DR JOYCE BANDA KUYANKHULA KOYAMBA MU CHAKA CHINO

2024 ж. 23 Нау.
46 680 Рет қаралды

Пікірлер
  • APM MY VOTE

    @user-dd4mn3yk4f@user-dd4mn3yk4f
  • Ife sitikufuna zaulere ayi ife tikufuna kumazidyetsa tokha tikamalima amalawi ndi anthu olimbikila panonso sitikufuna mbusa ayi takanana abusa onse avunda basi ife sitizawakhulupililanso ayi abusa mwatipusitsa iweyo Joyce Banda usamathe zamkwamwa palibe angakuvotere iweyo ayi

    @user-ee6be5kl5o@user-ee6be5kl5o
  • Boooooooon kalindo🔥🔥🔥activist mmodzi yekha

    @jamessingini-fh1bz@jamessingini-fh1bz
  • Mayi ngati mukufuna ulemu musankhe kukhala chete.

    @user-vd6gu7tv5u@user-vd6gu7tv5u
  • Inu mai banda mukuthandiza anthu because ndalama zimene munabera amalawi. Ndalama za cash get munagulisa ndege imene bingu anagula ndalama zili kuti musakhale ochenjera apa

    @thulanimpphiri6873@thulanimpphiri6873
  • Iwe ndi hule chitsilu wayamba kapeni iwe wagwa nayo my vote is peter

    @RobertLuka-wy9cl@RobertLuka-wy9cl
  • Ine ngati zika ya Malawi Joyce banda Chakwera chilima asakhaleso atsogoleri amalawi moyo wawo wose ngati mukufuna Malawi akhale wabwino.

    @thulanimpphiri6873@thulanimpphiri6873
  • Good job❤

    @user-wm5tv7on2u@user-wm5tv7on2u
  • Good speech i like how you Tok my best Mom, onyasidwa anyasidwe

    @user-oq5rg5mz7q@user-oq5rg5mz7q
  • Please pamene pafika malawipaaa, sizomazichemereraaa ndizithu Zaulele. Help these people to be independent not tizizichemerera ndikupereka zithu zaulele. Mai Joyce Banda you are contributing to the poverty of this country. Help these people to be independent like you not this Nonse of building nyumba. Let’s give malawi good future, don’t take advantage of these people. 😢

    @khumburanimukhupa4792@khumburanimukhupa4792
  • Mungozitukwanisa inu aaaaa daily salu pa phwewa grace chinga akukudikilani ku mwamba mukayakhe

    @AishaChipande@AishaChipande
  • Best speech our beloved former president osat chopotoka mikono chija ayi

    @user-gj4li2gc8o@user-gj4li2gc8o
  • I like the massage osalola kulolodwa kuti ndiwe osauka powerful massage

    @saisonmwenda1275@saisonmwenda127528 күн бұрын
  • Ife zogawazo tatopanazo tikufuna tizipanga zanthu zolandilazo ndiye zausiruzo zimenezo

    @McphersonMsulira-zx2lj@McphersonMsulira-zx2lj
  • Nkhani ndiya straight iyi peter mutharika anthu amadana awa kwacha mayi atisokosere uyu anapumatu😂😂😂

    @jamesgama5489@jamesgama5489
  • APM my vote koma kalindo ekhayo akusambwanzani mayiii

    @giftjamali8204@giftjamali8204
  • Well spoken i do proud of you always mama

    @JonesMajiya@JonesMajiya28 күн бұрын
  • Allomwe kwao ndi kutukwana nanga si sukulu inavuta

    @JohnPoul-lk5yq@JohnPoul-lk5yq
  • Mutilakwitsa mayi, zipatseni ulemu nokha

    @user-hx9mg6ei1t@user-hx9mg6ei1t
  • Good speech mama❤❤❤

    @hadgeyahyaa8574@hadgeyahyaa8574
KZhead