Malawian needed such a good leader of opposition,Mary Navicha do your job without being intimidations
@user-mz5ys1cx5r3 күн бұрын
Mama am proud of you, your a mother lndeed
@merviselias623015 күн бұрын
Brilliant MP my favourite villagemate,truly God chose you to serve Malawians from Bagamoyo living.Lord blesses and secure you.
@user-jl7oo6gd6i11 күн бұрын
Chemwali Mary Navitcha, poyamba sindimakutengani serious koma panopa u r one of my favorites. Where were you when Grezelda Jeffrey was given position of secretary general, that woman is a monster, she didn't deserve to be given that position. She is very rude and clueless, just good at talking trash.
@user-nj4ob8jw6y15 күн бұрын
May God continue protect you Mom ❤ mwayankhula mwamphamvu kwambiri ndipo Mulungu atinthandize mu 2025 Muno
@chrisboyce216 күн бұрын
Powerful speaking from our leader of opposition, congratulations madam Navicha
@LysonMtalika-tb6fk15 күн бұрын
Amayiwa palibeso chomwe akuchitika sakusiyana ndi nankhumwa leader of adafunika atakhara suleman osati awa palibepo
@ChristopherKabanga15 күн бұрын
You're a true leader and God bless u mama
@user-cq1wv9nq4y11 күн бұрын
Leader of opposition Mary Navitcha has Spoken Clearly. Keep it up
@LilianKachala-yz2xf15 күн бұрын
Nankhumwa ndiye amabweretsa mpungwepungwe ku DPP. Mai Navitcha is ahorse power for leader of opposition.
@prophetjacksonmakonda6311 күн бұрын
Navitcha umayankhula mwaumunthu siumanyoza koma chilungamo chokha bola musazasinthenso ngati Nankhumwa
@user-le3lr6jn7g16 күн бұрын
Zimayi uyu merry amandisangalatsa ever
@user-pl2lj6mh1z11 күн бұрын
Koma may uyuyu ndi kawawa❤
@YamzyAmos11 күн бұрын
Chilungamo chikhala poyera indeee mamie osagwedezeka imani njii kumeneyera nkhondo mtundu wa malawi...God time always is the best ...we all proud of you
@ChimwemweBottomani-hc5ju15 күн бұрын
Such a wonderful speech mom, hoping good in 2025
@OmarManjawira-wz3nt15 күн бұрын
Mama wangwiro powerful massage ❤❤❤❤
@NgomaRaheem15 күн бұрын
God bless you mary❤❤❤❤❤
@RobertLuka-wy9cl15 күн бұрын
Mbambande mai, congratulations for your clarifications how the situation it is in Malawi.
@user-lb6ek3ee6d16 күн бұрын
❤ Mai wa nzeru keep it up
@mofolomphamba341015 күн бұрын
Our mother Malawi ❤❤❤❤❤❤ thanks a lot Mom we love you and tikudikilira kukuvoterani Adad athu akulowadi m'boma pompanopa ❤❤❤
komatu zimayiyu atati akayimire u president wa DPP athakukawina mosavuta ameneyu arindikuthekera kotsogorera ndinthu
@user-nz9ty3ih1v16 күн бұрын
Speaker ujatu.. ndi hule. amanyengana.. ndi. Nankhumwa. Komanso. ndi wa. MCP. ndi chifuwa. amakondera hule
@SandraBanda-hd1li16 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂
@innocentlipenga15 күн бұрын
Mayamba bwino mama,
@WisikiBlack-gj4gu16 күн бұрын
A speaker nayeso ndi galu akutengela za chipani cha mcp Chipani chankhanza
@user-du9qs4tb6u16 күн бұрын
Munachita bwino osamasusa simwawona dziko lawonongeka koma mukanati muzisusa mukanathandiza kukonza zinthu akanazalowa mboma mosavuta koma apa nde mwayiphura amawona ngati madolo kumalimbana ndi inu chete wa nankhumwa wakuthandizani inu a dpp kuti muzaduse moyera.
@jamesgama548915 күн бұрын
😂😂😂😂
@SameKaposa13 күн бұрын
Very incoherent statements, koma mwati sukulu zuti bwanji? 😂😂
@johnmhango940515 күн бұрын
Apm boma 2025
@HedgensChisale15 күн бұрын
Some questions from the host....very useless
@EmmanuelEthanMaloya15 күн бұрын
DPP has to learn to identify and deal with its enemies. APM has to know this is not US this is Africa. Ndale imakhala yothana. Wake up DPP.
Malawian needed such a good leader of opposition,Mary Navicha do your job without being intimidations
Mama am proud of you, your a mother lndeed
Brilliant MP my favourite villagemate,truly God chose you to serve Malawians from Bagamoyo living.Lord blesses and secure you.
Chemwali Mary Navitcha, poyamba sindimakutengani serious koma panopa u r one of my favorites. Where were you when Grezelda Jeffrey was given position of secretary general, that woman is a monster, she didn't deserve to be given that position. She is very rude and clueless, just good at talking trash.
May God continue protect you Mom ❤ mwayankhula mwamphamvu kwambiri ndipo Mulungu atinthandize mu 2025 Muno
Powerful speaking from our leader of opposition, congratulations madam Navicha
Amayiwa palibeso chomwe akuchitika sakusiyana ndi nankhumwa leader of adafunika atakhara suleman osati awa palibepo
You're a true leader and God bless u mama
Leader of opposition Mary Navitcha has Spoken Clearly. Keep it up
Nankhumwa ndiye amabweretsa mpungwepungwe ku DPP. Mai Navitcha is ahorse power for leader of opposition.
Navitcha umayankhula mwaumunthu siumanyoza koma chilungamo chokha bola musazasinthenso ngati Nankhumwa
Zimayi uyu merry amandisangalatsa ever
Koma may uyuyu ndi kawawa❤
Chilungamo chikhala poyera indeee mamie osagwedezeka imani njii kumeneyera nkhondo mtundu wa malawi...God time always is the best ...we all proud of you
Such a wonderful speech mom, hoping good in 2025
Mama wangwiro powerful massage ❤❤❤❤
God bless you mary❤❤❤❤❤
Mbambande mai, congratulations for your clarifications how the situation it is in Malawi.
❤ Mai wa nzeru keep it up
Our mother Malawi ❤❤❤❤❤❤ thanks a lot Mom we love you and tikudikilira kukuvoterani Adad athu akulowadi m'boma pompanopa ❤❤❤
Respect mayi wathu ❤❤❤
Muli bwino mama APM boma
Mai Navitcha osabwelera mbuyo keep it up
Keep it up mama❤❤❤❤
Congrats mother❤
Ulemu wanu ❤❤❤❤
Ulemu wanu mama ❤❤❤❤❤😊😊
Yes
I like you mama just be strong 🎉
Maiwa ankayankha mwau professor tu 😂😂
DPP woyeeeeeeee ❤❤❤❤❤❤❤❤
Osaiwala APM boma
Powerful ndipo tikuona kuchedwa kwambiri Amalawi talira mokwenza
We're with you mama ❤❤❤
Osadandaula Mai mulungu akupasani mphamvu
Usamubakire sipikayo ndiwaboma iyaaaaa
Powerful mama
chakwera ndi chitsiru leader of oposion sasankha aboma kungoti speaker ndi chitsiru ngati chakwera pamozi ngalu uyu nankhumwayo
Appreciate you mn
Navitcha ndi nkangala doro captain makina katundu wa boma❤❤
God bles u mai
Love 💕 you Mama.
Mai wolimba mtima keep it up
Tonse and dpp haha chimodzimodzi
Ndifeyo a DPP
Asiyeni azimuwombera manja nankhumwayi sakuziwa kuti ndamenenso wathandiza kuwononga zinthu checking and balance yi isiyeni choncho nthawi yatha kale iyi. Mcp akangoyamba kuzikonza zizakupangisani kuti musazawine.
❤❤❤❤❤❤❤mama
We love u mum bt don't play with mcp bicoz they're so dangerous pipo
Leader of opposition siuyu
Wise woman 👩
Mayi navicha akanakhala kut mwina siwoyelako bwenzi akuwoneka bwa nkhwangwa yeniyeni
❤🎉Mai
🔥🔥🔥🔥🔥
❤❤❤❤❤
Moto ku booooo mom
Chipani Cha family...zachikalekale
❤osaiwala APM NDIYE CHIDA CHOPHERA CROCODILE PARTY
APM ❤❤❤❤❤2025🎉
Nchonyozo wakwathu ulemu wanu mai mlungu akhale kumbali yanu APM amatha
Mayi Navitcha kumeneko nde kunena chilungamo
I like you Mon ❤❤❤❤
Mwala wamaziko ndiwaDPP kkkk MCP does it
Mumatha ma
❤❤❤❤❤❤
Anavitcha takudarirani Ifeyo osamusekerela chakwera ayi mukatelo Ifeyo tikutayani
♥️♥️♥️♥️♥️♥️♥️
Apm 2025❤❤❤
Court Order vs Standing Order which is more functional than the other in parliament?
Mulungu akudaliseni mom l love you too
Osafoka mai wathu
I know this woman shes woman of God
Mumatha mama
Wathuthu Mary navitcha asafuna asiye
Awuzeniso kt ma speaker woso ndi a mcp
Hule uyuuu kd wapenga boma lake litiiii😂😂😂😂😂
Osamaika khope yako adha
Azikhala ngat Bakili Muluzi TV samaika pic yake.
Kd ndinu mai mumatukwana a nsonda?
Shaga fologonya
Kkkkk mpaka Professor enanu mitu idauma basi?😂😂😂😂😂😂 Pepani
mamawa amakwana
Mafunso amenewa mumalephera kuwafunsa anthu achipani cholamula kuti akupanga chani, mumangowanvera akamakunamizani , koma otsutsa ndiye kuwapanikiza
Too late where u was b4
Mai inu mulungu akudaliseni kwambili ndipo musafowoke ndithu
Dpp munthokoze nankhumwa kukhala chete ku parliament wasokoneza zinthu mboma la mcp checking and balances ija it's a good strategy osakhala nayo busy.
Zandale izi tisamachedwe nazo tizafa osauka andale akulemera
Kodi andaleso amakhulupilila mulungu weni weni amene adatilengayo
11:02 mmmmm being a lop doesnt mean that you are an enemy to the government mmm
Mayi Navicha muli pachilungamo
Mcp down
10:48
Mayi mbambande tatopa ndi namachende galu nankhomwa boyfriend wa gotani hara
Koma akulu musamaoneke pa screen apo ayi,sizoneka bwino,tidzingoona anthu awiri okhawo basi.
Nankhumwa sadziwa ndale machende ake akagwele uko
😂😂😂😂man mwandisangalatsa bwanji
Zabwino zabwela titakhuta kale Umphwawi utati pwasamula mayi wamzeru ngati uyu anali kuti
komatu zimayiyu atati akayimire u president wa DPP athakukawina mosavuta ameneyu arindikuthekera kotsogorera ndinthu
Speaker ujatu.. ndi hule. amanyengana.. ndi. Nankhumwa. Komanso. ndi wa. MCP. ndi chifuwa. amakondera hule
😂😂😂😂😂😂😂😂
Mayamba bwino mama,
A speaker nayeso ndi galu akutengela za chipani cha mcp Chipani chankhanza
Munachita bwino osamasusa simwawona dziko lawonongeka koma mukanati muzisusa mukanathandiza kukonza zinthu akanazalowa mboma mosavuta koma apa nde mwayiphura amawona ngati madolo kumalimbana ndi inu chete wa nankhumwa wakuthandizani inu a dpp kuti muzaduse moyera.
😂😂😂😂
Very incoherent statements, koma mwati sukulu zuti bwanji? 😂😂
Apm boma 2025
Some questions from the host....very useless
DPP has to learn to identify and deal with its enemies. APM has to know this is not US this is Africa. Ndale imakhala yothana. Wake up DPP.
simungawine u are waisting ur time on fighting
Ukunama iwe dpp izawina ufune usafune
Akulu inu si m'malawi
Omwe mukuganiza zoti awinawo nde apanga chani