KWAGWANJI? LERO KWACHEMASO🔥🔥🔥🤔🤔🤔 MALAWI SAZATHEKADI. 22 April 2024

2024 ж. 21 Сәу.
14 109 Рет қаралды

Пікірлер
  • Kumangoti ma court, ma court ake ati??? America sinalakwise coz too much delays ma court anthu especially milandu yeni yeni osati za born kalindo anthuwa onse ngakuba chakweraso ndiye mbudzi yeni yeni.

    @chitanibenito1109@chitanibenito110926 күн бұрын
  • America ayenela kulankhula chifukwa ndi ayini ake a ndalama ,it's painful kumaona kuti akutumiza Thandie wina mkumaika mthumba make Malo mothandizila anthu Osauka

    @user-te3ps3kf2t@user-te3ps3kf2t26 күн бұрын
  • Mbuzi ya president chakwela moyenda chinyau watikwana

    @ChangeChambo@ChangeChambo26 күн бұрын
  • Kodi olo inuyo a kunkuyu mungalole kuti munthu amene ali ndi mbili yakuba adzibwela kunyumba kwanu kumadzacheza ndizachidziwikile kuti munthu wakuba sitimulola kubwela kunyumba kwathu

    @patassonelucaszovuta3431@patassonelucaszovuta343126 күн бұрын
  • Chakwela the fool of the foolest

    @JIMMYWATHONJE@JIMMYWATHONJE26 күн бұрын
  • Nkhaniyo kukhotiko mpaka 4years akudikira chiyani sadalakwitse boma la America

    @samsonmtumbati4855@samsonmtumbati485527 күн бұрын
    • Makhothi kulibe, Acb kulibe asamaname apapa ma Judge nda Mcp aweruza bwanji milandu🙌🙌

      @eliffagondewe8214@eliffagondewe821426 күн бұрын
  • MALAWl has destroyed because of Chakwela and his cabinet and his family , I will Happy to see this Crue are arrested , big criminals in MALAWl , We don't have court of justice here in MALAWl because all of them are under corruption of this particular government of MCP

    @rashidadan2533@rashidadan253327 күн бұрын
  • Chakwela kunkuyu chimwendo mkaka mukuzitenga ngat Madolo muli agalu enene fwesek

    @DylesMtenje@DylesMtenje26 күн бұрын
  • President wopanda manyazi ndipo mwayaluka Kuba mupaka ku dziko la eni ake mwalengeska Malawi

    @marryphili5419@marryphili541926 күн бұрын
  • Pulezidenti omvetsa chisoni ndipo alibe manyazi

    @sweeneykamwendo6251@sweeneykamwendo625127 күн бұрын
  • Chilungamo chili poyela apa abale palibe zozungulila zungulila apa ,milandu paka ifike 2025 kuma vote 🗳 chigamulo chizakhala liri?

    @WisikiBlack-gj4gu@WisikiBlack-gj4gu26 күн бұрын
  • Çhakwela ATI tiyipasemoto yakuba 😂 okalozedwa suununkha chithandizo muchipeza Kuti. AAAAAA chimozesi kukuyu 😂😂😂 mbuziyi yatisausa

    @user-ul5hh3cz8z@user-ul5hh3cz8z27 күн бұрын
  • Ma jaji athu palibe ilipo alimumbuyo ma boma lachakwela akupanga business ndichakwela ,,mukhani zakatangale

    @WisikiBlack-gj4gu@WisikiBlack-gj4gu26 күн бұрын
  • Yes zoona zikanateladi kumbali,,koma chakwela inamukhudza khani ija, chifukwa mu athu akatangalewo chakwela alimo,chifukwa walupha malile kuesa kuzibisa koma ziululika zayamba kale man chakwela

    @WisikiBlack-gj4gu@WisikiBlack-gj4gu26 күн бұрын
  • Zoti a Malawi adziwe nzoti milandu ku Malawi kuno ndi a ife osauka chifukwa siyimatenga nthawi kutha Ku ma court koma zandare pa nkhaniyi ayi. President wanthu afulumira ovutika tinkhara ifeyo common people. Chonde iwo a pepese

    @masoyaonamunkhondya9074@masoyaonamunkhondya907425 күн бұрын
  • Pamafunika kt milandu yonse imene ili mmakhoti izengedwe chaka chino chisanathe coz kuzengereza kuzenga milandu ndichifukwa chake maiko ataya chikhulupirilo ndimmene tukuchitira

    @happymumba2261@happymumba226127 күн бұрын
  • America sinarakwuse coz america ikutivera chison ife amarawi coz khani ikakhara ku court imachedw kt aweruze mpaka zaka zambili

    @esthermalixani2244@esthermalixani224426 күн бұрын
  • chakwera ndi chitsiru zamukwana ban imeneyi chifukwa iye ndimbavanso yayikulunso

    @JafaliAkimu-ll1bf@JafaliAkimu-ll1bf26 күн бұрын
  • Mbava chakwela

    @DylesMtenje@DylesMtenje26 күн бұрын
  • Plezident waunsilu ameneyu

    @user-mp5sd7yb7l@user-mp5sd7yb7l26 күн бұрын
  • Milandu ili mokoti ,, tsono mosemuja mukoti igemulidwa liti kodi kufufuza kwake kotani

    @WisikiBlack-gj4gu@WisikiBlack-gj4gu26 күн бұрын
  • Chakwera kodi wadziwa liti kuti America ndiyokuba ndiwe galu kwambiri usazapitenso kumeneko

    @ChikumbutsoJohn-rs4tt@ChikumbutsoJohn-rs4tt26 күн бұрын
  • President chakwera sadaganize polankhula kunyoza America, akukhala ngati akugwirizana ndi kuba.

    @user-pv9uk6sc3w@user-pv9uk6sc3w27 күн бұрын
  • President akuziwapo kanthu, ndithu. And kufufuza mpaka ati 4 years akufufuzabe , aaaaaah koma amene anatilozayo ndi emweyo tili ndi vuto la muwubongo makamaka akuluakulu ku ntundaku zosaenda . Ma mericans-wa ndie kuti anafufuza kale pa okha why inu mukuchedwa pa zifukwa zoti nonse ndi akuba ndie ndi zovuta kuti akuba okhaokha sangayalusane. Ndie angoona kuti anthuwa ndi amozi asatipusise tingowauza zochita bsi eyetu.

    @user-jk8sh7fh2d@user-jk8sh7fh2d27 күн бұрын
  • Maloya ake mbavazo mese amachedwesa mulandu daladala kumaonangat amalawi ndiopusa

    @MustafaLikaomba@MustafaLikaomba26 күн бұрын
  • Mbava zokha zokha mwaonjeza kwambiri bomalimeneli ndi LA anthu okuba kwambiri zikubisana chifukwa onse ndi ambava kulibwino achoke anthu amenewa sakuthandiza mzika za amalawi

    @user-ee6be5kl5o@user-ee6be5kl5o27 күн бұрын
  • Musadabwe nazo akudziwa zochita America kalipo kalipo

    @PiliraniDenesi@PiliraniDenesi26 күн бұрын
  • Achakwera akuopa awa kuti kwatsala tchire ndikomwe kupita moto. Akudziwa kuti nayenso akachoka pampando milandu yake ikazayamba iyeyu ndi ana ake adzaletsedwanso kulowa ku America poti ndikumene amakabitsa ndalama akuwabela amalawi.

    @mcsellahntv6896@mcsellahntv689626 күн бұрын
  • Mvuto a chakwela iwonso ndi mbava ndi chifukwa achita zimenezi

    @user-ev4or2kg4z@user-ev4or2kg4z27 күн бұрын
  • Aba zambiri ayamba kukula mtama a Malawi kkkkkkkk tiziona.

    @chipilirokalison1334@chipilirokalison133426 күн бұрын
  • Umphawii sizinthu ayi antthu amakutukwana chifukwa chaumphawi apule ali ngati kholo tele amalawi akutukwana apule chifukwa chowayimila

    @user-pt8wb4vw6r@user-pt8wb4vw6r27 күн бұрын
  • Chakwela ndiwolakwa

    @user-nf3ik3ff6y@user-nf3ik3ff6y26 күн бұрын
  • Iiii kunkuyu ngati sudziwatu iweyo mkaka , zikhale , Richard ndiamene mukuononga dziko lathu dziwa lero

    @user-un6qv6sj3h@user-un6qv6sj3h26 күн бұрын
  • Akulu process in low yake itiyo ? Ma count athu amachedwese milandu dala ?

    @robertchitsulo8006@robertchitsulo800627 күн бұрын
  • God job America 😂😂😂

    @Dorah-zl9uf@Dorah-zl9uf26 күн бұрын
  • In malawi we need a crismatic leader not a trained leader

    @GiftMshani@GiftMshani26 күн бұрын
  • 🤔

    @user-ce5gf4im1m@user-ce5gf4im1m26 күн бұрын
  • Bayana ndi wa mcp

    @ChikumbutsoJohn-rs4tt@ChikumbutsoJohn-rs4tt26 күн бұрын
  • Chakwela ulibe nzelu nonse ndi mbava zokhazokha

    @user-zk7jw9up6m@user-zk7jw9up6m27 күн бұрын
  • Chilungamo chili poelatu tisamachedwe ndikufunsana mafunso apa, chakwela walakhula zambili chifukwa waona kuti luphanga likupita kwaiye because iyeyo ali mugulu la athu 4 ayimikidwa kutuluka ku America, chakwela alimo America yangopanga manyazi kwambili

    @WisikiBlack-gj4gu@WisikiBlack-gj4gu26 күн бұрын
  • Muziponya nkhani zimene zachitika.kumene osati zakale Big

    @MustaphaMvula@MustaphaMvula27 күн бұрын
  • Uyu ndiye manyi eneene

    @MustafaLikaomba@MustafaLikaomba26 күн бұрын
  • America has followed its laws as quoted, the bsn is applied in America not Malawi...in Malawi they're free and relaxed BUT not America, they don't entertain those issues

    @paulmakaula4937@paulmakaula493726 күн бұрын
  • Sindikuziwa kuti anthu Andale mumayanlhula mozungulira bwanji koma nkhaniyo mukuyiona kuti ikupita apo a president akuopa kuti nkhaniyo ndiyawo

    @mussamapira801@mussamapira80127 күн бұрын
  • Kodi Vuto ndilakut zinthu zi ndizagulu chifukwa zinakhala za anthu watha BweZi nda police omwe akut america yachita bwino kutelo

    @ChristopherBaluti@ChristopherBaluti27 күн бұрын
  • Chakwera mutu wake sugwila ntchito 😂😂😂😂mutsogoleri opoira Anthu akubvutika kwambiri no vote for 2025😂😂😂😂😂

    @anthonymhango9924@anthonymhango992427 күн бұрын
  • Mbava zokha okha izi mkuona zikuberekana iyaaa. Timakhalira kukapempha konko,. Sitikidzera mpoto ophika nsima

    @marypatriciamakuru226@marypatriciamakuru22627 күн бұрын
  • Chakwela is efeliaa

    @DylesMtenje@DylesMtenje26 күн бұрын
  • Dziko la malawi limadalu

    @user-og4oe5yp4w@user-og4oe5yp4w26 күн бұрын
  • Manyumba mwanga onse oganilizidwa zakuba asalowe. Yatero America. Simple

    @user-xz7mo8zy8f@user-xz7mo8zy8f27 күн бұрын
  • Makhotiso mukumapanga chinyengo mukudziwa kit anatigura chakwera

    @user-zl8fl7yp8q@user-zl8fl7yp8q25 күн бұрын
  • Chakwela nd I mbuzi ya president

    @patiencetebulo@patiencetebulo27 күн бұрын
  • Ukamamubwezera mawu munthu okuzuzula zimangowoneseratu kuti ukuvomereza kulakwakwako . Kunena zowona boma lachakwera ndirazimbava ndipo makhoti onse Akulamuliridwa ndi chakwera ndi chipanichake cha mcp. Akunkuyunso sangalankhule chirungamo chifukwanayenso ndibamva.

    @user-oe1lg4xo7w@user-oe1lg4xo7w26 күн бұрын
  • Wosawuka alibe mawu ,mukanakumana Kaye NDI anzanu wotsutsa boma akupatseni mayankhidwe

    @user-im7sc2my4w@user-im7sc2my4w27 күн бұрын
  • Chakwera ndi chitsilu amaleka kuyakhula chizungu chakwa America bwanji

    @NgomaRaheem@NgomaRaheem27 күн бұрын
  • Ndeakuti ma Court anthu akumalawi amatha kugwira ntchito kuposa America????😂😂😂 Koma Chakwera guys i think wapenga

    @ShabaniKuswere@ShabaniKuswere26 күн бұрын
  • Kodi nkhaniyo kumakothiko idapita liti? Koma mukungopondereza chifukwa mukudziwa kuti munaba limodzi .america isiye kaye kuthandiza Malawi kwa 10 month kaye tione kuti mulipanga solve bwanji dziko lamalawi

    @user-og4oe5yp4w@user-og4oe5yp4w26 күн бұрын
  • Amalawi ku opa America dziko lopanda yankho pa lokha

    @jonathanmalanda7742@jonathanmalanda774226 күн бұрын
  • America yachita bwano kutelo

    @petertaulo8014@petertaulo801427 күн бұрын
  • Kodi wakuba alindiufulu zopusa

    @MustafaLikaomba@MustafaLikaomba26 күн бұрын
  • Alibe mphatso yawu president!!

    @kubengovender6996@kubengovender699627 күн бұрын
  • Support criminal adha awa and wina akamati amuvotela😮

    @johnjoachim3820@johnjoachim382026 күн бұрын
  • Kumkuyu garu wa munthu.

    @petertaulo8014@petertaulo801427 күн бұрын
  • Zozungulira ayi tangoyankhani mafunso komanso palibepo mbalume pamenepo ndi Street thing answer the question pls

    @user-og8qm5qx8f@user-og8qm5qx8f27 күн бұрын
  • Makhothi ake ati,???? Ku Malawi kulibe mathoti anapangidwa Captured ndi mcp ngati injunction ya nankhumwa kutha years nde milandu zinazi anga kambe.. Tinawombera mfiti mmanja...

    @eliffagondewe8214@eliffagondewe821426 күн бұрын
  • Guys ma American siwofunika kumawasekelera eya zowona amapereka mathandizo Koma amakhara ndicholinga mudzikomo pamapeto adzakupusitseni then atenge zofunazo mosavuta and we need to know dziko lirilose limene mulimikangano ma American akango yamba kulowelerapo mapeto ake dziko limalowa nkhondo mcholinga azidzapangamo ma businesses azida zankhondo president wa Malawi akadapanda kulankhulapo mukadatiso ndiwogona kwambiri

    @chipanganofackison5185@chipanganofackison518526 күн бұрын
  • Chakwera is corrupt,thats why he is defending those people.

    @user-yk3wc9ei5g@user-yk3wc9ei5g25 күн бұрын
  • Dziko la Malawi limadalira kuphepmpha ku america komweko ndiye americawo awone zochita basi

    @user-og4oe5yp4w@user-og4oe5yp4w26 күн бұрын
  • Galu waluma mbuyache kkkkkk wapenga chakwera

    @user-un6qv6sj3h@user-un6qv6sj3h26 күн бұрын
  • Musavutike ndi kuganizaso chakwera ndi mbava.akanakhara wanzeru akanat America yandithandiza athuwa ndimbavadi

    @user-zl8fl7yp8q@user-zl8fl7yp8q25 күн бұрын
  • Chakwela ndi. Wakuba. Amange bas mboni ndine

    @DylesMtenje@DylesMtenje26 күн бұрын
  • Makhot anthu akugwila ntchito ndi emusip

    @user-hx6ly3cl8m@user-hx6ly3cl8m26 күн бұрын
  • 😂Galu wankota sakandira pachabe.les wait and see. wait

    @bensonmughandira@bensonmughandira26 күн бұрын
  • American tsinalakwe chakwelalayo ndiye wakuba kwambili mbava dzokhadzokha sitikumu funa pamozi ndi kunkuyu achoke dpp boma 2025 tatopa komaso joice banda usiletu kunamidza athu komaso athu muchenjele Joyce anaba ndalama ya ndege anayda yekha ndiye chenjelani mudza wona mavuto ngati womwewa komasotu Joyce banda alinali ku mcp motelo idzi akupanga dala akupanga akufuna kuti dpp isawine ku mwela akufuna dpp ndi pp pakati akudziwakale kuti mcp ndiyo winawina kale chonde amalawi musapange mistake kawili Joyce ndiwo tsokonedza my name is Patrick form South Africa

    @YohanePatrick-lc2lq@YohanePatrick-lc2lq26 күн бұрын
  • Makondela inu koma akanakhala azipani zina bwezi mutamanga kalekale

    @user-uv7yq1fx4r@user-uv7yq1fx4r26 күн бұрын
  • Kodi kumkuyu mmutu mwake mulimzeru?

    @ShabaniKuswere@ShabaniKuswere26 күн бұрын
  • Sizikugwilizana watsala iwe

    @alexmkolongo3089@alexmkolongo308927 күн бұрын
  • kumkuyunso ali limodzi muwumbsva

    @JafaliAkimu-ll1bf@JafaliAkimu-ll1bf26 күн бұрын
  • America sadalakwitse ,manyumba mwathu,tikaona kuti mwana wathu akuba,amasalidwa ndi abale amakolo Ake kuti asabwere kunyumba kwathu, chifukwa Cha mbiri yakuba,ndiye dziko Lili ndi anthu akuba ndye ma mericans asekere zupusazo?

    @CyprianoSandalamu@CyprianoSandalamu26 күн бұрын
  • Eee achita bwino pule akwiya

    @user-zg9se4rw6v@user-zg9se4rw6v26 күн бұрын
  • Koma abaalee 😂

    @violetnkhoma8535@violetnkhoma853527 күн бұрын
  • You are not honest Mr President, kutha mau chifukwa aletsa mbava kulowa dziko lawo?? Mr President mukanakhala wina mukanauza a ma court athu azifulumiza milandu osat mpaka 4yrs milandu isanathe. Munthu womvesa chisoni Chakwera.

    @JonesChingaya-yf4gg@JonesChingaya-yf4gg26 күн бұрын
  • Akuzengeleza kuzenga milandu chifukwa chani

    @user-un6qv6sj3h@user-un6qv6sj3h26 күн бұрын
KZhead