zomwe zachitisa kut Tamia amangidwe

2024 ж. 14 Нау.
49 524 Рет қаралды

Пікірлер
  • Ndiwakuba

    @Dricofame@DricofameАй бұрын
  • Munthu sungatenge ndalama zoti sizako , kumeneko ndi kuba , amupani apolice kuti apereke ndalamazo.

    @user-ym6xu3xt2i@user-ym6xu3xt2iАй бұрын
  • umenewo ndimoyo wakuba ndichifukwa amalawi tikuvutika ndiumphawi tidazolowela zaulele

    @afoso-hy1hc@afoso-hy1hcАй бұрын
  • Tamia ndi wakuba kumene akufuna kukolora pamene asanalime mmmm ntsikana iwe umuziwe yesu ndi ophunzira ake 12

    @user-ce6hy6tp7e@user-ce6hy6tp7eАй бұрын
  • Ndikuba anakana bwanj atamutumizila?

    @HawaPearson@HawaPearsonАй бұрын
  • Mbava imeneyo boss😂😅😂

    @user-nz7bd7lm4i@user-nz7bd7lm4iАй бұрын
  • Ndikumba kumeneko ikhale kuti ndiyake sakanasitha account

    @FrankGoodwill@FrankGoodwillАй бұрын
  • Kt ndiokuba

    @ShamimGeorge-bg8si@ShamimGeorge-bg8siАй бұрын
  • Wakuba

    @user-kr8nm1sx5j@user-kr8nm1sx5jАй бұрын
  • anaba basi

    @samuelben9607@samuelben9607Ай бұрын
  • Kuba kumeneko kma why tamia

    @HajiraJaffar-bt3ci@HajiraJaffar-bt3ci2 күн бұрын
  • Oimba wakuba mbala?😂

    @HappyFlamingo-dz1uo@HappyFlamingo-dz1uoАй бұрын
  • Ndiwakuba basi big

    @prayphiri3184@prayphiri3184Ай бұрын
  • Otumiza tiyeni tizionesesa, osamayikana mmayesero Malawi wavuta uyu tonse tikudziwa chonde!!😊

    @joycemhango4353@joycemhango4353Ай бұрын
  • Ameneyo.ndiwakuba Kwambiri.akufuna Nzake.angwire Ntchito.yopanda Malipiro

    @OmakiMataya@OmakiMatayaАй бұрын
  • Ndye yake Tamia mistake siyako Mulungu amapatsa mosiyana osalora munthu kulanda zomwe Allah wapelereka mu mwezi wa Ramadan uno

    @user-tt1sh5wv8k@user-tt1sh5wv8kАй бұрын
  • Kubakumeneko

    @AnastasiaChakwiya@AnastasiaChakwiyaАй бұрын
  • Kkkkk zonsayenda bwanjik apa 🤔🤔

    @George-yi2iz@George-yi2izАй бұрын
  • Kumeneko ndikuba sakazisakusa ndalamazo

    @frankkassim1254@frankkassim1254Ай бұрын
  • ,,,😂😂😂same Story life goes on with straggle....sapasa pamanja guys amene anyambisa mawu awo analakwisa *(SAPASA PAMANJA)*

    @T0R1N0.@T0R1N0.Ай бұрын
  • Kkkkkk km khani zake 😊

    @lusolawo73@lusolawo73Ай бұрын
  • ndiwakuba ameneyo

    @danielmataka4403@danielmataka4403Ай бұрын
  • Timvele nawo brother zimenezi 😂😂😂😂😂😂

    @RichMavoko-nx8cn@RichMavoko-nx8cnАй бұрын
  • Ndiwakuba ameneyo 😂😂😂

    @user-wq2ix7ck5v@user-wq2ix7ck5vАй бұрын
  • Chotola salanda

    @nditumenichagunda4192@nditumenichagunda4192Ай бұрын
  • Zalowa zokha 😅 amujata bwa

    @user-sw1cs9dh1p@user-sw1cs9dh1pАй бұрын
  • Kkkkkkkk sanabe

    @sokanyabralosa844@sokanyabralosa844Ай бұрын
  • Ndimbava apereke ndarama zamwiniwake

    @user-hg8zy8pt5b@user-hg8zy8pt5bАй бұрын
  • Chesu sapasa pamaja

    @user-xw9sk1iu6i@user-xw9sk1iu6iАй бұрын
  • Sangalakwitse Mulungu sapereka pa manja aaaa

    @MathewsEnamu@MathewsEnamuАй бұрын
  • Eya ndiwakuba ammeneyo ndipi wazionongeka cv

    @nathanvanderberg6558@nathanvanderberg6558Ай бұрын
  • Angobweza

    @user-fo3hm8rh1i@user-fo3hm8rh1iАй бұрын
  • Kumeneko ndi kuba

    @estherbunaya254@estherbunaya254Ай бұрын
  • Akuyenera kukhara ndi m'mene information ilili

    @Patricia-db9yl@Patricia-db9ylАй бұрын
  • Tamia ja siwakuba,ndipo sikutiso walakwitsa ai ameneo ndi manner😅😅

    @user-lj7lm6ly7z@user-lj7lm6ly7zАй бұрын
  • Amangidwe basi, apeleke ndalama ya eniwake

    @user-pv9uk6sc3w@user-pv9uk6sc3wАй бұрын
  • Kumeneko ndikuba abweze ndaramayo

    @user-rh6kp9ts3x@user-rh6kp9ts3xАй бұрын
  • Ndiwakuba ameneyo

    @AngelManda-vk1nc@AngelManda-vk1ncАй бұрын
  • Mabigi ameneyu sanabei mutakhala inu mungatani amalawiso umbuli udakula inu mungatani

    @EduardoTipa-pb2bc@EduardoTipa-pb2bcАй бұрын
  • Ndiwakuba basi khani ikuzikamba yokha big

    @ShafineLouis@ShafineLouisАй бұрын
  • Chakuba chimenecho ayse

    @Rajabuhassani-nu9cd@Rajabuhassani-nu9cdАй бұрын
  • ngati zilichoncho ndekuti anaba

    @osbornleman2500@osbornleman2500Ай бұрын
  • Ndiwakuba basi aaaa

    @AustinYusuf@AustinYusufАй бұрын
  • Ndikuba kumeneko

    @user-hc5fm7ig4n@user-hc5fm7ig4nАй бұрын
  • Akanakhala kt siwakuba akanabweza ndalama kwa mwini wake koma ngati sanabweze ndiwakuba

    @user-hl3st3cc4v@user-hl3st3cc4vАй бұрын
  • Mmmm ndiwakuba

    @marypatriciamakuru226@marypatriciamakuru226Ай бұрын
  • Amayenela kubweza ndalamayo kwa miniwake chako ndi chako chamwini ndi chamwini basi

    @AustinKanjoka@AustinKanjokaАй бұрын
  • Or ndili ine ngatenge😂😂😂😂

    @patienceThomJannah-xy8uw@patienceThomJannah-xy8uwАй бұрын
  • Akanabweza ndalama zaeni ake bas

    @user-cu6gd1ze7x@user-cu6gd1ze7xАй бұрын
  • Ameneyo anali mayesero

    @user-md7pk3yq6t@user-md7pk3yq6tАй бұрын
  • Ndiwakuba hule

    @user-vh9uk1jy7w@user-vh9uk1jy7wАй бұрын
  • pa ndalama sitisewera sapasa pamanja

    @SamsonChimwaza@SamsonChimwazaАй бұрын
  • Sana chite bwino

    @user-jv7jh3pr4l@user-jv7jh3pr4lАй бұрын
  • Sanabe koman zangochitik alanakhal iwow akanatan😥😥😥😥

    @denissegabriel2752@denissegabriel2752Ай бұрын
  • Siwakuba Tamia apopo apolice aziona Kaye information yankhani ndi mene nkhani inachitikila mtulutseni Tamia izo ndi chisomo chamulungu kuvomela anamuuza mkului kuti unditumizile ndalama wa shaut mulandi ine watson kuno Ku Durban SA

    @WatsonChimphine@WatsonChimphineАй бұрын
  • Siokuba km anachita kumungayila

    @user-cm7iw8ii3h@user-cm7iw8ii3hАй бұрын
  • Ndiwokuba basi

    @user-sb1cm1nm7e@user-sb1cm1nm7eАй бұрын
  • Siwakuba wapereka yekha wachola kunyumba kwake?

    @user-gw6mx8zw6t@user-gw6mx8zw6tАй бұрын
  • Wakuba ameney

    @ManessJana@ManessJanaАй бұрын
  • Hule mbava chigawenga

    @YasiduPemba@YasiduPembaАй бұрын
  • Siwakuba ai km muthuyo amamuyesa

    @user-el2ch3vn4u@user-el2ch3vn4uАй бұрын
  • Ea niwakuba iyeyo anakavomela

    @ChikondiKajawo-tm1ud@ChikondiKajawo-tm1udАй бұрын
  • Koma zamanyazi ndiwakuba

    @macleanmachamo@macleanmachamoАй бұрын
  • Pena chilungamo chimafunika ndithu uku ndikuyaluka choncho munthu ndiwachichepere mbiri yako yikuonongeka eish zandikhuza bwanji bola abwenze aona kuti apanga bwanji chamwini ndichamwini basi tamia uzivere chisoni komwe uliko

    @user-dc4yd3oo5r@user-dc4yd3oo5rАй бұрын
  • Kudziko lapansi kulibe yemwe samaba kungoti timangosiyana mabedwe.Tamia asayankhulidwe chipongwe Chifukwa cake zaoneka lero

    @user-ky4we4nu2v@user-ky4we4nu2vАй бұрын
  • Ndiwakuba ndi chifukwa chan anasintha acount

    @user-bp2hm7lt5c@user-bp2hm7lt5cАй бұрын
  • Kkkkkk eeee kma zavuta mayeselo awa

    @user-tu2xx9mm7l@user-tu2xx9mm7lАй бұрын
  • Mbava pa town

    @user-ot8ym2bg9z@user-ot8ym2bg9zАй бұрын
  • Koma ameneyi wayaluka chaka chino nkhani chake chachuluka uhule ulimomo apaso akuba kkkk zachisoni

    @user-ri3xd7fl2i@user-ri3xd7fl2iАй бұрын
  • Ea ndiwakuba coz nga munthuyo anamuuza kt warakwisa number anayenera kuvomereza ndikubweza ndaramazo

    @esthermalixani2244@esthermalixani2244Ай бұрын
  • Ngwakuba

    @SmilingFinishLine-fr6vy@SmilingFinishLine-fr6vyАй бұрын
  • Ayitu analakwisa akangovomela ndikumubwenzera mwiniwake yo if zili zoonadi

    @user-fe2iz2kb7c@user-fe2iz2kb7cАй бұрын
  • 😂😂 km yooo

    @JimmyBanda-fi3pw@JimmyBanda-fi3pwАй бұрын
  • Ndikuba

    @MaideiChishiri@MaideiChishiriАй бұрын
  • mwachiziwikire ndikuba

    @user-ul5wx6kb4f@user-ul5wx6kb4fАй бұрын
  • Sanalakwitse

    @user-el2ch3vn4u@user-el2ch3vn4uАй бұрын
  • Zokambilana siwakuba kape ndiotumiza

    @AronAlfazema@AronAlfazemaАй бұрын
  • Zaziii kungo funapo ma comment athu ku KZhead

    @mphatsomonjeza4371@mphatsomonjeza4371Ай бұрын
  • wakuba

    @MdalaJames@MdalaJamesАй бұрын
  • Analakwisa kusamusa ndalamazo

    @ishmaeldama8906@ishmaeldama8906Ай бұрын
  • Ai siwakuba

    @BridgetMBanda@BridgetMBandaАй бұрын
  • ngati zili chocho ndiye analakwisa anabweza koma akuti watuluka zulo lomwelinja

    @omarlux3434@omarlux3434Ай бұрын
  • Kumanena chilungamo Tamia ja ndi wakuba

    @PUTOJOAQUIMUPILARE@PUTOJOAQUIMUPILAREАй бұрын
  • Eya Tamia analakwinsa chifukwa munthuyo anatumiza by mistake mwanchidule kumeneko ndkuba

    @arabisaidi4768@arabisaidi4768Ай бұрын
  • Umbava ndthu

    @user-tn1xz8md7o@user-tn1xz8md7oАй бұрын
  • Kodi nanga mesa pamatsamba a zodiak ndi enawo akuti koma zoti walandira ndalama anavomera?komanso 8million yo anaipanga transfer online pakamodzi Kodi sikhala ndi limit patsiku?

    @user-yo6ix7nn9q@user-yo6ix7nn9qАй бұрын
  • Eya Tamia ndiwakuba chifukwa anakana chithu choti wachichita

    @user-og9hw8lg8u@user-og9hw8lg8uАй бұрын
  • Kkkkkkkk..... No idea

    @JamesMakina-lr9ij@JamesMakina-lr9ijАй бұрын
  • Siwakuba

    @user-dh4io2cb2b@user-dh4io2cb2bАй бұрын
  • Nde tinene kuti ndi wakuba

    @user-nm8gp1du2m@user-nm8gp1du2mАй бұрын
  • nKhambakamwa

    @DESERTSEED@DESERTSEEDАй бұрын
  • Kubatu uku

    @emmanuelagness3516@emmanuelagness3516Ай бұрын
  • Ndiwakuba kunonso zinachitika chimozimozi ndipo anagamulidwa kukaseva 2yrs chifukwa three qts yandalama anayipeza

    @user-oz1ts3yi7d@user-oz1ts3yi7dАй бұрын
  • Nsikanaya ndiwakuba

    @ReubenSoko-wx1if@ReubenSoko-wx1ifАй бұрын
  • 😂😂😂😂sizochtanso kufunsa ndkuba kowonekera kwaumbuliii

    @user-ft3qr2gk4y@user-ft3qr2gk4yАй бұрын
    • Amai amenewa ndi mbava yoopsya

      @bangwehealth3777@bangwehealth3777Ай бұрын
  • Kuba kweni kweni

    @user-te8we7gp5e@user-te8we7gp5eАй бұрын
  • Aaaaa analakwitsa kwambili

    @LoydPhandwo-yv4gf@LoydPhandwo-yv4gfАй бұрын
  • Ndiwakuba obvious

    @user-mz8nw6nx6p@user-mz8nw6nx6pАй бұрын
  • Wakuba 😂😂😂

    @user-gv1yv6ob2r@user-gv1yv6ob2rАй бұрын
  • Ngati poyamba panali transaction Ina to her a mistake can likely happen abweze ndalama zo kuba sikwabwino,

    @tenexchikumba@tenexchikumbaАй бұрын
KZhead