NSOKHANO WA DPP LERO 28 APRIL 2024

2024 ж. 27 Сәу.
21 679 Рет қаралды

Пікірлер
  • APM my vote

    @LysonMtalika-tb6fk@LysonMtalika-tb6fk16 күн бұрын
  • Dpp🎉🎉🎉🎉❤❤❤❤❤❤ .... MCP vayaaa booo

    @AhmadumkomaTambala-lr9gp@AhmadumkomaTambala-lr9gp14 күн бұрын
  • APM ❤❤❤❤❤❤❤❤❤

    @user-uc1pd1tc2x@user-uc1pd1tc2x16 күн бұрын
    • Ttyl bas but bbytt4tttt TT CV7f 1:29 1:29 o HTH v call to NYU 1:58 free 1:58 hi fyi free g great t Fred ext 2:41 two years n he 5 by5by 2:00 DD😮 2:01 😅😅😅😮😅 2:07 in hi h or gh5 2:10 ut BB 1:31 FYI

      @amazingmkhungo-qt9se@amazingmkhungo-qt9se13 күн бұрын
    • Ttyl bas but bbytt4tttt TT CV7f 1:29 1:29 o HTH v call to NYU 1:58 free 1:58 hi fyi free g great t Fred ext 2:41 two years n he 5 by5by 2:00 DD😮 2:01 😅😅😅😮😅 2:07 in hi h or gh5 2:10 ut BB 1:31 FYI

      @amazingmkhungo-qt9se@amazingmkhungo-qt9se13 күн бұрын
  • DDP woyeeeeee🎉🎉🎉.All the way from America mwana wa kumneno.

    @user-xu5nn2gx6e@user-xu5nn2gx6e16 күн бұрын
  • Team ya Anthu wodwala wokhawokha,akuveka munthu mmodzi!!!

    @EdwinMabviko@EdwinMabviko15 күн бұрын
  • DPP ❤❤❤❤

    @user-fp3dt1sz8j@user-fp3dt1sz8j16 күн бұрын
  • Dpp 2025 boma ❤❤❤❤❤

    @StanziaElias@StanziaElias15 күн бұрын
  • Apm my vote ✊

    @user-bq5ev7de1l@user-bq5ev7de1l16 күн бұрын
  • ❤❤Dpp my vote

    @user-vu9rt8gj3o@user-vu9rt8gj3o16 күн бұрын
  • Chakwera achokeeeeee

    @user-uc1pd1tc2x@user-uc1pd1tc2x16 күн бұрын
    • Choka iweyo

      @ziyamporoma377@ziyamporoma37716 күн бұрын
    • Cakwera akucokadi 2025

      @user-hm9nc7lz6e@user-hm9nc7lz6e16 күн бұрын
    • @@user-hm9nc7lz6e Ndikukuuza zedi ameneyi kwake kwatha Joy

      @user-uc1pd1tc2x@user-uc1pd1tc2x15 күн бұрын
    • @@ziyamporoma377 Chikuchoka chokuba chakochibe uwona soon

      @user-uc1pd1tc2x@user-uc1pd1tc2x15 күн бұрын
  • APM my vooooote

    @ThabisileKanyoza-sr4fz@ThabisileKanyoza-sr4fz16 күн бұрын
  • Apm vote❤❤

    @user-cy7gd1go6y@user-cy7gd1go6y16 күн бұрын
  • 🔥🔥🔥🔥

    @eliffagondewe8214@eliffagondewe821416 күн бұрын
  • My vote

    @user-ot8gm7nu5b@user-ot8gm7nu5b16 күн бұрын
  • Tikufunaso feteleza uja wa 5pin. Chakwera adalephera Ubusa nde angayendetse dziko? 100% Peter akuliphula dziko mu mng'anjo ya moto 2025.

    @spargomw@spargomw16 күн бұрын
  • ❤❤❤Adad

    @user-xw6rr9gm1z@user-xw6rr9gm1z16 күн бұрын
  • DPP Woyeeeee ❤❤❤

    @user-jw5rx9ze8k@user-jw5rx9ze8k16 күн бұрын
  • Ankanena adadi nyekhwe mukuinenai mudzaione ndinu lelo ndiizi ndimafuna ndisakavote kma apa ndikavota adadi woyeeee

    @user-fm5fk1zt1l@user-fm5fk1zt1l14 күн бұрын
  • DPP bomaaaaaa mbambande zedi ili❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

    @user-uc1pd1tc2x@user-uc1pd1tc2x16 күн бұрын
  • Apm is my vote 🗳 galu busa iweyo usamale chifukwa palibe chako chakwera

    @user-mx3rw2dt4z@user-mx3rw2dt4z16 күн бұрын
  • My Voye

    @maxwellmajawa6091@maxwellmajawa609116 күн бұрын
  • Galu akumana 🔥🔥

    @sungananigondwe2807@sungananigondwe280716 күн бұрын
  • Apm my vote ndinari konko lero MBAMBANDE Dpp ikulowaso mmboma

    @user-ky4ce9gb6j@user-ky4ce9gb6j16 күн бұрын
  • Chachikulu bola mupange chilungamo, chonde, anthu akuvutika

    @petermsamariamapira8933@petermsamariamapira893316 күн бұрын
  • DPP woyeeeeeeee ❤❤❤❤ boma iloooooooo🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

    @user-uc1pd1tc2x@user-uc1pd1tc2x16 күн бұрын
    • Boma limakhala kunja aise? Makweratu yokuphwa

      @ziyamporoma377@ziyamporoma37716 күн бұрын
    • ​@@ziyamporoma377ukhale maso aise udabwa

      @ShamilahSaizi@ShamilahSaizi16 күн бұрын
  • Adad❤

    @user-wv5hz8ce3i@user-wv5hz8ce3i16 күн бұрын
  • Kkkkkkkkk awa ndiye ai bolani mcp😂😂😂

    @casilasjawadu1586@casilasjawadu158616 күн бұрын
  • Kkkkkkkkkkkk I hope we will fast up September 16 3025

    @DerlinNyirenda@DerlinNyirenda16 күн бұрын
  • ❤❤❤❤❤❤❤

    @moyorobert9801@moyorobert980116 күн бұрын
  • ❤❤❤❤ dpp

    @EsnartBester@EsnartBester16 күн бұрын
  • Ha ha ha!!!! From TANZANIA..,. ZINA LANGA leni leni ndi CHIFUNDO..... A MCP... Tikumana kuseliku DPP WOYEEEEE!!!!!!

    @MikeMalinga-xx8ys@MikeMalinga-xx8ys16 күн бұрын
  • Kodi akaluza ndiye zinthu zitha bwanji???? All reputation that he has ever had will evaporate . Kusakhutitsidwa anthu greed

    @chesterphiri7523@chesterphiri752316 күн бұрын
  • Adad tikuvutika kwambiri. Chitsime chimaonekad kuphwa madzi akaphwa. Ambuye akhale nanu Adad.

    @spargomw@spargomw16 күн бұрын
    • Uzilimbikila pa zomwe ukupanga usamaloze chala munthu chifukwa chakulephela kwa ko

      @ChikumbutsoMaloya-zj2jq@ChikumbutsoMaloya-zj2jq16 күн бұрын
    • @@ChikumbutsoMaloya-zj2jq choka iwe, Dpp boma 2025 iwe nd mbuzi yakoyo, paulendi

      @spargomw@spargomw16 күн бұрын
  • tikudikila siku la voti

    @user-nk5mj5ws8v@user-nk5mj5ws8v16 күн бұрын
  • DPP ❤❤❤❤❤❤

    @UseniMailosi@UseniMailosi16 күн бұрын
  • Chakwera BOMA

    @jahlakechinsewu993@jahlakechinsewu99316 күн бұрын
  • K❤❤❤😂😂😂 kuli wa mcp ko akhoza kuzikozelatu

    @user-rd2td7bg4c@user-rd2td7bg4c16 күн бұрын
  • APM 2025 Boma❤❤❤❤❤

    @user-jw5rx9ze8k@user-jw5rx9ze8k16 күн бұрын
  • Munthu kudana ndi Amalalawi azake. Galu yinu nonse... DPP sazawina ngati woyimila galu wanuyo chitsiru

    @user-nj5vu8cd5l@user-nj5vu8cd5l16 күн бұрын
  • M'busa sangalamule dziko ndikuyenda bwino

    @AfickRobeni@AfickRobeni16 күн бұрын
  • My party

    @binalidjeyshabahzombamalawi@binalidjeyshabahzombamalawi16 күн бұрын
  • Vote for dpp

    @LuteSynos@LuteSynos16 күн бұрын
  • Mbuzi za anthu nonse munalikuti mu nthawi yanu ndie ngati munkapanga za nzeru munachotsedwelanju

    @ChikumbutsoMaloya-zj2jq@ChikumbutsoMaloya-zj2jq16 күн бұрын
    • Iweso mutu wako suumagwira mene akuyendela malawi pano unganyose dpp

      @user-cy7gd1go6y@user-cy7gd1go6y16 күн бұрын
  • mfumuyo ngati ili ya manja lende aziyembekeza kuti chakudya chichokera kuti?

    @brianwalawala@brianwalawala16 күн бұрын
  • Moto kuti buuùu 🎉🎉🎉🎉🎉

    @user-hk1lp2ho9w@user-hk1lp2ho9w16 күн бұрын
    • Moto wamapesi

      @ziyamporoma377@ziyamporoma37716 күн бұрын
  • Mukugawa za kudya lelo mukazawalengezesa pa gulu pali cha nzeru 😢😢😢

    @ChikumbutsoMaloya-zj2jq@ChikumbutsoMaloya-zj2jq16 күн бұрын
  • Mbavazikuluzikulu za DPP sangawine sleeping on duty

    @user-eo2ol3ww8h@user-eo2ol3ww8h16 күн бұрын
  • Ndakayika simungadutse

    @GiftJulius-ro9ev@GiftJulius-ro9ev16 күн бұрын
  • Mbuli zasonkhana apa kkkkkkkkkkk kunamizana aaaaaa boma la mangochi

    @user-uu9pv6jd4v@user-uu9pv6jd4v16 күн бұрын
  • DPP Boma 2025

    @JamesKamgwira@JamesKamgwira16 күн бұрын
  • awa alibe mfundo aaaa

    @user-pl6it7zc7c@user-pl6it7zc7c16 күн бұрын
  • Ndipo adad mukalowa m,boma mupange zositha zithu achite manyazi satana

    @user-eh1mg3ww6d@user-eh1mg3ww6d16 күн бұрын
  • Munali momwemo kukuvotelani inu nchimodzimodzi galu kudya masanzo ake.

    @brianwalawala@brianwalawala16 күн бұрын
  • Matapwisi eni eni mukunamatu…MCP ikusesani 2025 mulira

    @ziyamporoma377@ziyamporoma37716 күн бұрын
    • NO PAIN NO GAIN GO BACK 2 SCHOOL SMLL BOY

      @user-gx5ht9gm3z@user-gx5ht9gm3z16 күн бұрын
    • Wa manyi mutu iweyo eti

      @IdrisssJabu@IdrisssJabu16 күн бұрын
    • Wapwisa ndi iweyo

      @AleksaWilliams-qc6cn@AleksaWilliams-qc6cn16 күн бұрын
    • Chakwera bomaaa akusesani sakunama 2025 mukunya mukadetsenso sanjika zautsiru

      @JackMvura-ik2td@JackMvura-ik2td16 күн бұрын
    • Chakwera boma 🔥🔥🔥🔥🔥🤣

      @ancientnkhata1137@ancientnkhata113716 күн бұрын
  • Moti pali funds apa kkkkkk

    @user-uu9pv6jd4v@user-uu9pv6jd4v16 күн бұрын
  • Zaziiiii pitala mungamulalikire kuti ndiwabwino mtima

    @IbrahimWezely-qd4vj@IbrahimWezely-qd4vj16 күн бұрын
  • Apm or asanamenye kampeni akuwina basi chofunika inu azisogireri maso pasogolo sitikufuna kuti ena azabere ma vote

    @afrozwayson7482@afrozwayson748216 күн бұрын
  • Mcp my vote

    @KaipaEmanuel@KaipaEmanuel16 күн бұрын
  • Chakwera boom!

    @StanelyPhiri-kg1ix@StanelyPhiri-kg1ix16 күн бұрын
  • Kkkk mudyereni ameneyo mungawinise chipani inu??

    @brianwalawala@brianwalawala16 күн бұрын
  • Tikufuna ankaka or akabambe agogo akapume

    @user-pt8wb4vw6r@user-pt8wb4vw6r16 күн бұрын
  • Animation adhadhi, koma music musithe chinyengo

    @WisikiBlack-gj4gu@WisikiBlack-gj4gu16 күн бұрын
  • The guy sounds like Muluzi

    @MorrisMapiri@MorrisMapiri16 күн бұрын
  • Inu simmaonjezera ma wages kwa ma civil servant inu....

    @RABSONSIKELO@RABSONSIKELO16 күн бұрын
  • Peter muthalika galu ndi azako wonse ali kumbiyo

    @user-nj5vu8cd5l@user-nj5vu8cd5l16 күн бұрын
    • Pakunya pamako

      @user-rd2td7bg4c@user-rd2td7bg4c16 күн бұрын
  • Nkhani yabwino

    @dankunseyo6127@dankunseyo612716 күн бұрын
  • Osaganiza kuti Dpp idzatsitsa mitengo yazinthu ndibodza zinthu zikukwera molina ndi mmene zinthu zikuyensera padziko lose lapasi magnanimous amendable ndi umbuli chabe

    @user-zm4vy5rs4v@user-zm4vy5rs4v16 күн бұрын
  • Nonse agalu following galu Peter muthalika... Racist nyani pusi nkhwele

    @user-nj5vu8cd5l@user-nj5vu8cd5l15 күн бұрын
  • Kkkkk chipani ichi mamvuto alipo

    @FRADRICKMTANDE@FRADRICKMTANDE13 күн бұрын
  • Apm woyeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeee

    @DivinePhiri-se3xc@DivinePhiri-se3xc16 күн бұрын
  • Ayinso adhadhi

    @WisikiBlack-gj4gu@WisikiBlack-gj4gu16 күн бұрын
  • Kodi mwiwara zovuta zapitara chifukwa cha njara? Njala sabweretsa ndi president koma nyengo 2001 kunali njara kodi adabwertsa ndi president?

    @user-zm4vy5rs4v@user-zm4vy5rs4v16 күн бұрын
  • chilikwanzako dpp inkapanga zomwezi koma

    @user-yb2zl1nh9z@user-yb2zl1nh9z16 күн бұрын
  • APM woyeeeeeee ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

    @user-uc1pd1tc2x@user-uc1pd1tc2x16 күн бұрын
  • Kukapempha

    @user-zk7jw9up6m@user-zk7jw9up6m16 күн бұрын
  • Mbavazokhazokha izi

    @user-ul6gf4xb5l@user-ul6gf4xb5l16 күн бұрын
    • Mbava number one ndi cakwera mbusa wakumidima satana okumwa mwagazi

      @user-hm9nc7lz6e@user-hm9nc7lz6e16 күн бұрын
  • Adad omweo kuti Wawa wawa❤❤❤

    @user-eh1mg3ww6d@user-eh1mg3ww6d16 күн бұрын
  • Hahahhaha Maloto a chumba

    @giftzayawemaononga-zi8ci@giftzayawemaononga-zi8ci16 күн бұрын
  • Ndipo azayelekeze kubera mavoti anthu tizavuta osawelengaso kuti awa asilikari kufakufa bs boma ili latikwana ife mmmm anthu afa ndinjala zinthu kukwera mmmm mudzi iyi ya president sinayionepo ine

    @munashemoyo4190@munashemoyo419016 күн бұрын
  • Koma ziliko

    @user-rd4ft9nd8t@user-rd4ft9nd8t16 күн бұрын
  • Mwanvatu a Chakwera! Kkkkmmmm😂 udzaona nyekekwe 2025.

    @user-pv9uk6sc3w@user-pv9uk6sc3w16 күн бұрын
  • Amalawi mavuto tikadalinawo umphawi ukutivuta tikadavotelabe chakudya chatsiku limodzi

    @chizandaesau4611@chizandaesau461116 күн бұрын
  • Banja likatha Latha bas zilimbitsanani mtimawo muleka Chaka chamawa

    @ChrifordBiziel@ChrifordBiziel16 күн бұрын
    • Eti 😂 zitsiruzi

      @ancientnkhata1137@ancientnkhata113716 күн бұрын
  • Nkhalamba nthawi yawo yatha asiyeni azanu zawi zipitabe chitsogolo zipusitsani anthu osowa zochita zaulere zatitopetsa kutipusitsa ayi mulore ife tizigwira ntchito kuti banja lathu lizipeza zosowa zanu

    @user-yk9lx7xd1i@user-yk9lx7xd1i15 күн бұрын
  • DPP ikungotaya nthawi siizalowaso m'boma. Inatizuza kwa zaka 6 popanda chochita. Awuzeni amaliseche akumwera anene zomwe anachita kwa zaka 6 zomwe analamulira dziko lino zomwe zikupidulilaso amalawi.

    @user-mj3ms4jt3b@user-mj3ms4jt3b16 күн бұрын
    • Iwe ndiwe uzungulira mutu eti kkkk

      @frankbanda7333@frankbanda733316 күн бұрын
    • Misala yamupweteka ameneyu

      @ShamilahSaizi@ShamilahSaizi16 күн бұрын
    • Vutotu ndiloti amaliseche amwera tinawaona kale kuti ndiolephera. Chimene aziwa ndikutenga ndalama mu budget yaboma ngati akukapangira chitukuko iwo mkukangoika miyala. Mbombela university kuchokera 2014 mpaka 2020 akhala akungotenga ndalama koma mbombela university kulibe. Sizokhazo ndizambiri komaso tsankho, kumpha alubino , kupondereza, kuondera anthu akumwera okha, katangale, ziphuphu, kuba, kuikira mbamva zigawenga kumbuyo ndikusalabadila zokhumba aza amalawi. Inetu sindikungonena, pitani mukawafise kumangochiko amaliseche akumwera akakuuzani zaine kuti ndimkawauza ndipo ndimawauza mpaka pano kuti zonyasa ndizoipa zomwe munachita zotsatila zake munachoka mum'boma mukufuna. Komaso pano akukupopaniwo akungofuna apidule kuchokera mwainu koma simungawine chisankho loko Chair person wa MEC atakhala mwana wawo

      @user-mj3ms4jt3b@user-mj3ms4jt3b16 күн бұрын
    • ​@@user-mj3ms4jt3b yomweyo gule iwee 👿👹👺

      @IsmailNdemanga@IsmailNdemanga16 күн бұрын
  • Inu munamanga kut madzi anayamba Inu musanabwele m'boma

    @ChrifordBiziel@ChrifordBiziel16 күн бұрын
  • Zikomo chehe ulaliki wanu tauva moti tikausatila tikapulumuka Ku moto wa jahanam

    @MikeWyson-cf9os@MikeWyson-cf9os16 күн бұрын
  • Chakwera nigalu bora adada omwewo

    @muyabasamson@muyabasamson16 күн бұрын
  • Racist president in Malawi, chigalu chigalu chimbwe, machende ake peter ndi omwe akumutsatira

    @user-nj5vu8cd5l@user-nj5vu8cd5l16 күн бұрын
  • Galu zitsilu Peter muthalika. Racist president of Malawi.... Chinkhalamba chopanda nzeru peter muthalika

    @user-nj5vu8cd5l@user-nj5vu8cd5l16 күн бұрын
  • Mukuchedwa ndi agogo

    @PeterChikoja@PeterChikoja16 күн бұрын
    • Ukungovutika kuti cakwera angawine ukunama sangawine mbusa okupha oononga Santana wakumidima

      @user-hm9nc7lz6e@user-hm9nc7lz6e16 күн бұрын
  • Apm boma or wina asafune

    @user-xd1cm7tm7t@user-xd1cm7tm7t16 күн бұрын
  • Useless speech

    @gladsonritche7641@gladsonritche764116 күн бұрын
  • APM my vote

    @ChrisEnos-to5uv@ChrisEnos-to5uv16 күн бұрын
  • Nkharamba oyee mbombora yirikuti zaziii

    @user-gh6qm5ze3b@user-gh6qm5ze3b16 күн бұрын
  • Adad Mosgozedwa ndi Mulungu imani nafe atifinya

    @AleksaWilliams-qc6cn@AleksaWilliams-qc6cn16 күн бұрын
    • Ndipo kwambiri

      @user-ky4ce9gb6j@user-ky4ce9gb6j16 күн бұрын
  • APM my vote

    @RobertGoliat-gt2qh@RobertGoliat-gt2qh16 күн бұрын
KZhead