Mpakana Hanifa....aaa Dr Chilumpha mwamuwonerera et sanakukane bwanji?opanga interview ndi nkuluyu ndi achina Joab,Brian ndi enawo not pa Hanifa hiyaaa
@andrewkalima23 күн бұрын
Sukulu zimantha mwayankha bwino kaka
@MiracleMalichi22 күн бұрын
He is a liar and bitter and doesn’t look nor sound healthy. Issues of agriculture were on point during Kamuzu’s reign!
@Malani4119 күн бұрын
Kuthandizir kulemb malamul achikafir ndiy udapindul chiyan popez kt uko ndikukulat iwe
@yusufsadic293024 күн бұрын
It was really bad
@user-gt8nn5ic1v17 күн бұрын
Kumaso anagulisa mafacktale monga riverbothers ndi mafacktatale ambili akamzu banda ndi pamene zithu zinayamba kuvuta
Well spoken Mr Chilumpha
Timakunyadilani Dr
We all know you doc chilumpha❤
Waiting p2
Simunampatse Ulemu munthuyu...simungamuuze kuti azipange introduce yekha ...uyu amafunika Exclusive interview osati izi mwapangazi
Zoonadi
Kaka anga awa
Muli nzeru ndithu
dR cHILUMPHA NEED TO REST ....PHEEEEEEE
My vote
Mwasowa zokomenta et
Iweyo wakuuza ndani kuti ocoment
Mzimu wa chidziwitso amalawi ambiri aribe kamba ka tsankho
1949,1981,1990 nthawi kunali njala yoopsya
Timakunyadiran kaka wathu
Zokondweretsa kumva abwanawa kubvomereza za kuwonongeka kwa dziko though akunamizira mabungwe akunja kuti ndi oipa.
Nawe iwe awaa akutitaitda nthawi, ngati ayamba kuiwala pano😊
Ndatolapo chuma pa mawu anu kaka
Doc. Na pa nkhani ya fertilizer, Kamuzu Banda fertilizer distribution was universal
Mwati akufuna kukhala pulezidenti wa dziko? Komatu inuu!!!!! Aaaaaa
Kuyankhula Kwa bho
Kaka ndimunthu wozichepesa mpakana Hanifa next ndi interview ya jokes
Akuluwa kundaleku simbali yawo
Koma chani?
Kaka ndi munthu oyenelera bas malinga ndi mmene akufotokozera
Kaka
Mwakalamba kaka, inuo mudaona akuphedwa athuwo eti? This is a new generation tell us only the nows
Iwet wabodz Ndipo mtim siuvala sanza Iweyo wakuliram ukuganiz kt ungalamulir
IMF, (International Monitorly Fund ndiyoyipa
Mpakana Hanifa....aaa Dr Chilumpha mwamuwonerera et sanakukane bwanji?opanga interview ndi nkuluyu ndi achina Joab,Brian ndi enawo not pa Hanifa hiyaaa
Sukulu zimantha mwayankha bwino kaka
He is a liar and bitter and doesn’t look nor sound healthy. Issues of agriculture were on point during Kamuzu’s reign!
Kuthandizir kulemb malamul achikafir ndiy udapindul chiyan popez kt uko ndikukulat iwe
It was really bad
Kumaso anagulisa mafacktale monga riverbothers ndi mafacktatale ambili akamzu banda ndi pamene zithu zinayamba kuvuta
Naononga ndziko inu puman
Nthawi yakamuzu kunaalibe njala koma nthawi yaudf kunali njala yoopya ndipo zinthu zikwela kwambiri komaso kunali katangale woopya ndipo zinali zovuta
Inde sindinabadwe tine ya kamuzu km 1992 kunali njala pa history ndy tisanamizanepo pano
Ukunama 1949,1981,1990 kunali njala yoopsya
Don't waist our time
It's waste and not waist 😂😂😂😂😂
Ati waist 😂😂😂