MDYANGU COMEDY SERIES..16/09/23..Flora Suya's👉+265883106798LIKI-LIKI TELEVISION2023 ж. 15 Қыр.34 460 Рет қаралды Share Tweet Жүктеу
Nkhondo y chin'ganin'gani ndi mdyangu tione wowina ndani🎉🎉🎉
Mlelemba ndi more fire!!
Nyimbo zamulelemba zimathera panjira kkkk
Chiphwanya sakusowekera kugula koyendera ka mira wapeza voxy mophweka .mo re fire
Mdyangu tikuyikonda koma muyipange KUT ikhale easy kupanga download plz tiku misar ma episode
Kuno south Africa, Johannesburg
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🥰🥰🤣🤣 km ma gyz mukumvetsa kukoma kuno south Africa mukwana mupitilize luso lanulo ndipondo mulungu kumuyika patsongoro nthawi zonse
Mdyangu n'dala n'dala tuluka apa ine nitulukepo kkkkk
Kodi bwanji pa times sanaonese
A mlelemba akudziwa bwino zoti chemwali awo ndi a chonde 😂😂😂
Shaaaaaa mukubebetsatu
Achiphwanya ndiye mwakwatira
Mumandinvetsa kukoma mulelemba, ndi chiphwanya😅😅
Mulelemba ni 🔥🔥🔥🤣🤣🤣
Achiphwanya kutola khasu ndi mpini omwe
Mwana wa queen zinalake ndi mercy akabadwa
Munyanyiwa ndi mulamwake Mrs sasoka azandipha mkuseka sure,
Yatha ikukoma..can't wait for next episode
😂😂😂 chiphwanya wabelekedwa
I love you all the way from Lusaka I see you my neba
MKAZIE apeza achiphwanya ndi mbola
Koma magaye mwamenya
Kkkkkkkk😂😂😂😂😂😂 mdyangu asanduka sakhuta koma yah ndafa kuno 😂😂😂😂😂
Munyanyiwa akufuna gumbagumba kkkkkkk😂😂😂😂
chamasoni amatha kkkkkkkk brusili 🔊 speaker kkkk
chiphwanya wakwatila sopano a dyangu akufuna kumulanda tiziona😀😀😃
😂😂😂😂😂😂😂😂😂 sasoka mwandikomola kwabasi, blus Lee speaker😂😂😂😂😂
😂😂😂😂chiphwanya uja kuno mpaka kumbuyo komatu next episode kuvuta
Tinaluzatu hope timawona ngati basi kulibe komano apapa mwabwela ❤❤
Zili bwino kwambiri angochepesa ma speechless okhala Ngati onyoza anthu Ali Ku jon musakhale Ngati anthu Andale plz musakhotese zithu
Muli Ku joni
Ya Week ya mawa idzakhala mbambandetu kkkkkk ndimmene ndayionelamuu
Wachonde....ccta wanu a bro bwanji kod kkkkkkkk
Queen ndi mercy mandiwaza😂😂😂
Ati kaya 4 kamoz nd kamoz km mlelemba 😅😅😅
Chimphwanya pakat pa ma Duntu kkkkkk😂😂😂
Koma week yamawa kuli ntchito 😂😂😂😂 chiphwanya wabelekedwa
Mdyangu comedy kunena chilungamo mumativetsa kukom ipatsan moto i love you too much guys good work ❤❤🇲🇼 🇲🇼 🔥🔥🔥
Kkkk pa mdyangu pamvuta nd mabanja
😂😂😂😂pachisime cha yakobo
Sakhuta kkkkkkkkk subuhana watwahala
Ndyangu kkkkkk uzakhala nakazi angati
Koma amdyangu ndi tsakhutadi 😂😂😂
Koma Chiphwana mpaka kumbuyo komayaaaaa
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣mlelemba akuti amene wamuona kuti masanzi ake angatsangalatsidwe nawo ndi iyeyo kkkkkkkkkkkkk komanso akuti chiphwanya ndiolimba mtima kkkkk
Mulelemba haha this guy amathaa😂😂
Mdyangu comedy ili mushe
Komano next chiphwanya mpaka kumbuyo 😅😅😅
😂😂😂😂😂koma chiphwanya omweyo lulululululu🎉🎉🎉🎉
Achiphwana kona Nde mwakwatira ndi kumbuyo komwe😂Sindi mimba abale😂😂😂😂😂😂😂
Mdyangu sadzathekatu kkkkk
Achipwanya more fire 😂❤❤❤
Tifane umatha,,
😂😂😂😂 Koma guy mwayiponyera kwakuya..... Kachepa kayenda akuva kukoma ndichikondi😅😅😅 Mdyangu anatchena magalasi ndi chisoti
Kkkkkkk chiphwanya mpaka yaku mangochi ? Kkkk
😂😂 koma chiphwanya chobelekana ngati chaku mangochi
Excellent 👍 work guys , keep it up 👍👍😂😂😂😂😂😂
Chiphwana mmmmm 😂😂❤❤❤
😅😅😅 chiphwanya zake zikumuendera
😂😂😂😂😂 l love Khwini akakuma ndi Mercy
Prisca gud advance Mai Franco nyumba yapetedwa ya Franco
Next week kuli moto kuti buu!!¡ chiphwwnya kuberekedwa guys
chiphwanya ulemu wanu umakwana
Kamukazi aka ndikahule kagula bwanji mafuta??
Koma Munyanyuwa alibe khalidwe😂🔥🔥♥️
Kkkkkkkkkk cindi mimba kkkk may God be blessed always. Achiphwanya kkk
Kkkkk❤I can't wait next week yooo this pple make my No1 🎉🎉🎉
Akuti mutakhala pheee munawona kuti amene angamusangalatse masanzi ndine?
😂😂😂😂😂😂 koma mulelemba nisala sizamuthela uyu ndithu kkkkk
Tabwerela sakhuta.
Manage material 😂😂😂
Mulelemba waiphula
komah apapa kwachema
Kkkkkkkk lululuuuuuu chiphwanya chiphwanya wayaka kukwatira nkadzi wa 2 simcard proti yonse yemwe wakwatira ndi chiphwanya . Nankha n'dyangu zizamuthera bwanji atamuulula zofunsira nkadzi chiphwanya n'njamoto.❤❤❤❤
waaaa waaaa
😂 koma zikubhebha
😂😂😂😂😂😂koma agogo chonde kulani😅😅😅😅. Mdyangu aaashi.
Mumatha
AMarcy mimba ikukukhalan
Kkkkk kma munyanyiwa kulidzithu
Koma mdyangu sazatheka
😂😂😂😂😂 ndalama adyaaa
I can't wait kkkkkkkk achiphwanya zafika pamenepo eti hahaha
😂😂😂 Koma chiphwanya 😂😂 Mpaka kubelekedwa 😂😂 AMULELEMBA pena mudziona malo okhala, Zimanyumba izi Zidzakugwerani pamutu Tsiku Lina. Kkkk
Bola inu mumapanga vibration 😂😂😂😂😂
Chiphwanya wakwatiladi
Kkkkk chipwaya ndiwe one
Koma mdyanguu magalasiwoo ngt gompha nthikooo kkkkkkk lv u gyz
Koma gyz episode Yi mwaizukuta ma connections ake -flow yake ili boh
Wawina
Chiphwanya umatha
Mochedwa momwemo we r still together
❤
Mr sasoka with your beloved wife,
😂😂😂 Koma musayambise zojamisa jamisa ngati zili ndi masikirasha chimphwanya yemweyo😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂❤❤❤❤❤
Ndazikonda izii❤
Chiphwanya ndi Kha kha kha 😂😂😂😂😂😂 🎉🎉🎉🎉
Mulelemba
🤣🤣🤣🤣🤣 nice koma Saskia
Koma next week iliko kkkkkkk chiphwanya number 1
Munthu wankulu mulelemba umandiwazw
kkkkkkk mukadalipandakonso khulukulo 😂😂😂😂😂❤❤❤