Mbiri ya Dr Bakili Muluzi PART 1

2021 ж. 22 Қаң.
82 958 Рет қаралды

Dr Bakili Muluzi ndi president wakale wa dziko la Malawi🇲🇼

Пікірлер
  • Anyamata apa town❤

    @mosesharoldngolombe@mosesharoldngolombe8 ай бұрын
  • 1981 bakili muluzi anaba ndalama za makad a MCP, mbava yeni yeni.

    @bonjechaula8542@bonjechaula85423 жыл бұрын
  • Wow ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

    @EsnatSayiwala@EsnatSayiwala6 күн бұрын
  • God bless bakili muluzi adathandiza amalawi kuwachotsa muumbuli waukulu

    @fanizoabrahamchimbalanga6529@fanizoabrahamchimbalanga65293 жыл бұрын
    • Kwambiri anatisambisa kumanso

      @amisichiphiri8227@amisichiphiri82272 жыл бұрын
  • We will waiting for part 2

    @lastlevel1999@lastlevel19993 жыл бұрын
  • FDU... NICE

    @ibrahimyusufu3927@ibrahimyusufu39272 жыл бұрын
  • Wonderful di

    @davidbulla9390@davidbulla9390 Жыл бұрын
  • Well done sir

    @fredrickkhebozy6683@fredrickkhebozy66833 жыл бұрын
  • Kodi achair kuba anayambira patali eti? Mpaka kuba £6? Ndi kudzasololanso K1.9bn

    @Littlefair7@Littlefair73 жыл бұрын
    • Komanso kulemera pamaso pa kamuzu zizinali zocheza ayi ameneyu adzafotokoze bwino part 2 akunenayo akhatiuza kuti a Gadama ndi amzawo aja akhati mukutipheranji akuwakhoma ndi hamala iye anali kuti ????????

      @franciskaponda8608@franciskaponda86083 жыл бұрын
  • Thanks for the info. Keep it up

    @charlesmuyaya8839@charlesmuyaya88393 жыл бұрын
  • I like this man chair

    @alexjeremanuel2541@alexjeremanuel2541 Жыл бұрын
  • Please upload it, we are waiting

    @sharifsaidi6706@sharifsaidi67063 жыл бұрын
  • Bakili ndi mbuz imoz ya president mu africa opanda vision aaah tisabise apa

    @chimwemwechimwaza7512@chimwemwechimwaza75123 жыл бұрын
    • zoonadi abraz.

      @m00n_pInK@m00n_pInK3 жыл бұрын
  • Timakunyadilani tiphuzila zambili kuchokela kwainu

    @bashirbanda6519@bashirbanda65193 жыл бұрын
  • Anatiombola ,palibe analimba mtima nthawi imeneija.

    @user-we4ue5dc4e@user-we4ue5dc4e5 күн бұрын
  • Kamuzu inali mbalame

    @maongambonde1004@maongambonde10043 жыл бұрын
  • Fast part 2

    @umaliisah6920@umaliisah69203 жыл бұрын
  • Dr Muluzi /kuchitekete

    @shabbanmatewere439@shabbanmatewere4393 жыл бұрын
  • APA NDe mwakwanilisaatu

    @yamikanimkanthama4354@yamikanimkanthama4354Ай бұрын
  • Anagwetsa dziko la Malawi koposa Mafia wakuba

    @richardnkosi1934@richardnkosi19343 жыл бұрын
    • oky?????? zako zimenezo

      @mouricesaidi5348@mouricesaidi53483 жыл бұрын
    • kuti malawi ilowe pansi ndi bakili akuluwa amakondela zoika apa.

      @m00n_pInK@m00n_pInK3 жыл бұрын
  • Following

    @abdulrafiquekalembo469@abdulrafiquekalembo4693 жыл бұрын
  • ❤❤❤❤

    @KametaMasina@KametaMasina7 ай бұрын
  • Nawoni osawasiya abwele poyela masatanawa

    @humairamalombe295@humairamalombe2956 ай бұрын
  • Bodza tu ili adapita ku Malosa uti???

    @charleskafodya7019@charleskafodya70197 ай бұрын
  • Skype Skills

    @Ibrahimson-su5ks@Ibrahimson-su5ks10 ай бұрын
  • Ali ndi ana angati?

    @allanmakwiti5145@allanmakwiti51453 жыл бұрын
  • I do owe his car from 1998

    @warlubie@warlubie2 жыл бұрын
  • Narrator sangayankhule zonse zoipa za Bakili ndi abwana ake amenewa agwira ntchito ku Bakili muluzi tv

    @olipamaseko2693@olipamaseko2693 Жыл бұрын
  • Bakili anali wamabodza kwambiri ndi amene anapangitsa kuti dzikoli lisauke kwambiri atagulitsa ma company onse a boma ndalama ndi kunyambita

    @olipamaseko2693@olipamaseko2693 Жыл бұрын
  • Kudzindikira kodula dziwalo

    @alexanderkaunda9554@alexanderkaunda95543 жыл бұрын
  • nkhani ya mcp or bakili muluzi? adha inu penapake simumakhala objective with your narration

    @nkhwaziaeros1845@nkhwaziaeros1845 Жыл бұрын
  • Bakili ndi dolo

    @hopesonnsongolo1049@hopesonnsongolo1049 Жыл бұрын
  • Nkhani ili apa nnja Bakili or MCP? Koma akulu awa😂😂😂😂😂😘

    @luciuschigoga2607@luciuschigoga26073 жыл бұрын
    • Monga wekha sukuona kuti zikugwirizana? The narrator akufotokoza zomwe zinachitika kuti Muluzi apange resign.

      @charlesmuyaya8839@charlesmuyaya88393 жыл бұрын
    • Bakili anali nduna ya Kamuzu zonse zoipa amapangira limodzi ndi Bakili sikuti Kamuzu amapha yekha anthuwa ayi

      @olipamaseko2693@olipamaseko2693 Жыл бұрын
    • @@charlesmuyaya8839 chisiyeni amwene ndichitsiru they miss understanding amavera alipanjinga 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣

      @uthmanalex@uthmanalexАй бұрын
  • zokuti anapha matafale simunanenetu amwene anakakhala wa mcp bwezi ndizoipa zomwe mutanena.

    @m00n_pInK@m00n_pInK3 жыл бұрын
    • Nkhani ya Matafale anthu ambiri munayimva mukuthamanga. Amene anakasuma Ku polisi kuti Matafale wamubera katundu wake anali O.G ISSA. Matafale anapita Ku shop kwake ndi marasta anzake nkukaphwanya katundu yense. Sizikugwirizana ndi Bakili Muluzi izi.

      @charlesmuyaya8839@charlesmuyaya88393 жыл бұрын
  • Ati "mfana upange resign"

    @chikondimwale7517@chikondimwale75173 жыл бұрын
    • Hahaha eyetu

      @goldencitytowerent9554@goldencitytowerent95543 жыл бұрын
  • Or pano ma school achisilamu Ali kuti? Awa akungoyankhula za mmutu mwao pano ndi ndani anaphunzirapo sukulu ya chisilamu ndipo zili kuti?

    @olipamaseko2693@olipamaseko2693 Жыл бұрын
    • Masukulu achisilamu kumalawi sukuwaziwa😂😂😂

      @user-cy5ko2qw5d@user-cy5ko2qw5dАй бұрын
  • Mbiri ya Bakili ija mwalowaso za khaza za MCP kkk

    @goldencitytowerent9554@goldencitytowerent95543 жыл бұрын
    • 😂😂😂😂😂😂😂😂koma adha

      @LouisjrSaka@LouisjrSaka3 жыл бұрын
    • @@LouisjrSaka kkk koma kamuzu anamulakwira chachiku mukulu ameneyu, ofcourse a MCP anali akhaza koma kumapolako

      @goldencitytowerent9554@goldencitytowerent95543 жыл бұрын
    • @@goldencitytowerent9554 chomwe adalakwa kamuzu kwa mkulu ameneyo nchachikulu heve 🤣🤣🤣🤣

      @LouisjrSaka@LouisjrSaka3 жыл бұрын
  • Zabodza izi Bakili sanaphuzile ankagulitsa matumbi ku zomba. School anaphuzila atasankhidwa kale u president

    @alankasiya7329@alankasiya73293 жыл бұрын
    • So You mean Bakili Muluzi anapeza scholarship yokaphunzira ma college akunja mzaka za mma 1960 ali osaphunzira? I think mbuli ndi iweyo palibe chomwe ukudziwa chokhudza Bakili Muluzi.

      @charlesmuyaya8839@charlesmuyaya88393 жыл бұрын
    • Bakili muluzi ankagwira ntchito ngati clerk wa Ku court poyambilira penipeni. Ndie ukati anali osaphunzira ukutanthauza chani. Moreover bakili muluzi anali principal wa Nansawa technical college, kamuzu banda anamusankha kukhala MP komanso nduna ya boma pa nthawi yomwe anali mphunzitsi wamkulu wa pa Nansawa technical. Ndie ukati anali mbuli ukutanthauza chani. He was even minister of education mnthawi ya kamuzu. Mwina unangomvera ma propaganda a anthu kuti bakili muluzi anali osaphunzira iwe

      @danielmaluwa7896@danielmaluwa78963 жыл бұрын
    • U have been mis informed Bakili ankamphuzitsidwa school ndi Dr Ken lipenganga Ali kale president. Jce and msce anazipeza Ali kale president.

      @alankasiya7329@alankasiya73293 жыл бұрын
    • @@alankasiya7329 kutanthauza kuti ukutsutsa kuti Bakili Muluzi sanagwire ntchito Ku khothi ngati clerk? Sanagwire ntchito ngati principal pa nansawa college? Sanapite kunja mzaka za mma 1960 kukaphunzira ma college a ku Denmark ndi ku Britain? Sanakhalepo minister of education mnthawi ya Kamuzu? Ukamati we were mis informed what do you mean? Ife tikunena zoona zenizeni zooneka ndi maso pomwe iwe ukunena zongomvera anthu za mabodza. Bakili Muluzi was even minister of portfolio mnthawi ya Kamuzu, and you think munthu angakhale minister of portfolio ali mbuli?

      @charlesmuyaya8839@charlesmuyaya88393 жыл бұрын
    • @@charlesmuyaya8839 maphunzilo amene anenedwa kuti anaphuzilawo that's what I'm against kale anthu ankamphuzila up to STD 5 nkumapeza ntchito ngakhale Aleke Banda anali minister nthawi ya kamuzu koma anali ndi jc . Ngakhale ma minister ambiri muthawi ya amuluzi anali osaphunzira. Kukhala minister sikuphunzira

      @alankasiya7329@alankasiya73293 жыл бұрын
  • He was more worse than useless

    @kool2493@kool24933 жыл бұрын
  • Following

    @lovemapwina6661@lovemapwina66613 жыл бұрын
KZhead