Anthu ena amakhulupilira kuti ufiti kulibe - anthu amenewa sanakumane ndi a Eliya William. Iwe amatsimikiza kuti adatambako komanso adapangako using'anga. A Eliya anali mkulu wa bungwe la asing'anga ku Malawi kuyambila 1986 mpaka 1996.
Iwo siabisa kuti achita zinthu zoopsya komanso aona zambiri kudzela mmatsenga. Iwo akutsindika kuti zambiri zimene timamva zokhudza amfiti ndizoona; amfiti amauluka kugwilitsa ntchito lichelo kapena tsache, ndondocha ndi anthu akufa amene amawathila mankhwala kuti achepe akatelo amawagwilitsa ntchito mmatsenga kuti azikaba ndalama kapena kulima kumunda, anthu amalodzana munjira zosiyanasiyana kuti wina afe kapena azikumana ndi matsoka.
Nkhani yabwino ndiyakuti a Eliya zaufiti komanso using'anga adasiya ndipo pano adayamba kupemphela ku mpingo wa Zioni komwe adakwela mpaka kufika pa udindo wa Bishop.
Am leaving this comment here so after a month or a year when someone likes it, I get reminded of watch. ELIYA ❤again and again🤣😂
Ive liked your comment its a reminder kuti udzamvere music ya Amulungu inu. Kkkkkk
Watch it again kkkk
Watch it
Watch now hahahahaha
Hey!
It's the song for me " Amulungu aaah, Amulungu nomwenu inu. Inu aah eeh, munatuma oyesu koma oyesu nkufa aaah, omulingu aah 🎉😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
I like this and I will watch whenever someone come and comment Kaya padzatha zaka zingati 😂😂
Lemme rewatch this interview in 2024😂
Am watching now 😂😂😂😂😂
Ayi tamva nawo zambiri kuli zinthu kunjaku thanks joab for bringing this guy
I will always come back here and rewatch this piece. Its the greatest ever
Joab umatha kunena zoona l like and love the way umakhalila serious on your job. ❤❤
These are kind of people we need when stressed.Please Mr Joab bring more like him.
Absolutely right sir. 🤣🤣🤣
Hello
😅😅😅😅😅koma awa anyanyq aaa ndi stress siingachokenso koma kuopsya kwa munthu
Kkkk I just liked the way Joab was composed the moment Eliya was singing
The best interview ever on cruise 5😂😂😂😂
❤Ndimayisaka cruse 5 ya Eliya God bless you both
Can’t get enough of watching this interview..bravo Mr chakhadza😂😂😂😂😂
Ufiti siwabwinodi,look at this,ngati wamisala,wopepera ndi chamba Kkkk thats y ku court amakanika kuweruza mirandu ya ufiti, Chomwe akunena apa does not make sense-ku court antha kumangonena mbwelera ndithu! But this is good for intertainment.
ndkubadwa kwake osat character yasintha NDI ufiti Kkkkkk NDI president tu awa
Joab ndiwe legend I would have collapsed with laughter atangoyamba kuyimba nyimbo
I just got this video today. The guy is humble. Malawi needs to address this issue of witchcraft.
Akut nyimbo ndiyimba ndekha kkkkk ine koma lero ndanjoya
😂🤣😂🤣😂this interview is therapy session already
Joab...... how you compose yourself not to burst into laughter is beyond me. Good job 👍🏻
Great interview. Love your composure, I am on the floor🤣🤣🤣
How Joab remains composed in this 🙌🏾🙌🏾🙌🏾🙌🏾and then Eliya keeps looking back anga ngati afiti anZake akumuona 😂
ndpo angoti maso mwa mwa ngati akumuwuzila zonena athakati anzakewo
Et et kkkkk
🤣🤣🤣🤣🤣
🤣🤣🤣🤣
Kkkkkkk
Koma A Chakhaza mumakumana ndi zinthu. Keep up good work
Great interview joab ur the bast
It never gets old 🤣🤣🤣🤣🙌Eliya anabwera kudzakhala
Ndipo live😂😂😂😂
Nyimbo ayimba live,koma the guy has 100% confidence ayaya this world
Kkkkkkkkkk die ndagwa ine akuti pano ndinafiila koma kumeneko joab u r my day maker from SA
The fact that he’s wearing a Ralph Lauren shirt 🙌🏾🙌🏾😂Pali phindu 😂😂
🤣
hahahaha
ahahahaha
😂😂😂😂
Best program in the decade, laugh laugh and laugh. We need part 2
i still enjoying to watch
i have to come back and watch Eliya 😂
This was the best exclusive ever my artist musician Eliya nzeru😅😅😅😅😅
Tamvako zambiri ndithu. Bravo Joab... Bravo Bwana Eliya
Uncle Joab mwandiwaza eti nanga nkhwanya, nanga mnkhwani,, ndondocha sikudya mnkhwani otendera???🤣🤣🤣🤣😂😂😂😂,,,, Mmaitha uncle Joe, respect
I had to watch this again 😂. Great job Joab 👏🏿
This guy Elia needs a big help he has real demons but thanks to jaob for good work your amazing ❤ from south Africa cape town
Muwauze, we need air Malawi back in the air space. Kaya idziyenda usiku okha okha, bola idziyenda basi. Apapa solutions to our problems are already at hand
The best gospel artist of the year 😂😂😂😂😂😂😂😂
Kkkk
Upcoming artist of the year😂
Exactly
Lol 😂😂😂 this interview was funny. Joab, how did you remain calm sir. I was stressed but I've laughed out loud 😸
😂😂😂😂🤣🤣🤣 Nzibambo a meiyu ngo seketsa
Starting off the year with this hilarious interview.Mr Eliya ndi stress reliever
Joab you are professional, salute. How you remained composed in this eeeeee. With loosening of association ili umu🤣🤣🤣🤣mnkachimwa ndi kuseka iiii
😂😂😂
kept up Mr joab you did agreat job !!!!
This was best Joab
I've watched this C5 twice first on fb now I'm here again just to promote home industry despite being entertained ....
Waiting for his album to come out 😂😂😂😂😂
😂😂😂
Amulungu inu 😂
Ulemu wanu Joab, good job 🙏🙏
Achimwenewa ofunika amulandile yesu chifukwa zomwe akulongosoladzi ndi mphavu yaziwanda
Akudura anyedzi ndani? Anzanu tikumvera nyimbo ya Amulungu bwinobwino apa! Tikusekelera inu anyedzi duledule. Aaah! Chiphwete cho Eliya aweee! Akati atsekelere ...
Hahaha a eliya gosekesa kwambili 😂😂😂😂
How did I not watch this all this time
Uyu ndiofookwtsa ... AMulungu mudatuma Yesu koma. Yesu Nkufaa aaaah
Eti Inu 😂😂😂😂
Had to revisit this one. Oh My!
Seriously, I haven't laughed this much in ages. Interview more real Malawians, Joab. Wonder how you kept a straight face man!! Good work!
Tadzipo zina zomwe sitinkazidziwa , Thanks to you JOAB FRANK CHAKHAZA
wow Mr joab frank Chakhaza tasangalala ndi program imeneyi ...akufukika azabwerenso abambowa ayiwala zina sadandifotokonzere bwino lomwe😅😅😅😅
That shirt is nice, he has class
Mmmmm ati nyimbo ndiyimba ndekha😂😂😂😂😂 apa mpaka kare ndikuonera😂😂😂😂😂
The great of all time .. Katakwe
Eliya wavala polo❤
Koma Ali ndi zaka zingati agogo Elia wa Chifukwa akukambatu za,Kamuzu
My oh my,on a serious note...Elia rocks period!his sense of humour is beyond measure...I can watch this repeatedly...koma Joab amaoneka ngati akuopa kkkkkk!love the Ralph Lauren shirt bwana.
1
1
This is fascinating
Mavuto amanjoti story, big brother wa papa Gopani.
Nafwa 🤣 great job Joab 👍🏾
Ndikafuna kuseka ndimaonera interview iyiyi Mr Joan mmakumana ndi zithu 😂 Eliya am still waiting for your Album😂
Joab u are super
KOMA ELIYA, akupweteka anzakò ndithu. Apolice alikuti kodi.
Akuti munatuluka chikatundu mu mazila kkkkk then the smile from Joab
Koma zina🤣🤣🤣🤣
Last song kills everything 🤣🤣🤣🤣🤣
🤣🤣🤣
Joab interview iyi inamusowesa mtendele mafunso amavuta😂😂😂😂😂 Eliya uja anakonza
Mmm muthu opatsa chidwi kuvetsela ndithu.wawulula zambili
Kikiki koma ndiye I can't stop watching this
Ngiwa we miss you on ur channel
Khala ngat mutu sukugwira bwino ntchito tuu a Eliya
My favourite program
I saw Joab was frightened, he really wanted to run away😂😂😂😂😂
Cruise 5 👍💖
Eish!! Kuli zinthu kudzikoku🙌🙌
Azungu otuluka mmazila kkkkkkkk mwatipatsa phwete! Kkkkkk Komatu achakhaza mumadziwa kusaka nkhani kkkk more fire!!!!!!! kkkkkkkkk
Omg I know Eliya personally as I went to his house in area 25 ku Sungwi that was 2001. He was simple guy.
am looking for him so hw can I faind u or Mr man plz
I think this mzeru man is real.
Who is here 2024?😂😂
am frowning you here in Lusaka Zambia kip tup
Chuma chochuluka zedi ,joab ee! Chochuluka zedi akuti chuma....dzindlama mipando mu tente 5'mu...kupeza ntendere koma
This interview is captivating
First time watching this 😂😂😂😂 so fascinating
I like Lilongwe accent, authentic! anything else he is saying is crazy 😂
Lilongwe accent ndi massive 😂😂
a Joab, serious mumafunsa bwino mafunso ndipo interview yanu imasangalatsa kwambiri. keep on it....we support
Hello
Mmmm...hilarious. Ba Joab ndimwe bapondo. Laughed so hard 🤣🤣🤣
Waiting patiently for part2😂
I'm Watching This But I'm Just Cracking😂😂🤣🤣 Madala Joab Be Bringing More Pple Of This Kind🤣🤣😂😂...
Joab ndiwe katundu pa ntchito yako
Never get exhausted 😂😂😂😂Joab umantha ,Nice Ralph Lauren Mr president
Minthuyu mmutu wake zikumandionekera kuti muli kavuto pang'ono
Joab plz am waiting part two kkkkkkk ndakomoka kwambili
Joab iweyo ayi umatiimilira
Aaaaaa, this man so called Eliya🙌🙌🙌🙌🙌.
MR.JOAB IM FROM MOZAMBIQUE I NEED NUMBER OF THIS MAN
Koma joab iwe anakonza uzabwele kwathu ndizakuphele nkhuku yalokolo
Aaaah koma a Chakhadza chonena chikundisowa.
We believe in the great physician...the Lord Jesus Christ.....this man needs to receive Christ ...lest he dies in his sins
Ndipo ine ndiye ndakomoka ndi phwete kona a Eliya amenewo mayimbidwe😂 ndipo ndajoya ndisaname ka stress konse kutheratu. Achakhadza mumakwana and mwatifunsira mafuso okhaokha ofunikira
Whose here 2024😂
Is the last song for me 😂😂😂
Kkkkk can't wait for part 2. Koma NDA Seka osati zibwana
😁😁😁😁😁fent
Koma amenewa angapweteke coz akuwoneka kuti ndi khang'a
zikomo Joab tadziwa nawo zinthu zina zimene ena amakanika kunena koma pamene amachita.
Guys komatu ndaseka mpaka kufika ponena kuti ngati Muthu salozedwa ife asing,ang,a tizidyanji this guy is very funny 😅😅😅😅