KWAGWANJI 🇲🇼 BRIAN BANDA NDI MR TCHUNGA 🙌 KWA YAKA MOTO🔥 2025 WAYANDIKILA 🫣

2024 ж. 6 Нау.
54 066 Рет қаралды

Пікірлер
  • Mr chunga is indeed man of God I remember tinagundana pa ku mibawa tikatengana limodzi kupita ku Blantyre police koma atawaona mr chunga a traffic akafuna awakondere koma Mr chunga anakana mpaka analakhula kuti alakwa ndi Iwo anamvomereza kuti ineo sindinalakwe mr chunga is true man of God

    @macantonymilliasi-sb5ev@macantonymilliasi-sb5ev2 ай бұрын
  • Brian you are talented where is my Mr Wonder,umakhwana kukhabakukhaba keep it up,enewo asamakuchedwetseni Man,you are really talented God bless youman. from ndauza village.

    @ConfusedAstronaut-qv6wq@ConfusedAstronaut-qv6wq2 ай бұрын
  • Sinanga alandile ndalama ndichifukwa wakuluwa amanena chilungamo bran Banda ndidolo watu amene amadana ndi mkuluyi ndi fiti

    @user-rh6kp9ts3x@user-rh6kp9ts3x2 ай бұрын
  • Keep up 💯🔥

    @Moses51@Moses512 ай бұрын
  • If there is accident by the road the first person to be questioned is driver , just same as country if leadership is poor it's just because of President Chakwera

    @AusmanBenthu@AusmanBenthu2 ай бұрын
    • There is no poor leadership here in Malawi, but before 2020 we had!

      @user-fi2by2ui9o@user-fi2by2ui9o2 ай бұрын
  • Kwagwanji yakalekaletu iyi

    @martinnyirongo2892@martinnyirongo28922 ай бұрын
  • Brian banda having u its blessings

    @CharlesNangoma-ji5zx@CharlesNangoma-ji5zxАй бұрын
  • Welcome back Brian we missed

    @emmanuelkhosa-ze6fl@emmanuelkhosa-ze6fl2 ай бұрын
  • Welcome back Brian banda ❤❤❤

    @mayesojameskatete@mayesojameskatete2 ай бұрын
    • Yakale kale iyi

      @honourablemcgregorysc97tv@honourablemcgregorysc97tv2 ай бұрын
  • Mwasowa chochitatu mukuponya zinthu zozizila bwanji

    @kagisoorapeleng2640@kagisoorapeleng26402 ай бұрын
  • Chakwela and chilima amavana koma zitsiru zawapanga surround eishhh Agalu, atombolombo, afisi ... Dziwanthu dzadyela

    @user-hm1bf6cw8t@user-hm1bf6cw8t2 ай бұрын
  • Why are you posting programme ya mwezi watha without indicating kuti its old? Titha kupanga unsubscribe muzionera nokhatu

    @tamariahisrael6563@tamariahisrael65632 ай бұрын
    • Ndipo inu eish yakale

      @honourablemcgregorysc97tv@honourablemcgregorysc97tv2 ай бұрын
    • Chimene mmamuchotsera Brian ku program iyi ndi chani??? Nde musamaponye za kale ayi uyu ama bebetsa program iyiii aaaa

      @eliffagondewe8214@eliffagondewe8214Ай бұрын
  • Pagwanji imakoma ndi brian banda ndi achunga ndi abishop tathokoza kuti abanda abwelaso

    @HildatoweraMhango-et4mz@HildatoweraMhango-et4mz2 ай бұрын
  • Kwagwanji wakale uyu

    @user-ln5hw7dn9g@user-ln5hw7dn9g2 ай бұрын
  • Eshi ivi Va ndalevi

    @AkafaaAdin@AkafaaAdin2 ай бұрын
  • Chakwela ndi empty tin mangolongolola zopanda zeru

    @MustafaLikaomba@MustafaLikaomba2 ай бұрын
  • Uyu ndiamene amabebesa times km pano ndie ndimanyaka enini😊

    @MapojubaBanda-ch8pd@MapojubaBanda-ch8pdАй бұрын
  • Zakale kale izi

    @user-wy5od6gz2j@user-wy5od6gz2j2 ай бұрын
  • Mukutumidza zakale bwanji

    @DECENCYMUSSAH@DECENCYMUSSAH2 ай бұрын
  • Aaaaa timadikla kuti tima zina mukutipasila zakale

    @user-qk6if2or2n@user-qk6if2or2n2 ай бұрын
  • Go straight to the point so that we can have Idea for your conversation

    @jamesphiri4204@jamesphiri42042 ай бұрын
  • mumamiya mbali imozi

    @user-vp3ph1ig9f@user-vp3ph1ig9f2 ай бұрын
  • Aseh, mboli yanu mwamvq eeet. Can't u post new thing

    @shupikayintuwaluwa-5899@shupikayintuwaluwa-58992 ай бұрын
  • Tamapangani post zinthu zatsopano not this

    @BlessingsTembenu@BlessingsTembenu2 ай бұрын
  • Momwe umkachitira iwe usanakhale president,momwenso umkachitira iwe Chilima kumusungira kampeni Ku mphasa

    @henryphiri6100@henryphiri61002 ай бұрын
  • Kodi kwagwanji iyi ndi ya liti?

    @Littlefair7@Littlefair72 ай бұрын
    • Yakalekale iyi , Eni channel angofuna ma views, click bait 😢

      @masterkachingwe7448@masterkachingwe74482 ай бұрын
    • @@masterkachingwe7448 Ndiye azinena, otherwise ndi zausilu.

      @Littlefair7@Littlefair72 ай бұрын
  • Mukuponya zinthu zakale

    @alexsumani6823@alexsumani68232 ай бұрын
  • Munasowatu abanda welcome

    @user-ge9xd8mj7g@user-ge9xd8mj7g2 ай бұрын
  • Osamatiyesa please tinaziva kalekale izi

    @DanMhone-iw6xg@DanMhone-iw6xg2 ай бұрын
  • This kwagwanji is not new😮

    @chimwemwechiundira6002@chimwemwechiundira60022 ай бұрын
  • Wasowa chopanga post eti? Nkhani zakalekale ngati izi zaiiii

    @chikagwaharrison389@chikagwaharrison3892 ай бұрын
    • Ndipo wandinyasamo bwanji zakale kale ngat izi

      @lacksonsiyadi943@lacksonsiyadi9432 ай бұрын
    • @@lacksonsiyadi943 Ayamba kujayila ofunika enawa azipangidwa unfollow asiye kulandila

      @chikagwaharrison389@chikagwaharrison3892 ай бұрын
  • But what if the roads that are present are the ones contributing to that accident? He is not the first president remember, so should we really blame the driver even though the car is not in a good condition nor the road? The driver was given the car that was not in a good condition at first, so I don't think it is necessary to point the driver that he is the one that caused the accident, just unfair to say that

    @classicmalipenga8196@classicmalipenga81962 ай бұрын
    • Kulibe driver angayendese galimoto yoti sili good condition

      @user-mq7ou5xp5m@user-mq7ou5xp5m2 ай бұрын
    • Who has the responsibility to fix the car n the road

      @kelvinmphande3754@kelvinmphande37542 ай бұрын
  • Uyu ndiamene amabebesa times km pano ndie ndimanyaka enini😊

    @MapojubaBanda-ch8pd@MapojubaBanda-ch8pdАй бұрын
KZhead