eeee!! ZAWAVUTANSO ANANKHUMWA AJA- MAVUTO SAKWACHOKABE 🤔🤔🤔🤔

2024 ж. 22 Сәу.
34 529 Рет қаралды

Пікірлер
  • 50 + 1 was a judgement conived by MCP and the Judges. Now the same MCP seems it as a disadvantage to win the 2025 election. So let it remain like that, God os God, Chakwela ndi u Satana wake avutika.

    @user-jn9tz3li3v@user-jn9tz3li3v14 күн бұрын
    • Those judges. I don’t know how far they are now with their reputations. They betrayed Malawi.

      @johndauya2245@johndauya224514 күн бұрын
  • The only thing I blame this country is that we divided ourselves into three and we need to understand if this continues koma nde tudzavutika and will never develop

    @HanockBanda-rr5uf@HanockBanda-rr5uf14 күн бұрын
  • Anankhumwa tazikalimani mbatata tizikakugulani kwachinakanaka 😂😂😂😂😂

    @DanielSingano-bb7xq@DanielSingano-bb7xq12 күн бұрын
  • Good point bambo banda ❤

    @trynessmsowoya4187@trynessmsowoya418714 күн бұрын
  • Ndipo ngalu ameneyi chakela azaziona wakumwamba akazamuyang'anila kumbali km ubwino wake akudziwa kt waluza kale ndiye alibe ntchito galu wamunthu chakwela

    @ElijahdChilemba@ElijahdChilemba14 күн бұрын
  • Now it's when we will know how our courts behave otherwise Nankhumwa is not fit to be a leader of opposition

    @kondwanimunthali7401@kondwanimunthali740114 күн бұрын
  • Akhothi ndi omwe akupangitsa kuti a Navitcha asakhale ndi mphamvu adagulidwa ndi MCP

    @user-ev6bi7jr7g@user-ev6bi7jr7g13 күн бұрын
  • MCP ndigalu simuzayiwona voti Yanga .MCP rabish

    @eliaskachali-xn2ve@eliaskachali-xn2ve14 күн бұрын
  • Mudalankhulamo za nzarutu iyiyi yokha Mr Steve

    @ThokohKalonga-je9rx@ThokohKalonga-je9rx14 күн бұрын
  • i like this guys analysis I wonder why we don't like this channel

    @Johnybegood260@Johnybegood26014 күн бұрын
  • Apatu Steve lero wanyankhulako zanzeru sunaope chakwera

    @munashemoyo4190@munashemoyo419014 күн бұрын
  • Kalanga ine .. chilichonse kulilongwe ?? Ma boma enawa tizingodya nyika emweyo mcp kuzuza

    @JohnBanda-ux9fy@JohnBanda-ux9fy14 күн бұрын
  • Agalu awa angotinamiza ife amalawi akut ona kupusa kwambiri, ndimadabwa nawo ife amalawi ife osauka koma timankhala ndimantha kwambiri ndichifukwa ationelera agaluwa

    @MustafaLikaomba@MustafaLikaomba14 күн бұрын
  • Anankumwa ngati zavuta kumeneko vomerezani bwerani kuno ku South Africa tizizagwira maganyuwa bro bola musinthe Malo ovutikira

    @user-xv5pr3ji6w@user-xv5pr3ji6w14 күн бұрын
    • Kkkkkkkkkk

      @ThoccoBondo-mx7vt@ThoccoBondo-mx7vt14 күн бұрын
  • Nankhumwa ndiwosokoneza kwambiri,

    @eliffagondewe8214@eliffagondewe821414 күн бұрын
  • Timvele nawo

    @PitchMarley@PitchMarley13 күн бұрын
  • 😂😂😂😂😂 Nankhumwa tapezani zochita zina

    @ThoccoBondo-mx7vt@ThoccoBondo-mx7vt14 күн бұрын
  • Mmmmm malawi for sale

    @user-nh1xh4mc7u@user-nh1xh4mc7u14 күн бұрын
  • Chilichonse kulilongwe bwanji zigowozonse zizima pazokha aliyense azipangazaka kumpoto pakat kumwera ndikumawa asativutisepo awa

    @user-ln3zx6wo4w@user-ln3zx6wo4w14 күн бұрын
  • Wamkulu mutu galu amulume Nakhumwa alibe manyazi nzeru mmutu zikuoneka kuti nzopelewera

    @FosterChilumba@FosterChilumba14 күн бұрын
  • Esh

    @user-xj9uy6wz7b@user-xj9uy6wz7b14 күн бұрын
  • Mwana achepa nazo uyu

    @kondwanimunthali7401@kondwanimunthali740114 күн бұрын
  • Passport ku lilongwe ID ku lilongwe Madera ena zero??? Boma la kuba

    @thulanimpphiri6873@thulanimpphiri687314 күн бұрын
  • Steve ...gud explanation

    @RABSONSIKELO@RABSONSIKELO14 күн бұрын
  • Gwedegwede ya athu awili okha bas chiyambilen program iyi athu muli ndi zibwana muzi ntchitomu bas

    @wysonkomela8223@wysonkomela822314 күн бұрын
  • Makamaka Joyce banda akundi nyatsa kwambili anawononga dziko komaso wakambilana ndi chakwela kuti akhalangati akupanga dzake lilibodza akudziwakuti kwmwela chakwela sanga patse ndiye akufuna ku pombonedza dpp kuti agawane mavot kumwela pakat akudziwa kut mcp niyawo chenjelani ni Joyce banda chonde athu akumwela chotsani akubawa panpando Joyce chakwela chilima please amalawi asawela Joyce banda wakuba ameneyu mayi okuba ngati ameneyu sinamuwone pamoyo wanga bingu anasiya ndege komaso dziko lamalawi lilibwino kwambili anabwela mu dzaka dziwili dzokha analemela modetsakhawa galuyu Wa mayi anabwela Peter anakudza lelo mukut mupangetso kapeni mwaononga kale mu tsiyeni Peter muthalika akodzeso ngati kale unu mudziononga iye azikodza monga chitsilu chanu Peter niwophudzila kwambili osati inu ayi

    @YohanePatrick-lc2lq@YohanePatrick-lc2lq14 күн бұрын
  • Ine ndikadakonda kuti zibwelere chikare chipani chilichose chizaime pa chokha

    @SaidiMbawa-st6bj@SaidiMbawa-st6bj14 күн бұрын
  • A DPP mukatenga boma zanu zopanda tsankho zija musiye. Akakamira boma. Pangani za federal tidzipanga zathu kumwera kuno. Awonso adzipanga zawo.

    @user-lc3sw8iz2g@user-lc3sw8iz2g14 күн бұрын
    • Zoonad kwambiri brother

      @user-uc1pd1tc2x@user-uc1pd1tc2x14 күн бұрын
    • Anthu awa ali ndi anthu ambiri koma akawina sasamala anthu awo

      @user-lc3sw8iz2g@user-lc3sw8iz2g14 күн бұрын
    • @@user-lc3sw8iz2g Koma zinthu zimakhala zotsika koopsa ndipo njala amathesa zedi

      @user-uc1pd1tc2x@user-uc1pd1tc2x14 күн бұрын
  • Court la ku malawi siliziwa kuweruza chilungamo

    @AubreyNyambalo@AubreyNyambalo14 күн бұрын
    • That is politics in malawi that's why malawi is poor country because they don't know how they can do to prove our country

      @HappyBirchForest-zy8nq@HappyBirchForest-zy8nq14 күн бұрын
  • Trash

    @user-nn7ys7fu5u@user-nn7ys7fu5u10 күн бұрын
KZhead