PP YAZUZULA MCP26 April 2024

2024 ж. 25 Сәу.
15 808 Рет қаралды

Пікірлер
  • Ngati saulula zomwe agwizana ku Israel, ndiye bwanji amaitana atola nkhani? Za ziii!

    @user-pv9uk6sc3w@user-pv9uk6sc3w11 күн бұрын
  • Ashilungamo amakhala opondelezedwa bass asule MN akwalakwila kukamba shilungamo

    @user-tg1ms3us6k@user-tg1ms3us6k11 күн бұрын
  • Nyanja yagulitsidwa ku Tanzania now anthuno kumalawikuno tikugulisidwanso ku Israel ndi MCP😢😢😢😢

    @user-uc1pd1tc2x@user-uc1pd1tc2x11 күн бұрын
  • Everything that is hidden carries some air of being sinister...

    @FefieTenisha-du7ge@FefieTenisha-du7ge11 күн бұрын
  • Iwe mzimayi joyce ndiwe osokoneza.unawatengera a Malawi ku ulamuliro wa nkhanza.

    @abdulrafiquekalembo469@abdulrafiquekalembo46911 күн бұрын
  • Joyce Banda asamadandaule, coz iyeyo ndiamene amatilozera kwa chakwera kumat ndi m'busa ndie lero astitopese ife tili ndi maso ndipo tikuona zonse zikuchitika.

    @JonesChingaya-yf4gg@JonesChingaya-yf4gg11 күн бұрын
  • Amukazaona mtsogoleri akuti zina tinena koma zina ayi ndizachisisi muziwe kuti musogoleri yo alibe zeru akuziwa kuti zachisisizo ndizopanda pake anthu azeru akana ndichifukwa akunena kuti ndizazisisi paja mukuziwa kuti tili ndi atsogoleri a mbuli zaku Israeli zo sakuwuzani

    @thulanimpphiri6873@thulanimpphiri687311 күн бұрын
  • A Joyce Banda mwakalamba inuuuu. Punulani a Mai.

    @mchipengule@mchipengule11 күн бұрын
  • Ukuyitha hot 265

    @samsonmtumbati4855@samsonmtumbati485511 күн бұрын
  • Mama nthawi ya Amai idatha,,,,,inu or nokha azkhare Zaka ziwiri mongogwirizira mwaruza kkkkkk musiyeni Peter or atupeli alamure Malawi

    @user-yg9em7qq2v@user-yg9em7qq2v11 күн бұрын
  • Chabwino sindikuchiona ulamuliro wa chakwera

    @user-vl5on2lj8b@user-vl5on2lj8b11 күн бұрын
  • I want my Job ,as the president promised me ,1000 jobs😂😂

    @user-im7sc2my4w@user-im7sc2my4w11 күн бұрын
  • Kodi chakwera ndi nkhumba chadzelu ndi chiti

    @FrynessMoyo-to2du@FrynessMoyo-to2du11 күн бұрын
  • Makape bwanji mukubisa zomwe zili mu mgwilizano wanu ndi Israeli? Kapana mukuwagulitsa anthuwa etill?😢😢😢😢😢😢

    @user-qm1qb2jp4s@user-qm1qb2jp4s11 күн бұрын
  • Kodi mayi Inu mesa chipani chanu munachigulitsa ku MCP inu

    @user-tb6yh1kx3o@user-tb6yh1kx3o10 күн бұрын
  • NO PAIN NO GAIN MALAW PAMALONDA MALAW 4SALE

    @user-gx5ht9gm3z@user-gx5ht9gm3z11 күн бұрын
  • Chimene akubisira ndichani

    @user-dy4gc2hr5e@user-dy4gc2hr5e11 күн бұрын
  • Boma lalephera apa, chifukwa akanayamba ntchito za ulimi kokuno ku Malawi kuti achinyamatawa adzigwila ntchito konkuno.

    @user-pv9uk6sc3w@user-pv9uk6sc3w11 күн бұрын
  • Zomwe akuti saululazo ndiye kuti ndi ukapolo umenewo,ngati ndizabwino bwanji sakuulula

    @KimChisola-gm7yw@KimChisola-gm7yw11 күн бұрын
    • Ndipo muli Zoopsa mumgwirizanowo

      @user-uc1pd1tc2x@user-uc1pd1tc2x11 күн бұрын
  • Akayambe zaulimi ku Mallawi kuno muwapatsa chiyani ku Malawi kuno anyamatawo 😂😂😂

    @mchipengule@mchipengule11 күн бұрын
  • Wanzelu sanganyamukile dala waku Israel

    @gabrielben-vj2eb@gabrielben-vj2eb11 күн бұрын
  • One million jobs 😢😢😢

    @HanishaissahKagansa@HanishaissahKagansa11 күн бұрын
  • Why not saying the agreement with Israel.....? We got friends and families there😢 Eeeeeish this is hectic 💔

    @malawigeneralguide1646@malawigeneralguide164611 күн бұрын
  • Mayi Joyce banda akudandaula chani poti ali mu mcp mo paja musayiwale kuti mcp imatenga nyasi. Za suleman ndizovesa chisoni ngati akuti sangaitanidwe kumukumano poti ali ndichileso nanga chilima wapita bwanji ku Tanzania pamene ali ndichileso. Kodi boma la mcp mitu yikuyenda koma mwina wose ndiopenga akupanga zinthu mopeoera wina kumulesa wina ayi useless people

    @thulanimpphiri6873@thulanimpphiri687311 күн бұрын
  • A Malawi tiyeni tiphuzile kuyamika 😂😂😂😂

    @mchipengule@mchipengule11 күн бұрын
    • Chomwe ungayamikile apa ndichani? Chamzelu apa ndicha

      @Austinnkhula@Austinnkhula11 күн бұрын
KZhead