Mr Jokes "WACHAKE COMEDY SERIES" episode 6 (Full Video)MR JOKES2024 ж. 21 Нау.134 249 Рет қаралды Share Tweet Жүктеу
Even ma Surname ake, Ngoziyankhuku eti🤣🤣🤣🤣
Zili bwino guys, Mumakwana Watching from RSA in Cape Town, Big up 💯👏👌🙏🙏🙏!!!
Ooh yes timalakwitsa kusangalatsa gulu wina mkumajaila kuti imfa ndiimene idzatilekanitse
😂😂😂 uyu ndiovuta kulera Jokes
Yonse ndi minda kkkk kukana kuvomeleza kulakwisa😅 abusa
Undimenyaaa? Uziti timenyana😂😂😂🙌ching'aning'ani adha
By then how are you 😂😂😂, Mr Jokes mwaitha nkaz uja Ali ndi mimba yamwini😂
Osati undimenya kumati timenyedwa hahahahah Ching'asy
Jokes am happy for you That spirit of asking zamavuto and matenda paukwati zikuyenela zitheka ma church
Kkkk abusa nawonso m'munda wa getsemani
Yosee ndi Minda🤣😂🤣🙌🙌
😝😝 koma mr jokes iwee anakoza kungochoka zako atakomoka
Yose ndi minda😂😂😂
Mayina akewo , ngoziyankhuku ,😂😂
Osadandaula muzivala ife tilipompano 😂😂😂😂😂😂❤❤❤❤❤
Live from krugersdorp town Jozi...iwe umath basi❤
Ineyo mavuto anandikwana kwambiri 😂😂
Iye mavuto sakuwafuna akufuna mtendere okhaokha
Kkkk😅😅 jokes wanditopetsa😊😊😊
😂😂😂mkaz muzamuwon tsik la ukwati ndikakuuzan mukumanditambila😂😂
Coming from fb
Makwana mr
Painful truth from Mr Jokes. I like that
Watching from mwineriwa vg mulanje
Yonse ndi minda kumene 😂😂
😂😂😂Abusa awawa
Eeee koma yah🤣🤣🤣🤣🤣🤣
🤣🤣🤣🤣🤣udziti timenyedwa
By then how are you,🥺🤣
Pamene ndingatopere 😂😂😂
I'm here for Mr jokes and Ching'aning'ani
Atiii yonse ndi minda ah😂💔🚶ukwati uwuwu sungalimbe abusa inu
🤣🤣🤣🤣🤣yonse ndiminda komaso ching'axy mpaka kukoza amfumu
My favorite jokes love you
😅😅😅😅 koma iweyo ching'aning'an atimenya eti 🎉😂😂😂😂 goood job guys
Kkkkkkk Ching'axy anadza 😅😅😅
Ati basi yose ndiminda😂😂😂😂
Koma ineo honestly the whole episode palibe ndatolapo
Sanje ibweletsa kaduka
Koma iweyo Ching'axy🤣🤣🤣🤣
Ine ndisasangalase gulu😂😂
Mmakwana all the way from SA
Ching aksy ndi machine
Zikut bwanji kodi😂😂
Yonse ndi minda😂😂😂😂
Mr mukumakomesa km chomachedwesa ma episode
A best boy wo😂💔🚶 Ah
mumaitha Mr jokes 👍
Koma ching'aning'ani ayi ndithu usazamfe ...uzit undimenya timenyedwa for me 😂😂😂😂😂😂
Yonse ndi minda basi kkkkkkkkk
🤣🤣🤣🤣🤣 yose ndi minda ya yolodani kumene
Kkkkkkk Koma abusaa🤣🤣🤣.. akuti basi yonse ndi munda
Yonse ndi minda😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
😂😂 bas jokes warepheretsa ukwat
Kkkk eti ching'axy pepan abusa Munda wa Eden 🤣🤣🤣
Chomwe ukufunacho Mr jokes uchipeza ndithu.suukufuna Banja iwe😂😂 km kulimbandi Mdalayo
Abusa ayiwala dzina la munda😂😂😂😂😂
kkkkkkkkkkkk km ndaseka abusa akut yose ndi minda😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Chinyaxy adha🤣🤣🤣🤣
Munda waGetseman🤣🤣💔💔
Ching'aning'ani ndi Dolo ase eeeeee
Mbambande Mr Jokes ...chilungamo basi kkkkk
mwatisiya mwendo mmwamba
Oyamba ndineyo sapota Mr jo tujuane mashabiki wa mr Jock's
Ching'axy sukukukalamba bwino iwe 🤣
Kkkkkkkk koma Mr Jokes
Sure, Malawi 🇲🇼 moto
👍👍👍👍👍👍👍👍👍😍😍😍😍😍Very nice This is evidence that MALAWI 🇲🇼"" -~a swing
Kwisa ma big
Ching'aning'ani uja ndi Dolo kuposa ena tonse pano
Yonse ndi minda
Kkkk ati yonse ndi minda😂😂😂
😂😂Yonse ndi minda😂😂❤
Kkkkk ati yonseyo ndi minda
Mpaka Ngoziyankhuku
Yonse ndi Minda
Kkkkkk good joks izarekanise infa mwina achedwa kufa nanga kkkkkk
😂😂😂😂😂 Za imfazo ai moyo ndiwanga 🤣🤣🤣
Mr Jokes unabwela iweyo 😂😂😅😅
😂😂😂😂😂😂 ching'asi iwe wa ideni
Chilungamo Cha nyooooo
Mkazi wa Jokes mutu samasintha abambo kuwumila
Komatu jokis 😂😂😂eeeeh
Basi yonse ndi minda🤣🤣
Ndathokoza kwambiri boss wanga
Kkkkkk ati timenyana
aaah basi yose ndi minda 😂😂 koma abusa😂😂
Jokes sazatheka ndithu 🤣🤣🤣
Akut yonse ndi minda 😂😂😂😂
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
😂😂😂 mr jokes saku funa matenda m banja
Mbambande 🔥🔥🔥
Koma mr jokes anakonza
Munda wa getsemani hahha
😂😂😂😂 problem vs problem
Nde nzomwe ndukanazo kkk
Mr Jokes você tem Razão kkkkk
I remember those days ngoziyankhuku
Mr jokes samamufuna mkadziyo kkkkk
Yabaya Imba Belu Imba Belu 🤣🤣🤣🤣🤣
😂😂😂😂 Jokes too much talkative 🤣🤣🤣 sazakwatila uyu kuyankhula uku 😂😅😅 tell him ching, axy 😂
Makwana guys 😂🤣🤣
Koma jocks ndiwe ovuta😂😂😂😂