ZOMWE WAYANKHULA JOYCE BANDAHanifa Mw 2024 ж. 20 Сәу.10 511 Рет қаралды Share Tweet ЖүктеуINU ZOMWE WAYANKHULA JOYCE BANDA
Hule wandale iwe ndiye ayi wakuba iwe mfiti my is for Apm❤❤❤❤❤
Takuvani kma vot yanga sinkupasa APM my vote🎉
Apm my voti❤
😂😂😂😂😂 munagulisa dege iwe my vote Apm
Ndege yathu ilikuti Mmai iwe
Vote Apm ... mai asowe
Kkkkkk the. big boss chilima saulo my vote
APM my vote
Manyazi ayi, Ku malawi
Dpp ndi peter zinaba kwambiri bwa osasipumisa ayi Joyce naweso uyime
Anthu osakonda dziko lanu in muyambisa kuononga malawi NDI inu
Kkkk SKC my vote ❤❤❤❤
Uyu ndiamene anabwelesa chimpilikiti Malawi Muno chokuba wandale ndimfitidi timaona Ngati mayiyu mwina athela kumakhala ndimanyazi koma ayi ndithu
Apm mbaliyanga
Kkkkkk ajoy manyazi mulibe Kodi Cash gate
Cash gate a again is coming 😢😢
MayiJoyce banda takhalani pasi musayime ndinu woluza kale.
Zikungovuta koma akunena chilungamo
Mbava iyi osakhala ndi manyazi, Joyce ndi Chakwela the same ndi mwana wanu Chilima mbava zokha zokha
Mwaona kuti zomwe unawauza Malawi sizinachitike sopano mwati bola muthawe komatu pali mawu onenakuti somba zikaola mundengu ndikuti zonse zaola pano musabwele ndi boza kumene mumangwilizanako zonse zilinali zabwino bwino 😂😂
You were put to the test but what people can remember about you are just trivialities....cashgate and presidential jet saga...tazikalerani ana mamma
Abiti cashget
Chilima my vote
next president SKC
Udapusa hure iwe wachabe chabe
Mwai abweranso ataona kuti chakwera palibe akuchita ,mwaganiza bho mai Koma vote yanga ndi APM
Mmai wakuba ukhaula
Mwachita bwino amayi kut muzayime nawo pa masankho ,muzagawane mavot akumwera ndikupasa moto chakwera azaduse bwino
Usavutike lwe ukumenya kampeni ndimayesa uli limodzi ndi bushili mukufuna mupulule anthu
Cashgate unakadyera Ku America iwe mzimayi oipa iwe
Tiye uko kapolo
Mphechempheche mwa njobvu salowamo kawiri munaba zokwanira karereni dzizukulu basi
Kkkkkkk
Hahaha
Azungu andituma, Azungu andituma shut up woman.
Shameless woman
This woman she's a lie
APM my vote