Apanga izi kuti azabere chisankho 2025- APM

2024 ж. 24 Сәу.
13 619 Рет қаралды

@changemalawi2025

Пікірлер
  • Dpp 2025 ndiyomwe tikuyifuna zinaz tatopa nazo

    @user-bz7hm9qf4u@user-bz7hm9qf4u24 күн бұрын
  • Azibusa okwela chikhoma mkumalalikla amakhala abodza ndaonela a president athu aku malawi, munthu olemekezeka mbusa koma wabodza, amalawi osavotela anthu a bodza ,mwaona Nokia kumalephela kumwa tea chifukwa cha kudula kwa sugar,malawi akumvetsa chisoni.

    @user-te3ps3kf2t@user-te3ps3kf2t24 күн бұрын
  • Good comment bro your good person bro God you.

    @user-rd4ft9nd8t@user-rd4ft9nd8t24 күн бұрын
  • APM my vote 💪

    @user-is5dl7np9g@user-is5dl7np9g24 күн бұрын
  • I mean you are a good person bro God bless you good comment

    @user-rd4ft9nd8t@user-rd4ft9nd8t24 күн бұрын
  • APM is a good leader, no doubt about that.

    @omarajibu860@omarajibu86024 күн бұрын
  • Apm my vote

    @BensonLipita@BensonLipita8 күн бұрын
  • APM my vote

    @user-ev6bi7jr7g@user-ev6bi7jr7g24 күн бұрын
  • MCP tikuzatha nawo tizavota opanda ma ID, APM bomaaaaa iloooooo ❤❤❤❤

    @user-uc1pd1tc2x@user-uc1pd1tc2x24 күн бұрын
    • 😂😂😂😂😂😂😂 ma rubbish okhaokha Dpp siingazawineso sure mark my words

      @talimilejosephmakawa4967@talimilejosephmakawa496724 күн бұрын
    • @@talimilejosephmakawa4967 Ukunama adha uwonanso lija ndi Boma lokhazikika mnthesa njala eni nkhokwe

      @user-uc1pd1tc2x@user-uc1pd1tc2x24 күн бұрын
    • Only wicked people support the wicked

      @chrischiwere7279@chrischiwere727923 күн бұрын
  • Perfect ❤❤❤❤

    @SolomonNjolomole@SolomonNjolomole19 күн бұрын
  • APM woyeeeeeee ❤❤❤❤❤

    @user-uc1pd1tc2x@user-uc1pd1tc2x24 күн бұрын
  • Komatu mau oti conservation nde mwawakondatu. Tiyeni tiziyankhula chichewachi aaaaaa🏃🏃🏃

    @liki-likiladies---lilongwe6963@liki-likiladies---lilongwe696319 күн бұрын
  • Anthu enewa amayakhura ngati ndi wopemga kaya ndi ndarama zimene amalandira kwa chakwera kaya panopa basi winawake aziti akufuna president wa chinyamata kodi amene alipowo akuzuza a Malawi ndi wokaramba za ziiiii

    @marryphili5419@marryphili541924 күн бұрын
  • Fine vidios

    @AcksonKamwanza@AcksonKamwanza24 күн бұрын
  • DPP woyeeeeeeee ❤❤❤❤❤❤❤❤

    @user-uc1pd1tc2x@user-uc1pd1tc2x24 күн бұрын
  • Tizingobandulanapo apa yamanja basi kwasalaku

    @WilsonLimited-os1xd@WilsonLimited-os1xd24 күн бұрын
  • Sizitheka tizavota opanda ma ID otherwise tizapha Chakwerayo

    @user-uc1pd1tc2x@user-uc1pd1tc2x24 күн бұрын
  • Ndipo chonde tigeilizane amalawawi tiyeni tikavotele adad osati chikhanila chimenechi chi chakwela bola adad ngakhale amafooka pena koma ndi muthu wachikondi ndipo akozaso zikoli mwinaso kuposa pamenepaja chifukwa waphuzila zambili ndipo akudziwa chomwe amalawawi akuchifuna ndipo Malawi asitha ndithu

    @user-eh1mg3ww6d@user-eh1mg3ww6d10 күн бұрын
  • Congress

    @user-hq6dq7zr1e@user-hq6dq7zr1e24 күн бұрын
  • Truly truly truly

    @user-jc9gy9ou3v@user-jc9gy9ou3v23 күн бұрын
  • Same applies to me, APM Vote

    @VincentNyabanga-dw9uj@VincentNyabanga-dw9uj24 күн бұрын
  • APM, ndi munthu okonda dziko lake la malawi, dpp bomaaaa, 2025

    @user-lg6om6wr8z@user-lg6om6wr8z20 күн бұрын
  • Apm ❤❤

    @user-oh5vs1gl4n@user-oh5vs1gl4n24 күн бұрын
  • Nkhani zobera mavoti ndi nkhamba kamba pslibepo...Nkhani ndiyoti ovotawo asankha basi

    @paulmakaula4937@paulmakaula493724 күн бұрын
  • APM bomaaaaaaa 2025

    @user-do2cs8nf4b@user-do2cs8nf4b24 күн бұрын
  • Bro one love comment yabwino

    @bokaalfan9146@bokaalfan914623 күн бұрын
  • We are indeed really tired with this government

    @LysonMtalika-tb6fk@LysonMtalika-tb6fk23 күн бұрын
  • Adad boma 2025 ❤❤❤❤❤

    @JenipherAlick-kd8pq@JenipherAlick-kd8pq24 күн бұрын
  • DPP WOYEEEE

    @hanifahmponda8711@hanifahmponda871124 күн бұрын
  • Onyoza Peter wa mutharika mitu yawo,

    @Anthonymendos@Anthonymendos24 күн бұрын
  • MCP lpanidwe tiyeni tigwilane manja amalawi please please boma lri lipha anthu ambiri 😢

    @Islammasiye-qg6lz@Islammasiye-qg6lz24 күн бұрын
    • Yes

      @user-lf6qf2tw5o@user-lf6qf2tw5o19 күн бұрын
  • MCP useless government

    @VincentNyabanga-dw9uj@VincentNyabanga-dw9uj24 күн бұрын
  • Ndiyekuti nawonso nabera Joice banda. Sleeping on duty sangawine . Angopuma basi

    @user-eo2ol3ww8h@user-eo2ol3ww8h24 күн бұрын
  • 😂😂❤

    @AmonSugar@AmonSugar24 күн бұрын
  • zaziii

    @user-pl6it7zc7c@user-pl6it7zc7c20 күн бұрын
  • Tikudikila inu adandi coz munatisiyatu malele

    @MaxwellChidothe@MaxwellChidothe24 күн бұрын
  • Ukuti tizibandulana ikubandule ndinjala muzimenya anzanu abwanawo zao zikuyenda kkkkkk

    @user-rd4ft9nd8t@user-rd4ft9nd8t24 күн бұрын
  • Alomwe kwanu kunatha asiyileniko anzanu sitikukufunani

    @user-gj4li2gc8o@user-gj4li2gc8o24 күн бұрын
    • Ukunama mulungu ndiwakutha satana achitamayazi

      @EllenLuwanika-tl5ck@EllenLuwanika-tl5ck9 күн бұрын
  • Chakwela zamanyi zakozo tiyambisa mkhondo

    @user-pj3qi7gb3s@user-pj3qi7gb3s24 күн бұрын
  • Zandale zikuphani

    @jameskingnsima3978@jameskingnsima397824 күн бұрын
  • man apo ndipakamwa koma musaiwale mwina munali amodzi mwaiwo umudyela ndalama palimbe chazelu chiomwe muthialika angapange muno ife ayi wakalamba

    @mathewssiliya574@mathewssiliya57424 күн бұрын
  • Zoona

    @JusticeMitigolo@JusticeMitigolo24 күн бұрын
  • Kalimbanani ife pano tikugulitsa fodya ndi chakwera $3.11 utisokosela zimenezo mlimi agafune apm ndani amatibera fodya uja

    @kingsleyhopematchaya5184@kingsleyhopematchaya518424 күн бұрын
  • Welll spoken apm my vote🔥🔥🔥

    @eliffagondewe8214@eliffagondewe821424 күн бұрын
  • Ngati kuti DPP izalephele kulowa mmboma ndiye bola chipani china chizalowe koma mfitizi zichoke basi

    @user-zg7iw8kq4r@user-zg7iw8kq4r23 күн бұрын
  • Kodi amalawi mukufunanso Mutharika azakulamulireninso?amalawife tulo kwabasi ,munthuyo wakalamba basi.apume basi,poti amalawi simumachedwa kuyiwala.why him only.we've got young stars and integrity people who can carry our country forward.poti ndinu atulo muzamuvotela ameneyo.very shameful to my brethren

    @OliverChimsewu@OliverChimsewu24 күн бұрын
    • Iwe ulibe okaramba kwanu sasogorera mbumba ufuna ukambe chani iwe

      @VincentSibu@VincentSibu24 күн бұрын
  • Abwana tilembetsa bwanji pamene maboma ambili sizikutheka zikutheka ku lilongwe bas nde amenewo tingowasiya choncho bas zobela zawozo apange ndithu tidzawonesana pansewu kudzakhala mademo owopya kwambli abwana asiyeni atase mmene angathere

    @IMEDISHAMILA@IMEDISHAMILA24 күн бұрын
  • Inenso ndinaimva bwino kwambiri

    @derekkolopo-ch7mb@derekkolopo-ch7mb24 күн бұрын
  • That's true

    @user-qp3gk8cj9g@user-qp3gk8cj9g24 күн бұрын
  • Mwakhalamo m boma anzanthu nawo adyeko ndalama zamalawi dpp out sitikufunaso kuti achilbino azizakhala ndi matha

    @user-pt8wb4vw6r@user-pt8wb4vw6r24 күн бұрын
  • Anganga kulibe tipex pano yimene mnapanga inu wakalamba wakalamba siyilani anyamata achina namalomba awa akungofuna ndalama basi

    @user-pt8wb4vw6r@user-pt8wb4vw6r24 күн бұрын
  • Tiyeni a Malawi tiyambise mkhondo

    @user-pj3qi7gb3s@user-pj3qi7gb3s24 күн бұрын
    • It must be after election izayamba

      @HanishaissahKagansa@HanishaissahKagansa23 күн бұрын
  • Iwe mbuzi petro ku zambia ,Mozambique, Tanzania ndi okwera kupambana ku malawi ndiye kwinako anakweza ndi chakwera? Fertiliser anakwera palipose ku uk anakweza ndi chakwera mbuzi yamunthu dpp inatha vomerezani chipani cha banja

    @kingsleyhopematchaya5184@kingsleyhopematchaya518424 күн бұрын
    • Did they devalue their currency too?

      @chrischiwere7279@chrischiwere727923 күн бұрын
    • Mamuna yemwe mutu wake sugwira amayangana kwa neba than kukoza za nyumba mwako mkufoira

      @SolomonNjolomole@SolomonNjolomole19 күн бұрын
  • Dpp, nthawi imeneyo,inachitaso chimozi mozi.lero,asalile😢😢😢,chimene,chilipo, anthu angowona,kuti if,ngati izi,zingachitike, what people of Malawi,as a citizen,tidzatani?

    @HarrisonMwanga-xy4sc@HarrisonMwanga-xy4sc24 күн бұрын
  • DPP inatha isazabwereso

    @user-fq3wz5dd2s@user-fq3wz5dd2s24 күн бұрын
    • Koma ikuramuliratu uwona dikira

      @VincentSibu@VincentSibu24 күн бұрын
  • Peter muthalika ndi galu wakuba chitsiru racist nyani pusi nkhwele

    @user-nj5vu8cd5l@user-nj5vu8cd5l16 күн бұрын
  • Tilembesa bwanji olembawo akulemba kulilongwe, kokha,

    @user-pj3qi7gb3s@user-pj3qi7gb3s24 күн бұрын
  • These are all lies and I wonder where the TV is based

    @josephMandala-hk4xs@josephMandala-hk4xs17 күн бұрын
  • Akuti akudzala ma tower obela mavote Titan ifetu lazalo watikwana

    @AhmadumkomaTambala-lr9gp@AhmadumkomaTambala-lr9gp24 күн бұрын
  • Nonsense

    @nahayopaulkim9097@nahayopaulkim909724 күн бұрын
  • Nkhaniyo nde ndiyoona tidzavote ndi chilichose not ID yokha ayi

    @IMEDISHAMILA@IMEDISHAMILA24 күн бұрын
  • Mcp out

    @user-ln3zx6wo4w@user-ln3zx6wo4w24 күн бұрын
  • Biased presentation. Don't bring your own ideas. Mwalandila zingati kodi?

    @kunkumbira@kunkumbira24 күн бұрын
  • Ukakhala wakuba umaonanso ngati anzakonso ngakuba

    @redetembo3249@redetembo324919 күн бұрын
  • APM bomaaaaaaa 2025

    @user-do2cs8nf4b@user-do2cs8nf4b24 күн бұрын
  • Tizingobandulanapo apa yamanja basi kwasalaku

    @WilsonLimited-os1xd@WilsonLimited-os1xd24 күн бұрын
KZhead