BON KALINDO LERO WACHISAMBWADZA CHIPANI CHOMWE CHABADWA DZULO |

2024 ж. 26 Сәу.
21 092 Рет қаралды

Пікірлер
  • Akunena zoona kalindo

    @PempheroMoleni@PempheroMoleniКүн бұрын
  • Alibeso ndalama anaba xochepa bolatu ma guys a sattal Ali ndi kanthu

    @CharlesMulikhiwa@CharlesMulikhiwa7 сағат бұрын
  • Msiyeni kalindo ayankhule nanunso ngati pali zoyankhula yankhulani ife tilipano kumva zoyankhulidwa zina zilizonse palibe apye mtima ndi kuyankhula basi ife tisitsunga mawuwo

    @JimukarimuAdini@JimukarimuAdini5 күн бұрын
  • Timakunyadira Bon the Dc ndiwe diso la dziko la malawi ndiwe chiwomba nkhanga usazafe kalindooooooo! The Dc

    @user-oe1lg4xo7w@user-oe1lg4xo7w11 күн бұрын
  • Nankhumwa ndi mwana.akulephela kupeza dzina la chipani chawo😂😂😂😂😂😂😂😂

    @user-vl8uw8mc3u@user-vl8uw8mc3u12 күн бұрын
  • Aise akumsngatu ndi ma dictator akupha uona

    @CharlesMulikhiwa@CharlesMulikhiwa7 сағат бұрын
  • Good message Mr bon Kalindo

    @user-nf3ik3ff6y@user-nf3ik3ff6y11 күн бұрын
  • Amalawi zonse tikuona zipani zoyambika CHIFUKWA CHA nkwiyo tikuziziwa osadandaula ayi ife tikavotera dpp basi komaso chakwera asaiwale mau amene ananena oti azakhesa mwazi chakwera akazangowina 2025 anthu sitizalola ai chakwera wazunza Amalawi kwambiri 🎉🎉🎉🎉🎉🎉Amalawi tisagone ai tipemphere zolimba kwambiri kuti Satan ameneyi achoke basi 🎉🎉🎉

    @user-rc3ze2oi7u@user-rc3ze2oi7u12 күн бұрын
    • 😊kupemphera ndekusakhale kolekeza cos mwazi nde uzakhesedwa ,mulungu atipqngire chifundo koma😭

      @blessingsmimu5236@blessingsmimu523611 күн бұрын
    • Mukunama DPP siyingawine anthu adatopanayo misewu yozila Chaka chimozi watha ndizimene mukufuna yiwalani take mau anga chipani chikufunika abweze Kwa bakili mwini wake ndiye bakili ananena kale kuti mcp yikalowa mu Boma basi Palibe chipani chingachose mcp

      @user-vu9es6nz3k@user-vu9es6nz3k9 күн бұрын
  • Ngat nankhumwa akulephera kupeka dzina la chipan chake nde angayendetse bwanj dziko 😂😂😂

    @user-lw9su5om5z@user-lw9su5om5z12 күн бұрын
  • Vuto ndiogulidwayo

    @user-yk9lx7xd1i@user-yk9lx7xd1i22 сағат бұрын
  • Akukambatu ngamoo. MCP ndi akamberembere basi. Akufuna aphe democracy 😢😢

    @TressLuka@TressLuka7 күн бұрын
  • Chipani cha Mtundu wanji chopanda intelligence????

    @chesterphiri7523@chesterphiri75238 күн бұрын
  • Chipani munthu sapanga form yekha ayi.this party is well organized ,

    @JustinPhiri-kq2bb@JustinPhiri-kq2bb12 күн бұрын
  • Kuwina ndi kuwina basi

    @sandramkaligida1163@sandramkaligida11634 күн бұрын
  • Ndi mwana uyu ndipo ndi kape

    @andrewBwanaisa@andrewBwanaisa9 күн бұрын
  • Kape uyu

    @macleanmachamo@macleanmachamo4 күн бұрын
  • Bwana DC mumatiimilila

    @MussaManyero@MussaManyero11 күн бұрын
  • Koma kalindo ndiwandare ine amandinyasa kwambili bora masewero omwe aja

    @user-pj3rf4rn9w@user-pj3rf4rn9w8 күн бұрын
  • Nankhumwa munthu osokoneza,Sudzakhala nsugoleli ku malawi. A mcp adzingokugwilisa ntchito basi.

    @user-dd1qq5xq1k@user-dd1qq5xq1k11 күн бұрын
  • 😅😅😅😂😂😂Ati malawi isazathe kwachuluka ma drama

    @JamesSpondo@JamesSpondo10 күн бұрын
  • Penapake kalindo nakhala ngati wakhuta mbwanda, kanundu mukati.

    @clivemhango6183@clivemhango61839 күн бұрын
  • Akulu boma silingatekeseke ndi inu. Sukugona tulo ndiwe

    @robertkalima874@robertkalima8747 күн бұрын
  • Akalindo aliyense ali ndimaganizo ake ake sionse ali aDPP ulindi manta tipitiliza mpaka 2030

    @atusayeMtalama@atusayeMtalama12 күн бұрын
  • No chance for Mcp again

    @DONNEXKhama-bk1gy@DONNEXKhama-bk1gy12 күн бұрын
  • umakwana DC

    @user-kr1kg5hy9l@user-kr1kg5hy9l8 күн бұрын
  • Ife kupoto Munthali ndiye ayi anatinamiza mbombora

    @user-gh6qm5ze3b@user-gh6qm5ze3b12 күн бұрын
  • Akunenadi zowona zipani zichenjele ndithu

    @InnocentDaveson@InnocentDaveson10 күн бұрын
  • Chakwela ndioipa ntima ngat kambuku akufuna kupitiriza kusokoneza malawi bas

    @user-ot6lt8iy8f@user-ot6lt8iy8f11 күн бұрын
  • Kalindo lengeza kuti walowa dpp osatinamiza. Umati atani atawathamangitsa ku dpp. Dpp yatha basi mwathetsa nokha zitsiru inu. Mulila 2025 simunati. Kalindo watch out.

    @ChisomoChikafa-dd3sj@ChisomoChikafa-dd3sj9 күн бұрын
  • Ndizoona mcp si kugona tiro ndi dpp

    @FabianoNgozo@FabianoNgozo11 күн бұрын
  • Bon mukasowa zolankhula muzikhala phee...how can u say there is plan yothetsa dzina la dpp?

    @user-rm8jd9mu8r@user-rm8jd9mu8r12 күн бұрын
  • Kodi akalindo mwalowa bpp

    @user-nc4vi1jt5g@user-nc4vi1jt5g12 күн бұрын
  • Awa ndi amisala p d p zanzawo izi akutani zawavuta

    @jonathanmunthali8500@jonathanmunthali850011 күн бұрын
  • Mulungu sinsuwani wake wa munthu dzanja likalemba lalemba Babylon is falling apart

    @FosterChilumba@FosterChilumba12 күн бұрын
  • Odana ndi bon ndi nsawi

    @AleksaWilliams-qc6cn@AleksaWilliams-qc6cn11 күн бұрын
  • Nankhumwa walakwaso chiyani achisilu akalindo pangani zanu gwape uyu

    @user-pt8wb4vw6r@user-pt8wb4vw6r12 күн бұрын
  • Kalindo ndiopenga. Mwawathamangitsa apa ayambitsa chipani chawo alakwitsaso. Pompano mumati angoyambitsa chipani chawo

    @user-lp2sd7lt8b@user-lp2sd7lt8b12 күн бұрын
    • Iweso mesa unali modz mwaiwo😂😂😂

      @blessingsmimu5236@blessingsmimu523611 күн бұрын
  • Amatha kalindo palibenso

    @blesstonphiri@blesstonphiri11 күн бұрын
  • Inutso opanda zelu ndithu peter mukumulankhulilayo,yemwe uja,anakumangani,mutaulula,kuti amapha ma alubino,ndipo mutoziwako,komwe amakagulitsa,mafupa uja?sitimaiwalatu,uyu, nankhumwa ali ndi ufulu,ndi joker yemwe amadikila Anthu,uja ndiyetu,ameneyi.a kalindo zelu mudzikhala nazo.dpp, kuwina sidzalamulila malawi.iweyo,usalodzedwe kubwela ku phalombe kumazalankhula,zonunkha.

    @HarrisonMwanga-xy4sc@HarrisonMwanga-xy4sc11 күн бұрын
  • The headless chicken

    @OwenKachipapa@OwenKachipapa8 күн бұрын
  • PDP woyee

    @macleanmachamo@macleanmachamo4 күн бұрын
  • We need DPP back

    @ValueSibande@ValueSibande12 күн бұрын
  • Whether you want or not Dpp 2025 boma

    @user-lw4hw9ce4w@user-lw4hw9ce4w11 күн бұрын
  • Akalindo ndinu chitsilu mulinditsanje mumagwlitsa ntchito anthuosauka mulindinsanje

    @user-nc4vi1jt5g@user-nc4vi1jt5g12 күн бұрын
  • Bon kalindo ndiwe chitsiru kwambiri ndiposo iwe sungamenyane nane ndiwe mwana

    @user-gj4li2gc8o@user-gj4li2gc8o12 күн бұрын
  • Bon tapangani zanu zoti zikuthandizeni

    @MmikeeMateyo-kj2pn@MmikeeMateyo-kj2pn12 күн бұрын
  • Kalindo watha supu. Walowa DPP mwachisisi. Dairy kulalata ukutisokoneza mmalo moti tizigwila ntchito uxitha mwezi osayankhula

    @user-ml2vw1dc9c@user-ml2vw1dc9c12 күн бұрын
    • 😅😅

      @user-mg9ie2pi3d@user-mg9ie2pi3d11 күн бұрын
    • @@user-mg9ie2pi3d Wamisala satopa. Mulekeni. Ngati chili chi ban chomwe wadya adzimbidwa nacho

      @robertkalima874@robertkalima8747 күн бұрын
  • Akalindo bodza inuu AAA osamakula ayi

    @blessingsgeoffrey9414@blessingsgeoffrey941412 күн бұрын
  • Alowa yadpp kuti aziwapasa banzi

    @user-pt8wb4vw6r@user-pt8wb4vw6r12 күн бұрын
    • 😂😂😂😂😂😂

      @HarrisonMwanga-xy4sc@HarrisonMwanga-xy4sc11 күн бұрын
  • Za adress usasochelese anthu bon address ndichitnthu chofunika kwambiri

    @macleanmachamo@macleanmachamo4 күн бұрын
  • Nsanje boni kalindo

    @macleanmachamo@macleanmachamo4 күн бұрын
  • Awa akupengatu

    @kalimawandale7161@kalimawandale71615 күн бұрын
  • Akulu awa ndi akhunyu che kalindo

    @user-kr1tf2tu7s@user-kr1tf2tu7s12 күн бұрын
    • Uzadwala wekha khunyulo,back to sender

      @AleksaWilliams-qc6cn@AleksaWilliams-qc6cn11 күн бұрын
KZhead