Ойын-сауықTONDE WADULA DRAMA SERIES EPISODE 92Nkhalango Multimedia2024 ж. 14 Нау.16 653 Рет қаралды Share Tweet ЖүктеуTONDE WADULA DRAMA SERIES EPISODE 92
A Zimveka self confident man
Koma chibilit kkkk ngopepera
Asiyatu Wayamba zozembela chinyaxx
mrs chiphwanya ndakhumudwa nanu mkumuyenda pansi mubale wanga ching'ani ng'ani 😅🤣🤣🤣🤣🤣
Ka covid nso pakhosi
Poyamba achibiliti ndi mawavera chisoni kma pano 😂😂😂😂😂😂
Asiyatu wagundika tu 😅🤣 Amfumu kutchena ... Gaga is troublesome
Kkkkkkk Mrs chiphwanya
Nazombe sangapereke nkhuku pachabe😂😂
Dola ndiwe number one kukana a azinveka kwantima biiiiii 😂😂
Zimveka nditabwali kkk umakwana .
Chibiliti kuiwala mwansanga. A Nambewe muphunzitseni Chibiliti wachibwana kwambiri
Kkkkkk koma guys muli bho
Koma Gaga ndi 1 kkkkk😂😂
Mai wa ndi ahule. Akufuna cholinga azizemberana ndi tonde
Amfumu a William akut ndimupha
Chibiliti nagumbo mtaye amabwelesa mimba munyumba
Mai ake azankhwima abwera motoo
Zikomo kwambiri koma tikufuna mwini wa mimba ya chisomo ndindani
Asiyatu la 40 likwanatu muyaluka mai Chiphwanya😂
He's dora uriboe bambo ako tonde
Anambewe ayakatu😂😂😂
nice
Bwiyake Che Gaga ulesi bwanji? Kkkkkkk ndima kunyandirani nose athuanga ine BM1 kapena kuti 100% Baby Rasta BT Malawi Bangwe Modiwa Namiyango
anabwewe sopano mwachita bwino kuwathila mphepo anagumbo,gaga ndimwana woipa,ili bwino koma mwayamba kuchedwesa ka
Zimveka ukadakhala mwamuna Muna bwezi utasiya Mumbai zambir
Mumatimvesa kukoma i lv Nchemwali wa chibiliti ali ngat agogo anga sabisila
Mrs chikwanya
Vuto ndichani sikutifika mokwanila film yathuyi atonde ndi anzanu
Anambewe mumakwana ndipo mumve kumene muliko ulemu wanu
Zimveka man of the moment
Mwayamba kuchedwesa pano tisiya kukusapotanitu
Anambewe kwa anagumbo
Koma afumu mwavala bwino 😂😂😂😂😂
❤❤❤❤
Zakhwima wang"ambika ndi ndalama za Chiso😂
masiku anowa mukumachedwetsa kuponya
Komandiye kuvala mwa ufumu eee
Nice guys keep pushing 🎉🎉
Koma muzamachedwe guys tikutulukanitu😂😂😂
Ndipo inu aaaa tinazilowela
Ndawonanso a chief William mfumu yofwatsa komanso yanzeru
Zimveka aa iwenso ndikatundu
Anfumu mwatchena m'manja mwanu 👏👏
😂😂😂 koma Ziveka aass
Mukuchedwa koma maguy iii
Ndipo Ife timadikili lachitatu
Ayamba zawozawo aaa
Anambewe aikungamo wamuchinyira mitengo😂😂😂
Gaga koma anakonza
Big up zimveka😂😂
Munasowatu guys
A gaga ules
Anagumbo musakane mwamdyesa mankhwara mwamuna 😂😂😂
Zimveka tambwali ndipo dzinali lidamukhala 😅
Anambewe kwa Anagumbo 🔥🔥🔥
Aaaaa ma ndola amasuleni aziveka asiye kupanga zamwanayo simwamuna wabwino ameneyo anakupangani khaza kukupangitsani kungona ndimuthu mpaka mwana koma osamudziwa fungo lake ayiayiayi osamuyandikila ameneyo ndi njoka
Gaga sadzatheka
🎉🎉🎉🎉🎉
mbili wapeza mamuna 😂😂😂😂😂
Eeee zinveka ndi nyengatoni paliso
mukuchedwa kwambiri , sibho ma guys.mufuna tikutulukine
Wow welcome gusy we miss u 😘 0:39
Kkkkkkk chiphwanya apha munthu
Kkkkk wasochera nayo nkhani kkkkkk
First comment iz mine
Kkkkkk agaga mwasowa ntendele
kazi wa chiphwanya koma 😂😂😂😂😂😂
Mwayamba zotani pano abale iiiiii mwayamba kupwekesatu now
Kodi NYUMBA yagagayi pa chitseko NDI katani KAPENA G string😅😅😅😅😅
Kkkk
Kkkkk koma anthu mmayang'anisisa kkk
I love u chisomo
Gaga zavuta basi 😂😂😂😂
Komatu zinveka😂
Guys dzilibwino kwambili kom kuchedwa eee❤❤
Zinveka sazatheka
Kkkkk koma anthu inu
Very nice
Nice movie
Asiyatu 😂
Good good
Ndipo ma gyz amenewa amathat😂😂😂😂
Nagubo wayichocha😂😂
Fire burning
Achibiliti mzavutikaso tu koma sayiwale kut anakuthamangidani anagumbo
gaga koma 😂😂😂😂😂
Pano chimanga chikukhwima nde uku bwanji
Nagumbo wakumana ndi nambewe
Guys mwayamba kusowa kod muzitipatsa episode imodzi pa week ngat zinaz? Tinazolowera angapo pa week
❤️❤️❤️🤣🤣🤣🤣🔥🔥🔥🔥🔥
Achibiliti tsopano
😂❤❤
Pano munanyamba kuchedwetsa ma video why paka too week
Nagumbo usasokoneze banja
Zakhwima akaloweso basi
Kom kakumachedwaano
Zilibwino
Ya
KOMA ZIMVEKA 😂🎉🎉😂
Where is falawo wasowat
Who is you? or who are you?😅😅😅😅😅😅
❤❤❤❤❤😂😂😂😂😂😂
Koma apa pa Dola pakufunika DNA chonde
❤❤ Nagumbo wamtani chibiliti
❤❤❤❤