifukwa chaumphawi Ali mmanja mwako and iweyo sudzapeza ntendele chifukwa chachimenechi. Ukanakhala wanzelu ukanangokhala chete.

    @joelkabambe@joelkabambe16 күн бұрын
  • Avala za nkhondo atambowa akuwopyezatu a Malawi akavula za nkhondozi mwina tiva

    @BrazioBauleni-sq9pu@BrazioBauleni-sq9pu10 күн бұрын
  • Following with interest

    @KingstonNgoma@KingstonNgoma15 күн бұрын
  • Kunyasa nkhope ndi mtima omwe Galu iwe kwabas palibe angakusatire iwe pumbwa iwe chimutu ngat......

    @munashemoyo4190@munashemoyo419017 күн бұрын
  • Izi ndiye zopusa izi musatinyatse ife tamangodyani ndalama anakupatsayizo ☹️☹️

    @EstherPeter-cf1vf@EstherPeter-cf1vf17 күн бұрын
  • Musatichedwetse man

    @MphatsoChikatentha-by4nl@MphatsoChikatentha-by4nl18 күн бұрын
    • Truly. Asatichedwetse galuyu.

      @macrinenduna1024@macrinenduna102417 күн бұрын
  • Aaaaaaaah man finish ni finish mkwayi😂😂😂😂😂

    @chikondigondwe4669@chikondigondwe466918 күн бұрын
  • Ine ndikumanena kuti zisilu zomwe zinapangisa kut anthu afe, ndi amanewa mpaka Pano amalawi akulilabe, anthu ake ndi amenewa.. ziyanthu zoila.. nzopanda pake or tikambilane za achina ntambo sizitithandiza.. tiyen ku 2025.. basi

    @MikeMalinga-xx8ys@MikeMalinga-xx8ys18 күн бұрын
  • Ichi nchigalu ichi mwalodzedwa kale ndizima bangili zanuzo

    @robertkipapa1709@robertkipapa170913 күн бұрын
  • Koma inu kuyima u president muzawina tayimani big man

    @user-vx6sv5wi1b@user-vx6sv5wi1b17 күн бұрын
  • Piease try to be answering the questions in chichewa for the whole of us as Malawi

    @roseemirymanda4083@roseemirymanda408317 күн бұрын
  • I phoned you Timothy mtambo, but upon realising that you were being recorded you dropped the call, conviction can't come in the fourth year

    @amoschisisi2070@amoschisisi207017 күн бұрын
  • Uyu ndi m'bulundi weniwenidi ndithu Tangomumvelani chichewa chikumuvutatu uyu....

    @MabvutoMwakalinga-yl3ft@MabvutoMwakalinga-yl3ft16 күн бұрын
  • Aidziwatu democracy mtambo kuti anthu saganiza mofababa

    @user-px6kt8rx2p@user-px6kt8rx2p12 күн бұрын
  • Mwabweranso kuzalipanga support boma kkkkk Komatsu mtambo

    @user-im4tc9qi4j@user-im4tc9qi4j15 күн бұрын
  • This led Malawian to this poverty and hard times.

    @mavutotizora-yz3yn@mavutotizora-yz3yn18 күн бұрын
    • This guy is as evil as msikidzi...who he think he is? Chimunthu choipa chazunzitsa amalawi ....all what is saying is shit ..listen to the way is answering muona kuti ndi munthu opusa mphenvu yeniyeni.....Ada awa will be responsible for all what we are facing now...if not us showing him then there is God who can definitely do that for our sake

      @sjrecordschannel7687@sjrecordschannel768716 күн бұрын
  • Aaaaaa iwe usatitengere kokatiyetsa ukuwona ngati a Malawi ndizitsilu

    @CholapitsaSamson@CholapitsaSamson17 күн бұрын
  • Antambo unatichotsa kwabwinobwino kutitengela kuyipa muti chan

    @ShadreckMalemba@ShadreckMalemba17 күн бұрын
  • iyi ndiye mbudzi yazaoneni

    @jemasmasimbi8109@jemasmasimbi810916 күн бұрын
  • Ntambo palibe chomwe anfanene ndipo sitikunfunanso ife Amalawi azipita uku

    @user-je8jm5uy1q@user-je8jm5uy1q13 күн бұрын
  • kodi kusukululko umaphuzila ndale basi kukamwa kobowoka

    @harrisonkwenyengwe9671@harrisonkwenyengwe967115 күн бұрын
  • Chakwera walowesa usiwa owawa kwambiri mmalawi ife amalwawi timadya chokudya chapasiku

    @user-pl8kw3dc9d@user-pl8kw3dc9d12 күн бұрын
  • Mcp izalamulila ngati chipani cha ku south africa

    @AgnesAkika@AgnesAkika17 күн бұрын
  • mwina wasiya china chake ku mademo akufuna akachitenge iyeyo akuganiza kuti akhalaso ndi molalo pansana pake zake zinapita basi azidya ndalama zona analandila pa u minister

    @ChundaLackson@ChundaLackson15 күн бұрын
  • Atuma ngati mene amutumila Joyce banda wakuba ameneya

    @YohanePatrick-lc2lq@YohanePatrick-lc2lq17 күн бұрын
  • komanso atolankhaniwo mwawayitanisa nonkha nde muwayankhe mwanzelu.

    @ottisoyezer7160@ottisoyezer716017 күн бұрын
  • Waziwa liti kuti zithu zavuta sindiwe unatingera sitingakukhulupirire iweyo

    @user-st6bt5vv9c@user-st6bt5vv9c17 күн бұрын
  • aaaaa😂😂😂😂 ichi ndiye chani wabwela ndiwe galu

    @user-vw4vc9xd5z@user-vw4vc9xd5z17 күн бұрын
  • Mbuz iyi he he fooled malawi for the past 3 yrs pano ndkumabwelaso koma kumutsatilaso ameneyi ndkutaya thawi adzayende yekha ulendo uno

    @RobertDJambo@RobertDJambo15 күн бұрын
  • Mtima wako mtambo mngwa dyera.🤸🤸

    @user-ku5fs6lv4n@user-ku5fs6lv4n15 күн бұрын
  • Ndimbava ameneyo 😂😂

    @yohanebotso@yohanebotso15 күн бұрын
  • Ukuyambe kunyumba kwanu how many month remaining for elections

    @CastenkWhite-fr4ne@CastenkWhite-fr4ne17 күн бұрын
  • Asatitenge ngati ndife makape uyu akagwere ukooo😂

    @LeonardMhone-cg1tk@LeonardMhone-cg1tk17 күн бұрын
  • Funso kwa CIC., Kodi nchifukw ninji.anawachotsa unduna ngati amatha?

    @eleckchimpanzi2124@eleckchimpanzi212415 күн бұрын
  • Uyu ndi ngalu wakumba asakunamizeni Amalawi apa akufuna kukuamizaninso Amalawi

    @user-jd9yz5hp7y@user-jd9yz5hp7y17 күн бұрын
  • Mr Timothy mmmmmmmmm Ayi Sana

    @AmandaConstance-fx8cr@AmandaConstance-fx8cr17 күн бұрын
  • kodi ukuona ngat ife ndiopusa kape iwe ndipo ngat ndikuyenda pamsewu uyenda wekha ndi banja lako unatigwetsera kumavuto galu iwe mutu oumawo shupit

    @EreneoMchenga-ly5vq@EreneoMchenga-ly5vq14 күн бұрын
  • Munthu oipa iwe ukuphesa anthu tilibe nawe function

    @EliousImedi-kd7nf@EliousImedi-kd7nf17 күн бұрын
  • Ndipo tchende lanu akulu ndiwe opweteketsa mtima kwina kwambiri

    @lameckfedson7647@lameckfedson764713 күн бұрын
  • kodi mufuna muzi atengati atora nkhaniwo chizungu samatha mesa mafusowo akukufusani muchichewa inu mukuyankha chizungu bwanji galu iwe mtambo

    @user-nz9ty3ih1v@user-nz9ty3ih1v17 күн бұрын
  • Unakafuna kulankhula chidzungu unakaitana atolankhani achizungu galu iwe

    @user-ub9on7oj7l@user-ub9on7oj7l17 күн бұрын
  • Lost relevance long ago, you can full the people once but you can fool the people all the time

    @chesterphiri7523@chesterphiri752317 күн бұрын
  • Munali kuti inu mwaona kuti mwaonongetsa kale dzikoli, mukuona ngati malawi uja wa 2019 mumkamuyendetsa kuti palowe agulu ulumawa sichoncho, ambuye akuoneni

    @MisheckAselo@MisheckAselo16 күн бұрын
  • Antambo tinatopananu boza two much asaziwa ndani kuti ndinu aboma

    @KinosiKameta-ud1ps@KinosiKameta-ud1ps16 күн бұрын
  • Mr ntambo if Malawian are thinking like an robot mean that your a biggest robot in malawi for being quite since tonse alayansi take the government....because so many things happen and you as a one of freedom fighter,citizen you keep quiet, where have been ? Now you come back while time is over for what?

    @RhoydNyandule-qr2ug@RhoydNyandule-qr2ug16 күн бұрын
  • Mayankhidwe awuyu mtambo sizinanveke bwino afuna atipusise pa mafunso onse sanayankhe monveka kuoneseratu kt ndi wa MCP sanayankhe funso Lina lokhunza zipani. Funso loti mulayimira chipani chit?

    @SmilingFishingRod-zc4wx@SmilingFishingRod-zc4wx16 күн бұрын
  • Mbuzi iyi

    @WisdomMsuku@WisdomMsuku15 күн бұрын
  • Ngisunayambe utsayambeso tsiyaya machendako

    @YohanePatrick-lc2lq@YohanePatrick-lc2lq17 күн бұрын
  • Atambo Pano sakudziwa zomwe akuchita awaa

    @BrazioBauleni-sq9pu@BrazioBauleni-sq9pu10 күн бұрын
  • Nzeru alibe uyuu iyaaa😊

    @BatsonKadzuwa-tl3rp@BatsonKadzuwa-tl3rp17 күн бұрын
  • heaven my foot...

    @rasulmaulidi2224@rasulmaulidi222417 күн бұрын
  • Ndipo atambo mulungu akuwoneni chomwe mumapaga simumaziwa koma

    @0betPhiri-mp8kq@0betPhiri-mp8kq14 күн бұрын
  • Chilango chilipo, ndipo chili pansi pompano muwerudzidwa pompano sure. God is watching everything.

    @user-jw5rx9ze8k@user-jw5rx9ze8k17 күн бұрын
  • Wawusilu uyu anthu ena amangidwapo chifukwa Cha ma demonstration koma iye kungikhala chete kumangowinelela osayankhula khandu koma akuti iyeyi ndi omenyela ufulu anthu sono now akufuna kufutfuta zibalima kuti anthu amukondeso Winiko wangidwa kambili mbili koma sanayankhulepo khandu koma Winiko amamangidwa chifukwa chowafunila anthu za bwino lelo akufuna kupusisa anthu powona kuti nthawi ya ma vote ikubwela ndi pomwe akubwela poyela uyu ndi Galu kwambili chikulupililo pa Atambo anthu anasiya kale. Chomwe ndiyankhule pano Amtambo muve anthu ovutikafe siyife makasu anu oti mukalima kukolola munayiwalaso makasuwo ndiye ife zotipepelesa tatopa nadzo koma ulendo wina dziko lizakutembenukilani agalu inu

    @user-dn3gp6yi4y@user-dn3gp6yi4y17 күн бұрын
KZhead