Zomwe Wayankhura Patricia Kaliati Zadabwitsa Anthu

2024 ж. 5 Мам.
26 382 Рет қаралды

Zomwe Wayankhura Patricia Kaliyati Zadabwitsa Anthu

Пікірлер
  • Anthu ena anangobadwa opanda manyazi ndikuyankhula.komanso anthu ena timasowekera wisdom from God kumangosatira zilizonse.zoona anthu omwewa ndiomwe anatipusisa leronso tikuwasatilanso bac atimbwititseso?koma aliboma momwemo palibe chomwe akupanga ndiye anthu opanda uzimu akuwatsatilabe komanso adzazivoteranso zitsiluzi.

    @eliaskhofielias8152@eliaskhofielias81527 күн бұрын
  • Chonde amalawi, amzanga osaononga vote kamba kokuti akukunazani ndi ma ti shet kapena msalu musamale.

    @LovemoreSalima@LovemoreSalima9 күн бұрын
  • Huleyutu wayamba Tikuthamangitsatu ndi maduka, Usamale hure iwe.

    @LovemoreSalima@LovemoreSalima9 күн бұрын
  • saulo Ali muboma chipanga iye ndi chani chanzeru.

    @lloydmalinga1198@lloydmalinga119813 күн бұрын
    • Nzeru ulibe iwe sukuona adayimisidwa ntchito kuti ngwa Kuba, ndipo wakhara asakulamura nawo, pano mwina poti akuti milandu isapitilire umboni alibe siolakwa

      @isaihmagani5697@isaihmagani569713 күн бұрын
    • 😢tachokani okuba inu ,mumubelenso ndani mmanyamula thumba la fertilizer paphewa palibe mwachita inu

      @phirimacdonald8638@phirimacdonald863813 күн бұрын
  • Mmmmmm ayamba kunamanso koma amalawi tikamvera izi ndife omvetsa chisoni

    @inessmsiyambiri8517@inessmsiyambiri85178 күн бұрын
  • Ufiti ulipodi ku Malawi 😢😢

    @FrankKambwani@FrankKambwani9 күн бұрын
  • Mmzimayi oipa manyazi alibe garu wen wen☝️

    @JasonJackets@JasonJackets13 күн бұрын
  • Mau amati awiri sayenda limodzi asanapangane, inuyo m'mene mumalowa mu alliance munagwirizana lero musayambe kusintha chichewa kamba koti zakuvutani. Zipitani tiyese anzanu, anzeru si inu nokha ndi a Chilima kulinso ena.

    @JonesChingaya-yf4gg@JonesChingaya-yf4gg8 күн бұрын
  • Uyu adameza memory card eeeee!!! Wayambapo Zonama zakezija.

    @Blessings-td4cr@Blessings-td4cr13 күн бұрын
  • kuonera live from south Africa mumakwana more fire

    @user-pl6it7zc7c@user-pl6it7zc7c13 күн бұрын
  • 😂 zazi palibe chomwe ukukamba pamenepo 😂😂😂😂 kagwele uko

    @HarryRefred@HarryRefred4 күн бұрын
  • Wazipeza zitsilu Ku chiladzuluko, osakuthamangitsa?

    @LovemoreSalima@LovemoreSalima9 күн бұрын
  • Zatha nfundotu, mungobweleza za kale mumawanamiza amalawi zija. Kuatengela amalawi ku mtoso basi. Olo manyazi mulibe.

    @mcsellahntv6896@mcsellahntv689613 күн бұрын
  • Pepani mayi, your time is gone. You are all failures. Now is time for DPP, UDF and AFORD. Enanu mukagwere.

    @omarajibu860@omarajibu86013 күн бұрын
    • Dpp uDf AFoRD my vote

      @EllenLuwanika-tl5ck@EllenLuwanika-tl5ck13 күн бұрын
    • Aah thawi ya Dpp inatha

      @chiluzbandah@chiluzbandah8 күн бұрын
    • @@chiluzbandah mukunama

      @EllenLuwanika-tl5ck@EllenLuwanika-tl5ck8 күн бұрын
    • @@EllenLuwanika-tl5ck tiyeni tidikire

      @chiluzbandah@chiluzbandah8 күн бұрын
  • 😂😂😂Sewelo latikufelanji anthu abodza awa

    @ThoccoBondo-mx7vt@ThoccoBondo-mx7vt11 күн бұрын
  • Manyaka weniweni🥺🥺🥺

    @sthoramexjrsa902@sthoramexjrsa90213 күн бұрын
  • Palibe chanzeru mukukamba inu, Chakwera anakupeperesani kale apa Chilima wanuyo azamuvotera ndi ambuyake .kodi a Amalawife mumatitenga ngati zitsiru eti

    @hmshohagshohag9483@hmshohagshohag948313 күн бұрын
  • Bodza la 2019/2020 lija mwayambiranso? I don't know what you guys gonna say this time. You can't fool a Malawian again, your time is over.

    @omarajibu860@omarajibu86013 күн бұрын
    • Akaliati zauhule basi kuyela kogulako mbudzi yamunthu zausilu basi ndi galu wakoyo chilimayo

      @mustafailanga2585@mustafailanga258513 күн бұрын
    • Akuti nsomba zikaola mundengu nde kuti zonse zaona awa asatimize ayi zisilu zaathu

      @user-hy4el8ov1l@user-hy4el8ov1l13 күн бұрын
    • Akwafusa athu kuti kondi simumadya kawili akuti zimene zija zodya kawili zo zinali za UTM akuti kasala kamozi komaso athufe timangosekelela zilizonse

      @user-hy4el8ov1l@user-hy4el8ov1l13 күн бұрын
    • Chilima 2025 BOMA lanyowani

      @umalimaganga@umalimaganga12 күн бұрын
    • Chilima 2025 BOMA lanyowani

      @umalimaganga@umalimaganga12 күн бұрын
  • Wasowa chonena ameneyi.

    @user-yk3wc9ei5g@user-yk3wc9ei5g13 күн бұрын
  • Muthu wandale ndi satana lero akubwela ndi boza 😂😂😂

    @user-hy4el8ov1l@user-hy4el8ov1l13 күн бұрын
  • DPP woyeeeeee❤❤

    @innocentnjoka7014@innocentnjoka701413 күн бұрын
  • Musagawe nsalu inu, gawani chimanga ndi kukwanilisa munalonjeza

    @francisvisage2705@francisvisage270510 сағат бұрын
  • Chitan manyazi akwen 😂😂😂

    @user-rd8vw1pc4b@user-rd8vw1pc4b13 күн бұрын
  • anthu andale ndinu oipa inu mulungu azikukhululukilani 100% tikuvutika chifukwa cha anthu andale inu

    @user-qe2lv3hs8q@user-qe2lv3hs8q11 күн бұрын
  • Tachionereni chikuyankhula ichochi apa manyaz bwanj isa upusa bas

    @Creslevison-vj2sl@Creslevison-vj2sl13 күн бұрын
  • Manyazi mulibe iyayi kkkkk

    @Hendersonspoon@Hendersonspoon8 күн бұрын
  • 🎉bodza bodza bodza koma ulibe manyazi.

    @StanfordGoda@StanfordGoda9 күн бұрын
    • Takambani zina, ndiye poti amalawi ambiri tinapoila sitimadziwa chomwe timafuna boza la 2024

      @johnjoachim3820@johnjoachim38208 күн бұрын
  • Anthu osowa zochita awo.

    @PleasantMagombo@PleasantMagombo8 күн бұрын
  • Mai opanda nzeru uyu kuwatenga amalawi ngati opusa eti

    @user-rd6zo8ry2d@user-rd6zo8ry2d13 күн бұрын
  • Kodi kaliati uwe ndi munthu kapena chidzukwa muudze chilima anyamule thumba lafertilizer lija ulibe nzeru chilima wakhala akunama pano angamumvere ndani mbavayo okuba ndi sattar

    @user-hm9nc7lz6e@user-hm9nc7lz6e13 күн бұрын
  • 😂😂😂😂😂Koma mbuzi Izi akatero awanamize anthu kena

    @MaliGomani@MaliGomani13 күн бұрын
  • Mai opanda nzeru akuwatenga amalawi ngt zisiru,

    @user-rk3jx3kg8i@user-rk3jx3kg8i13 күн бұрын
    • ife pambuyo pa adadi osati onamawa ,achilimaso ndi kape anali kuti

      @user-oh5vs1gl4n@user-oh5vs1gl4n13 күн бұрын
  • Ukuzikolakola wekhatu 😂😂😂😂😂 muziwona katatu😢😢

    @HarryRefred@HarryRefred4 күн бұрын
  • Kaliat mulungu akulange😊

    @ishmaeldama8906@ishmaeldama890613 күн бұрын
  • Zaboza zokhazokha eshii amalawi ndiyeno mukusekelela mmmmm

    @PeterPhiri-nd6op@PeterPhiri-nd6op13 күн бұрын
  • Amp my vote

    @user-iu3bf6oe1x@user-iu3bf6oe1x13 күн бұрын
  • Kukamwa konyasako mai iwe osamakayamikira amuna ako bwanji mxiii!

    @jamesgama5489@jamesgama548913 күн бұрын
  • Manyaz mulibe mai nd chilima wanuyo kagweleni uko

    @user-wi9pe2hz7e@user-wi9pe2hz7e13 күн бұрын
  • Kuyankhula kwa bwanji uku mukamati munangowalawitsa anthu, kusowatu chonena uku

    @JamesMalango@JamesMalango13 күн бұрын
  • Mwachedwa

    @LinessiTambala@LinessiTambala13 күн бұрын
  • Mbuzi iweee

    @user-vu9rt8gj3o@user-vu9rt8gj3o13 күн бұрын
  • UTM my vote

    @user-jr1kq9vc7n@user-jr1kq9vc7nКүн бұрын
  • Kweee is back....💪

    @llewellynkhungwa4712@llewellynkhungwa471211 күн бұрын
  • DPP WOYEEEE!!!

    @fatsanichibwana9438@fatsanichibwana943813 күн бұрын
    • Dpp tatopa nawoo apanga Chali mbili zakale

      @user-le9su3mt7r@user-le9su3mt7r13 күн бұрын
  • UTM my vote❤❤❤❤❤❤

    @user-qp8kh2hj9o@user-qp8kh2hj9o9 күн бұрын
  • Manyazi mulibe

    @chikumbutsomarch4484@chikumbutsomarch448413 күн бұрын
  • Panyinipako hele iwe komatso nyiyamako nyiya iviyo

    @YohanePatrick-lc2lq@YohanePatrick-lc2lq13 күн бұрын
  • Mayi asazampatsabe mpando,anthu oipa akuononga dziko ndi awa

    @lingstonenagoli7729@lingstonenagoli772912 күн бұрын
  • Kupepera zedi uku muuisova DPP ikulowa m'boma itchetcha afiti nonse okubanu

    @user-uc1pd1tc2x@user-uc1pd1tc2x13 күн бұрын
  • 😂😂😂😂😂😂 so funny the take Malawian for granted. Wht is doing now is in the government mxm

    @chrisschikozera7271@chrisschikozera727113 күн бұрын
    • You are very correct

      @AlidiNgalande-ou7ig@AlidiNgalande-ou7ig13 күн бұрын
  • Sopano apa muli muboma bwanji osapanga zosezi agalu inu

    @PeterPhiri-nd6op@PeterPhiri-nd6op13 күн бұрын
  • Hule uyu ali ndikukamwatu kobowoka kkkkk

    @WitnessKambwiri@WitnessKambwiriКүн бұрын
  • Akweni yokhayi yodya katatuyi Akweni sigwira ataaaaa or pang’ono kkkkkkkkkkk!

    @samsonphangire1523@samsonphangire152313 күн бұрын
  • Patrisha kawanamidze ana ako osakhala wamkulu ngati ine mmanfesto yanun : mwapanga chani mdiwe chisiru iwe kwabasi koma ndiwe wabodza eeeeeeereee satana

    @user-hm9nc7lz6e@user-hm9nc7lz6e13 күн бұрын
  • Mai oposa iwe wasowa chonena watokhuta

    @WhiteRichard-cw2fo@WhiteRichard-cw2fo13 күн бұрын
  • Chilima my vote

    @GladysPhiri-mb7ec@GladysPhiri-mb7ec13 күн бұрын
  • Olo mayi wakuyandikirayo wakhumudwa nawetu kwambiri😢😂

    @InnocentJavelo@InnocentJavelo13 күн бұрын
  • Palibe chamzeru chomwe mukunena mayi opusitsitsa inu, a malawi mwawatola

    @user-is5dl7np9g@user-is5dl7np9g13 күн бұрын
  • Aaaaaaah, musatinamizepo apa, UTM yili mu boma kale mukuchitapo chiani, za bodza basi

    @user-pv9uk6sc3w@user-pv9uk6sc3w13 күн бұрын
  • Onse Alliance sopano, eeeeh! Mbuzi zokhazokha.

    @mcsellahntv6896@mcsellahntv689613 күн бұрын
  • Ulape mulungu akukhululukile

    @StanziaElias@StanziaElias13 күн бұрын
  • Aaaaaaaa nanunso mwasowatu zokamba wadya katatu ndani inunso anthu ndi omvesa chisoni kwambiri fertiliser wosaka mtengo mwamugula kuti mitu yanu mwaiwala nsanga nsanga

    @ThoccoBondo-mx7vt@ThoccoBondo-mx7vt11 күн бұрын
  • Ndinu mai ovesa chisoni mulungu sakondwera ndi boza ngati limeneli

    @user-vp5mf6bd3o@user-vp5mf6bd3o13 күн бұрын
  • Mbuz yosafunikira kaliat

    @binalidjeyshabahzombamalawi@binalidjeyshabahzombamalawi13 күн бұрын
  • Mayiwa ndi aboza 😂😂😂

    @user-hy4el8ov1l@user-hy4el8ov1l13 күн бұрын
  • Ingobwererani ku dpp musowatu cholankhula campaign ikubwerayi.

    @user-xv3ju8yi9n@user-xv3ju8yi9n10 күн бұрын
  • Nanuso pangani chipanda chilima ndinu ndani inu

    @Agness-ic9tl@Agness-ic9tl12 күн бұрын
  • Koma ndiy kuti anthu akamanama samachita manyazi kut akunama anthu akuba

    @WitnessKambwiri@WitnessKambwiriКүн бұрын
  • Mai opanda chikondi inu mukuzanama ka chikena 😂😂😂😂 iamalawi akanali ogonabe shame

    @nathanvanderberg6558@nathanvanderberg655813 күн бұрын
  • Mzimai oipa uyu za dpp unasunga zija ukabweze kwa eni aka adad mzimai oipa iwe

    @user-gx8or3yz9u@user-gx8or3yz9u13 күн бұрын
  • Chokani nonse mukulankhula mbwereranu chifukwa chilimatu paja anamuchotsa mphamvu zonse ndiye mukuona ngati angatani?chakwera ankadziwa kuti chilima simunthu wamva ndiye ndimuchotsere kaye mphamvuzo cholinga asamatsutse komanso asamapange kanthu koma akanamusiira mphamvu zonsezija ndiye pano muzikamba zimenezi zikanakhala dzomveka

    @user-hn8sr9oc7k@user-hn8sr9oc7k12 күн бұрын
  • MAyi. KAyimeni komwe munagwa kuja ngati zomwe munena ndizowona

    @user-et3il7pi7t@user-et3il7pi7t13 күн бұрын
  • owinawina SKC

    @greychizaka4088@greychizaka408813 күн бұрын
  • Anyani Amenewa akufunika mfuti atikwanapo dzikomuno ndiboza

    @achintewhite1894@achintewhite189413 күн бұрын
  • Padiko pako garu iwe

    @rynordmagoli@rynordmagoli13 күн бұрын
  • Mayi mulungu akukhululukileni kwambili koma ndili ndifuso kuti inu mumapemphela?

    @StanziaElias@StanziaElias13 күн бұрын
  • Iwe usatitenge ngati ndi chisiru wamva amalawi timazithandidza tokha sitimadadalira prezdent

    @user-hm9nc7lz6e@user-hm9nc7lz6e13 күн бұрын
  • Kodi mai uyu mutumu muri ubongo ndithu . Ndikukaika kwambiri .

    @robertchitsulo8006@robertchitsulo800613 күн бұрын
  • Apm ❤

    @beinhardkausiwa7107@beinhardkausiwa710713 күн бұрын
  • Galu uyu, ung'omboka 2024

    @allanchangalusa6662@allanchangalusa666213 күн бұрын
  • Vuto simumaziwa kuti vice president ku malawi amachita kutumidwa ndi president, nde ngati president anamuyimisa iyeyo akanatani

    @farlenmkorongo@farlenmkorongo10 күн бұрын
  • Amalawi akadakhala anzelu avotere atupele muluzi..posayang'ana chipani

    @mosesadam-sk2yb@mosesadam-sk2yb13 күн бұрын
  • Onse a ndale ndi a BODZA. DPP, UTM, MCP, e.t.c, e.t.c nga BODZA. Dziko lino likufunika lilamulidwe ndi Asirikali basi. Am tired of the Politicians. Maganizo anga.

    @AngungaThatcherNgoma@AngungaThatcherNgoma13 күн бұрын
  • Apm my vote❤❤Dpp

    @WilliamMsimuko-mx7fu@WilliamMsimuko-mx7fu13 күн бұрын
  • Amai bwererani Kwa APM kumeneko mukuchedwako chabe

    @mitochilukas9170@mitochilukas917012 күн бұрын
  • Tsopano ngat manufesito onse mudalonjeza alipo ndindani akudya ndikugula fertilizer pa mtengo omwe mudalonjeza?Koma Mcp mukuiona bwino ubale wanu mmansomo ukuupenyetsetsa? DPP plus UDF more fire

    @MphatsoIshmaeladam@MphatsoIshmaeladam13 күн бұрын
  • Zaziiiiii😢😢😢😢

    @ChristopherNdalama@ChristopherNdalama9 сағат бұрын
  • Amai awa ndiopusa zedi alibe manyazi

    @SuratAmiduh@SuratAmiduh7 күн бұрын
  • 😂😂😂 koma anthu andale eeesh

    @Mike-du7zt@Mike-du7zt13 күн бұрын
  • Zomvetsa Chisoni kwambili ndipo akamayankhura sachita manyazi

    @GospelSoldiers-sr7np@GospelSoldiers-sr7np13 күн бұрын
  • Mungosiya kupemphela mwamva

    @StanziaElias@StanziaElias13 күн бұрын
  • Koma, mfiti iyiih

    @westednyachikadza6353@westednyachikadza635312 күн бұрын
  • Adadi woyeeeee

    @user-fm5fk1zt1l@user-fm5fk1zt1l13 күн бұрын
  • Zopusa et azakuvotera amako galu Chilima wakoyo azikalamulira kunyumba kwako demet fertilizer K4.595 alikut

    @NgomaRaheem@NgomaRaheem13 күн бұрын
  • Akweni mungobwelera ku DPP komkuja basi zinazi mungotukwanidwapo zamunsalu apa because we are tired of u guys ndi mabodza anuwo fotsek!!!!

    @user-mi3fw1zg8b@user-mi3fw1zg8b12 күн бұрын
  • Mayi opandanzelu kwambili

    @MackdonaldMilanzi@MackdonaldMilanzi12 күн бұрын
  • Malawi wake uti ameneyo😅😅

    @rich6Africamusic@rich6Africamusic13 күн бұрын
  • Anthu amodza inu

    @jeremiahmemmanuel9988@jeremiahmemmanuel998813 күн бұрын
  • Chilima boma akumu nanga chilima moto buuuuu

    @user-le9su3mt7r@user-le9su3mt7r13 күн бұрын
  • Palibe chanzeru chomwe mwayankhula.Ulendo uno simutinamizaso. Malawi pano adazindikira ndipo zimenezi muziyankhula mnyumba mwanu nd ana anu

    @spargomw@spargomw12 күн бұрын
KZhead