КомедияUSAUVERS09E01 BOXERPiksy TV2024 ж. 25 Сәу.63 449 Рет қаралды Share Tweet ЖүктеуENJOY & SHARE ;)
Guys sign a deal with one of the media companies u deserve to b on the screens of many malawi homes
I second🤛🤜
The fun has resumed😂😂😂😂😂...timve nkhani tisekenso lol waiting patiently
😂😂😂😂 koma Ngozo at ukachita mwano tizingot nd mutu 😂😂😂 Ganizani, Mtebe, Edo,mnyamata wamutu nde kulinso wina wa dzuwa lindiwalire iwenso undiwalire welcome back in action guys mix chithunzi mbambande 🔥🔥🔥🔥
Kmatu Edo kkk unaonako kuti kkkk cholinga anzanu akwere dpp kkkk.. mwabwera ngati coming 🔥🔥
Madala Gani..tsopan Mzika Mzika! 😂😂😂 hahaha My favorite!!!
Usovaaaa... mwabwela ngati coming magayeeeee🔥🔥🔥🔥🔥
Welcome back ma guy ndipo mwafika ndi 🔥🔥🔥🔥
Kkkk mwakoma nonse.. welcome back guys
yandiwaza ndiyachikabudula eti mwina waona ujenitu hhahahaha respect
Dzuwa lindiwalire, iwenso undiwalire aaah uyiwalire zimenezo 😂😂😂
clear and quality pictures! kuchita kuposa TV station inayake yozipopa kwambiri
Zodiak 😂😂
Kk koma aise in'galule basil
Kk koma aise in'galule basi
Kk koma aise in'galule basil
Mwaiziwa nyimbo ija amati,,, pang'ono ndpang'ono eyatiyendeeee
Improved Cameras and everything, so lit🔥
kkkkkk sitinakomebe tose welcome back gyz
agani ndikatundu sewelo lonseli😂😂😂😂
Welcome back guys ...... Ganizani my guy
Mwadza ngati coming😊😊, Ngauzo wadzaaaaa🎉🎉
Watsala Belita ndi mzake Mtebede ali kwani koma big up you are starting nice
Ndekuti munthu akapanga mwano tizingoti ndiwe wa mutu😂
Etini🤣
The closing song I love it🔥
Ngozo is responsible now... Zandiwaza 🔥
Usauver on point,,
Welcome Back guys........Ganizani kuzangobwela ndi ya unzika🤣🤣🤣🤣🤣 akuti iye si Tour
I saw it coming that u guys u wl going to make it✊✊keep up the good work
Mwabwera Moto guys zilibwino Kkkkkkkkk Koma ngozo nde mwati mmutu Ngati gwape
Ati mmmmh mmmmhh mpaka kufuna kulavula wine. 😄😁😆😅
🎉😂😂😂😂 ati nyimbo chopusa sichimwa mowa😂😂😂😂😂
Ma guy munasowa ,, welcome back❤
Agani akut "ine ndinzikatu ase" 😂😂😂😂😂😂
😂😂😂😂these guys make us happy😂😂😂
Mamuna ngati Albert ndingamupeze kuti
Ine ndili kuno koma nzisakumwetsa Gin not wine 😂
Hahahaha ati makoma nonseeeee aaah iwe Pikiseeeee
Mwaxa ngati coming tu ma guy 🔥🔥🔥🔥
Zuwa☀️ lindiwalire inunso mundiwalire aah muiwalire zimenezo
Mwabwera ngati coming 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Aaag koma Piksy🤣🤣🤣... Ati sitinakomebe tonse? Whaaaat!!! 😂😂
Fire 🔥 we missed you guys
HAHAA sitimalavula mowa, akanakhala Fanta tinakakulora kulavula. 🤣🤣🤣 koma HYPHEN
Ati , 'of course ndimwa poti mwati ndiyetse'. Glass yonse out 😂😂😂
😂😂😂😂😂Piksy ndiwe galu kwabasi😅😅😅😅. Sitinakobe tonse, akaka kabaya.
Nice quality videos👌
"sitinakomebe" that hit hard 🤣🤣🤣🤣🤣
😅😂😂😂
I know right! I laughed so hard-that was too crazy to be honest! Who thinks like that 😂😂😂😂
😂😂😂 aaaa
welcome back, camera ili mwala🔥🔥🔥🔥 Ngozo standing up for Patricia😅😅😅😅😅😅
For the 1st time🤣🤣
For the first time kkkkkkkkkk
Eee umunde mulikuyankhana kwa nyoo kwa nyooo 🤣🤣
Sangie alikuti queen of reggae
Kabudula obwereka savala opanda boxer.. mwambi wa lero kkkkkkk
Gani ndinzika ati
mwabwera ngati coming 🔥🔥
Tivale boxer ngt tourist ndi nzikatu 😎😎 tikoma lit
My favorites 🎉❤😊
Albert umusokoneza nkazi ndimabodza 🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Finally Usauver is here 🥳🥳🥳 time to watch Mtebe again 😂
The song at the end 🔥
Ati akwatire ngat akufuna aziwakonzera pakhomo wabwera iweyo😂😂😂
It's nyce to see you back
Nyimbo mwaika kumapetoyo eeh🔥
I just like malangizowo, I think titengelepo phunziro anthu omwe timakhala pakhopo pozibere athu
Akakuphunzitsani mowa choncho kenako akusiyeni akakwatile osamwa mowa chifukwa inuyo siinu wabanja saamwa mowa lol
Nice one big up ❤ Ti joiniseni nafenso tikhale mmodzi mwainu chonde...nafenso timatha
Ndie aganizan mwati ndinu zika simungavale boxer ngat tourist😂😂😂😂😂
U never disappoint guys
Welcome back guyz. Ganizan kabudula wanzako osamvala boxer koma iwe...
Hahahahaha osavalanso booxer
Kkkkkkk km guys chopusa sichimwa mowa kkkkkk
The episode is always short🤣😆😆 a bang on friday is back💪😆 iwe ife ndimzika💀💀
😂😂😂😂koma guys inuyo mumatha eeeh big up🔥🔥🔥
Ashado mwana mpaseni mpata akuoneka kuti ndi campaign director wabwino 😆😆😆🔥
We missed it , nice one 🎉
Sitinakomebe tonse😅😅😅😅mwano waukulu
Ati sitimalAvuka zimenezo, akanakhala Fanta ukanalavura😂
Mmnutu ngati Gwape choncho
We waited for so long nice to see you back guys ❤❤
Kkkkkk akuti sitinakome tonse kkkkkk anthu mumaganiza bwanji 😂😂😂
Kwabwera fire
Welcome back 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Albert akufuna kubesa mkazi uja ndamuona, nde mkazi wagodoka kale nd Edo 😂😂😂
And I quote "ndinatenga zinthu zanga Zonse kuti ndizikhala kuno"😂😂😂 Forced leave gone wrong😂😂😂
Ati kd sitinakomebe in ngauzo's voice
Kkkkkkkkkk ...kabudula wobweleka savala opanda boxer🔥🔥🔥
Welcome back Mr your the best
Chowawa pa dziko lonse ndi aluvera🤣🤣
My favourite drama indeed💥💥
Welcome Back we missed you!!!
This is lit 🔥
Ngauzo ndiwe galu 🤣🤣🤣 sitimayanambebe kukoma tonse
😂😂😂😂😂😂😂ati ine nzivala boxer ndine tourist chani😂😂😅😆😆aaaah😆😂🙌
Welcome back kkkkkkkkkk Eldo kusokoneza zithu
Welcome back ❤🎉
Welcome back 🎉❤❤
Mutu umene uja nauona ndekha😅😅😅😅😅😅
Apa ndie mwadza❤
Season 9 imeijao! Yayamba nd motso , angauzo
🤣🤣🤣🤣🤣 koma Gani, ati ukusunzumira zoona aise😅😅😅😅
Long time on the screen you guys.....mwadza🔥🔥🔥🔥🔥
Kabudula obwereka kuvala opanda boxer😂
🤣🤣🤣🤣🤣 ndipo
After long time mwabweraso❤😂
Sitinayambe kukoma 🔥🔥🔥🔥🤣🤣🤣🤣🙏
Ndinakusowani ma guy❤❤
A Ganizani kkkkk kungoyenda belu belu 😂😂😂😂
hahahahaha nzika siyivala panti hahahahah
Eish akuti sitinakomebe tonse😂😂😂😂😂
Wow, 😅 welcome back!!! 💃💃
Mmakwana guys fire🎉
Nde mwati mutu kkk waching'ala ng'ala
Mwakoma nonse😂😂 ayi zikomo😅
Onyamula khope yanuyo nkumaenda nacho 😂😂😂
Shado wozindikira. Samafuna ntchito uyu😂